sent_id
stringlengths
3
7
english
stringlengths
3
1.06k
chichewa
stringlengths
4
3.03k
topic
stringclasses
8 values
source
stringclasses
17 values
en2502
Agricultural practices that ensures uniform crops are encouraged in order to have few but high quality grades of leaf
Njira zaulimi zothandiza kuti mbewu iwoneke mofanana zimalimbikitsidwa kuti pakhale masamba ochepa koma apamwamba
agriculture
agriculture document
en2503
CG 9 is a newly released medium duration, Virginia type groundnut variety
CG9 ndi mbewu yatsopano yomwe imacha mwapakatikati, ndi mtundu wa mtedza wa virginia
agriculture
agriculture document
en2504
It has a yield potential of 2500 kg/ha
ili ndi kuthekela kotulutsa zokolola zokwana 25000kg pa hectare
agriculture
agriculture document
en2505
CG 12 is a newly released short duration, Spanish type groundnut variety
CG 12 ndi mbewu yatsopano yosachedwa kukhwima, ndi mtundu wa mtedza wa spanish
agriculture
agriculture document
en2506
It reaches 50% flowering in about 34 days.
theka la mbewu limamasula pa masiku 34
agriculture
agriculture document
en2507
It is tolerant to drought and groundnut rosette disease.
imapilira ku chilala ndi matenda a khate a mtedza
agriculture
agriculture document
en2508
It takes 100 to 110 days to reach maturity
zimatenga masiku 100 mpakana 110 kuti zikhwime
agriculture
agriculture document
en2509
During pegging, only hand weeding should be done to avoid damage to developing pods.
pamene zayamba kubereka, mukhona kuzula udzu ndi manja okha kuopa kuononga mbewu
agriculture
agriculture document
en2510
Tikolore is another indeterminate variety
tikolore ndi mbewu ina yosapanganika
agriculture
agriculture document
en2511
In the first place the farmer can choose to apply only Rhizobium inoculants for a certain yield target
choyambilira mlimi akhonza kusankha kuthira rhizobium inoculant yekha kapena kuti mbewu zosankhika
agriculture
agriculture document
en2512
Secondly, a farmer can choose to apply fertilizer only without the inoculum.
kachiwiri, mlimi akhonza kusankha fetereza okuti athire opanda inoculum
agriculture
agriculture document
en2513
Thirdly the farmer can choose to apply both rhizobium inoculants and nitrogenous fertilizer to the crop in order to achieve a very high yield target
kachitatu, mlimi akhonza kusnakha kuthila inoculant wa rizobium pamodzi ndi fetereza wa nayitrojeni kuti achulutse zokolola
agriculture
agriculture document
en2514
ICPL87015 is a nearly maturing and high yielding (up 2,500kg/ha)
mbewu ya ICPL87015 imakhwima mwachnu ndi kutulutsa zokolola zochuluka ( zokwana 2500kg pa hekitala)
agriculture
agriculture document
en2515
If ash is used to treat cowpea grain, apply 25% ash to the volume of the grains
ngati mumagwiritsa ntchito phulusa posunga mbewu ya nandolo, thirani 25% ya phulusa ku mbewuyo
agriculture
agriculture document
en2516
Kayera yields an average of about 880kg/ ha
kayera amatulutsa zokolola zosachepera 880kg pa hekitala
agriculture
agriculture document
en2517
It takes 55 days to attain a total of 55 leaves and 50% flowering.
zimatenga masiku 55 kuti zikhale ndi masamba okwana 55 komanso kuti theka la mbewu zonse limasule maluwa
agriculture
agriculture document
en2518
Sesame is interplanted with cereals and grain legumes.
bzalani chitowe mophatikiza ndi chimanga ndi nyemba
agriculture
agriculture document
en2519
Its average hieght is about 125 cm and flowers about 60 days after emergence.
zimatalika osachepera 125cm ndipo zimayamba kumasula maluwa pakatha masiku 60
agriculture
agriculture document
en2520
It produces bolls which mature and start opening at about 117 days after crop emergence
zimabereka tizipatso tomwe timakhwima nkuphulika paktha masiku 117 mbewu zikamera
agriculture
agriculture document
en2521
It gives 37 % more seed cotton yield than Makoka 2000, 86 % over RASAM 17 and 29 % over IRM 81
imatulutsa zokolola zoposera 37% mbewu ya thonje ya makoka 2000, 86% mbewu ya RASAM 17 ndi 29% kuposa mbewu ya IRM 81
agriculture
agriculture document
en2522
Its average height in Malawi is about 126 cm and flowers about 56 days after emergence
ku malawi kuno zimatalika 126cm ndi kuyamba maluwa pakatha masiku 56 zikamera
agriculture
agriculture document
en2523
Whether the ridge is spaced at 75 cm or 90 cm, planting stations should be 60 cm apart within the ridge
kaya mizere yatalikilana kwa 75cm kapena 90cm, mapando atalikilane 60cm mkati mwa mzere
agriculture
agriculture document
en2524
The seed should be sown at 20 mm depth in wet soil.
mbewu ibzalidwe 20mm kuchoka pansi pa nthaka yonyowa
agriculture
agriculture document
en2525
This gives a seed rate of 25 kg per hectare
mbewu yoyenera kubzalidwa pa hekitala ndi yokwana 25kg
agriculture
agriculture document
en2526
Farmers are advised to follow planting instructions printed on the seed pack for hybrid and Bt cotton varieties
alimi akuyenera kutsatila ndondomeko zobzalira zimene zalembedwa pa thumba la mbewu ya hybrid ndi Bt cotton
agriculture
agriculture document
en2527
A delay in thinning will result in plants severely competing for nutrients, sunlight and moisture
kuchedwa kupalila kumapangitsa kuti mbewu zizikanganilana zakudya,dzuwa ndi chinyontho
agriculture
agriculture document
en2528
Fertilizer recommendation for cotton is 34 kg N, 45 kg P205 and 22 kg Sulphur per hectare where the crop is stunted because of nutrient deficiency
fetereza oyenerera kuthira ku thonje ndi 34kg n. 45kg P205 ndi 22kg Sulphur a hekitala pamene mbewu zikupinimbira chifukwa cha kusowa kwa michere mu nthaka
agriculture
agriculture document
en2529
apply 23:10:5+6S+1.0Zn at the rate of 100 kg per hectare
thirani fetereza wa 23:10:5+6S+1.0Zn pa mlingo wa 100kg pa hekitala
agriculture
agriculture document
en2530
At first flower, apply 52 kg CAN per hectare.
maluwa oyamba akamasula, thirani 52kg ya CAN pa hekitala
agriculture
agriculture document
en2531
Farmers should not wait for dry spells before weeding because by the time there is a dry spell, weeds may already have overcrowded the small plants
alimi asadikile kuti mvula isiye kuti apalire chifukwa pamene mvula ikusiya udzu umkhala utadzakuta mbewu zing'onozing'ono
agriculture
agriculture document
en2532
Early weeds in cotton can also be controlled by applying Pendimethalin 500 EC (Dinitroaniline).
thirani Pendimethalin 500 EC (Dinitroaniline) kuti muthane ndi udzu wakumayambiliro mminda ya thonje
agriculture
agriculture document
en2533
Protect the orchard from fire hazards by weeding and making fire breaks of at least 3m wide around it
tetedzani munda wanu wa zipatso ku ziopsezo za moto popalila udzu ndikulimira mmbali pamulingo wa 3m kuti moto usamafike
agriculture
agriculture document
en2534
The planting holes should be 90cm in diameter and 90cm deep.
maenje obzalila azikhala 90cm kukula ndi kutalika komwe
agriculture
agriculture document
en2535
Soils should be deep, fertile and free draining
dothi lidzikhala lakuya, lachonde ndi lolowa bwino madzi
agriculture
agriculture document
en2536
Fertilizer applications should be based on soil and leaf analysis
thriani fetereza malingana ndi zotsatila ka kafukufuku wa dothi ndi masamba
agriculture
agriculture document
en2537
Apply half of the chemical fertilizer at the beginning of the rainy season and the other half when the rains are tailing of
thirani theka la fetereza kumayambiliro kwa nyengo ya mvula ndi kumaliza theka lotsala kumapeto kwa nyengo ya mvula
agriculture
agriculture document
en2538
Citrus can be grown in many areas depending on species and varieties.
zipatso zitha kubzalidwa madera ambiri malingana ndi mtundu wachipatso komanso mbewu
agriculture
agriculture document
en2539
The best time to apply manure is when preparing land
nthawi yabwino yothira manyowa ndi pamene mukusosa mmunda
agriculture
agriculture document
en2540
Plant with the first planting rains (rains of 50mm or wetting to a depth of 15cm)
bzalani ndi mvula yoyambilira (pamen mvula yagwa 50mm kapena dothi lanyowa 15cm kupita pansi)
agriculture
agriculture document
en2541
Supplementary watering should be done as required.
thilirani mbewu pamene kuli koyenera kutero
agriculture
agriculture document
en2542
Control is by hand picking and crushing of caterpillars.
mukhonza kuthana ndi mbozi potola ndi kunyenya ndi manja
agriculture
agriculture document
en2543
Plough deeply and incorporate 5 to 10kg of compost or khola manure per square metre
limani mwakuya kwambiri ndi kusakaniza 5 mpakana 10kg ya manyowa a zinyalala kapena manyowa a khola pa sikweya mita
agriculture
agriculture document
en2544
Apply 3 to 5kg of well decomposed manure per square meter and mix thoroughly with the soil.
thirani 3 mpakana 5kg ya manyowa pa sikweya mita ndikusakanika bwino ndi dothi
agriculture
agriculture document
en2545
The caterpillars eat the leaves
mbozi zimadya masamba
agriculture
agriculture document
en2546
Cinnamon requires warm and wet conditions with moderate temperatures of about 27ºC
Cinnamon amafunika nyengo yotentha komanso ya chinyezi wambiri ndi kutetha kwama digiri 27
agriculture
agriculture document
en2547
Aphids attack new shoots causing stunted growth
nsabwe za mmasamba zimadya masamba ophukila kumene kupangisa kuti zipinimbile
agriculture
agriculture document
en2548
Vegetables are easily attacked by many insect pests and diseases
mbewu zamasamba sizichedwa kugwidwa ndi tizirombo tambiri komanso matenda
agriculture
agriculture document
en2549
The adult flies are tiny about 1mm and yellowish in colour with white powdery wings
ntchentche zikakula zimakhala zazing'ono kwambiri kufika 1mm komanso za makaka achikasu ndi mapiko okhala ndi ufa woyera
agriculture
agriculture document
en2550
The disease occurs in orchards established on recently opened land which had natural trees
nthendayi imapezeka mminda ya zipatso yomwe yangokhadzikitsidwa kumene pa malo amene panali mitengo yachilengedwe
agriculture
agriculture document
en2551
Those that cannot die by ring barking must be dug out with as much root system as possible.
mitengo yomwe sizingaume pochotsa makungwa iyenera kukumbidwa mpaka mitsitsi yonse ichoke
agriculture
agriculture document
en2552
Pineapples can be established from suckers, slips and tops
nanazi zimadzalidwa kuchokela ku misitsi, ziphuthu ndi zimasamba
agriculture
agriculture document
en2553
The yields of mango are low in cool areas because of incidences of powdery mildew
mango amakololedwa ochepa mmadera ozizila chifukwa cha kupezeka kwa nthenda ya powdery mildew
agriculture
agriculture document
en2554
Presently yields of fully grown improved mango trees range from 200 to 500 fruits per tree
padakali pano, mtengo umodzi wa mbewu yamakono ukumatulutsa mango 200 mpakana 500
agriculture
agriculture document
en2555
Avocado pears are important food and cash crop
mapeyala ndi mbewu yofunikila ya chakudya komanso malonda
agriculture
agriculture document
en2556
The growing of available local cultivars should be encouraged especially where farmers have no access to improved varieties
kulima mbewu zamakolo kukuyenera kulimbikitsidwa makamaka kwa alimi amene alibe kuthekera kopeza mbewu zamakono
agriculture
agriculture document
en2557
Local cultivars such as Boloma and Domasi which are big and sweet, and small mangoes such as Waka, Nthulura and Kapantha that are widely adapted should be encouraged.
mbewu yamakolo ya Boloma ndi Domasi yomwe imakhala yaikulu ndi yokoma, mango aang'ono monga Waka, Nthulura and Kapantha amene anadzalidwa kwambiri akuyenera kulimbikitsidwa
agriculture
agriculture document
en2558
Plant trees in December or January for successful establishment
bzalani mitengo mu December kapena January kuti zikhadzikike bwino
agriculture
agriculture document
en2559
Apply 5 to 10kg of well decomposed manure per tree at the beginning of the rainy season
thirani 5 mpakana 10kg ya manyowa owola bwino pa mtengo umodzi umodzi kumayambiliro kwa nyengo ya mvula
agriculture
agriculture document
en2560
The fruit weighs 0.5 to 1.0kg and is of excellent quality
chipatsocho chimalemela 0.5 mpaka 1.0kg ndipo imakhala yokongola bwino
agriculture
agriculture document
en2561
It attacks the base of the tree and may eventually affect the root system
imagwira pansi pa mtengo ndipo imatha kukhudza mitsitsi
agriculture
agriculture document
en2562
The outer layer contains more sugars and vitamins than inner layer
Kunja kwake kumakhala ndi shuga ndi ma vitamini ochuluka kusiyana ndi mkati
agriculture
agriculture document
en2563
All unwanted trees should be ring-barked 2 years in advance and left to die to reduce the risk of Armillaria infection.
mitengo yonse yosafunikila imayenera ichotsedwe zikungwa kuti iwume ndi kufa zaka ziwiri zambuyo ndicholinga choteteza kuti isagwidwe ndi matenda a Armillaria
agriculture
agriculture document
en2564
Pawpaw is fairly drought-tolerent but irrigation is required after prolonged dry periods
mapapaya amapilira ku nyengo ya chilala komabe kuthilira kumafunika ngati nyengo yapitilila kwmabiri
agriculture
agriculture document
en2565
Seed may be stored up to 3 years
mbewu itha kusungidwa mpakana zaka zitatu
agriculture
agriculture document
en2566
It should be noted, however, that germination percentages declines with storage period
mukuyenera kudziwa kuti chiwerengero cha mbewu zomela chimatsika malingana ndi nthawi imene mbewu yasungidwa
agriculture
agriculture document
en2567
Seedlings should be transplanted when 6 weeks old or 30cm tall
okelani mbewu zikatha masabata 6 kapena zikatalika kwa 30cm
agriculture
agriculture document
en2568
Pawpaw have potential yields of up to 140kg per tree
mapapaya ali ndi kuthekela kotulutsa 140kg pa mtengo
agriculture
agriculture document
en2569
Pawpaws for sale at the local market should be picked at the first indication of the yellow colour to facilitate transportation and storage in the market process.
mapapaya a malonda akuyenera kukololedwa akangoyamba kumene kupsa ndi cholinga chakuti anyamulike ndi kusungika bwino pamene mukukonzekela zogulitsa
agriculture
agriculture document
en2570
The fruit must be handled with great care to avoid scratching.
zipatso zikuyenera kunyamulidwa mosamala kupewa kukala
agriculture
agriculture document
en2571
Pigs should normally be fed in the khola
nkhumba zikuyenera zizidyetsedwera mu khola
agriculture
agriculture document
en2572
Hand weeding should be done near the Coffee trees while a hoe should be used away from the trees to avoid bruising the stem and roots.
dzulani udzu ndi manja m'mbali mwa mtengo wa khofi pamene mbali zotalikilana mukhonza kupalira ndi khasu
agriculture
agriculture document
en2573
Mushrooms ready for the market are divided into various grades depending on size and degree of maturity
bowa wogulitsa amaikidwa mmagawo awirir malingana ndi kakulidwe komanso nthawi imene amatenga kuti akhwime
agriculture
agriculture document
en2574
Presently, 2 types of mushrooms are grown in Malawi, that is oyster and button mushroom
pakadali pano, mitundu iwiri ya bowa ikulimidwa malawi, bowa wa oyster ndi button
agriculture
agriculture document
en2575
Okra does not transplant well and should therefore be directly sown on ridges or beds
therere silichita bwino likawokeledwe kotero ndikofunika kubzalilatu osafesa
agriculture
agriculture document
en2576
Okra thrives in low altitude areas with warm climate
therere silikula bwino malo otsika amene ali ndi nyengo yotentha
agriculture
agriculture document
en2577
Cabbage can yield 11,000kg to 70,000kg per hectare depending on variety and management.
kabichi akhonza kutulutsa 70,000kg pa hekitala malingana ndi mtundu wa mbewu ndi kasamalidwe
agriculture
agriculture document
en2578
Vegetables are easily attacked by many insect pests and diseases
masamba sachedwa kugwidwa ndi tizilombo ndi nthenda zambiri
agriculture
agriculture document
en2579
Paprika belong to the same family of crops such as tomato, tobacco, egg plant and potato hence have similar diseases, insect pests and nematode problems.
paprika ali mgulu limodzi la mbewu ngati tomato, fodya, mabilinganya ndi mbatatesi kotero amakhala ndi matenda ndi tizilombo tofanana
agriculture
agriculture document
en2580
Tea should be kept free from weeds to minimize competition for moisture and nutrients
tiyi asamakhale ndi udzu kuti tichepetse kukanganilana kwa chinyontho ndi zakudya
agriculture
agriculture document
en2581
Irrigation of Coffee is important to increase productivity
ndibwino kuthirirra khofi kuti zokolola zichuluke
agriculture
agriculture document
en2582
Dried chillies should be stored in hessian sacks
tsabola owuma asungidwe mmasaka
agriculture
agriculture document
en2583
Being leafy vegetables, rape, mustard and Chinese cabbage require adequate nitrogen supply
pokhala mbewu zamasamba, lepu, mpiru ndi chinese cabbage pamafunika kukhala nayitrojeni wokwanila
agriculture
agriculture document
en2584
Seedbeds should be sterilized by burning maize stalks to control damping off diseases (Pythium, Fusarium, Phytophthora, Rhizoctonia spp.) and nematodes.
mabedi a mbewu akuyenera kuyeletsedwa potentha mapesi ndi moto kuopesa kufala kwa matenda monga: (Pythium, Fusarium, Phytophthora, Rhizoctonia spp.) ndi tizilombo
agriculture
agriculture document
en2585
Harvesting is done through out the year as flowers are produced all year round.
mumakolola chaka chonse chifukwa maluwa samasiya kumasula kwa chaka chonse
agriculture
agriculture document
en2586
The seed nuts should be selected from high yielding trees
mtedza wa mbewu ukuyenera kusankhidwa kuchokela ku mitengo yobereka kwambiri
agriculture
agriculture document
en2587
Farmers are encouraged to raise their own seedlings preferably in groups under the supervision of the Coffee Extension Staff
alimi amalangizidwa kufesa mbewu zawo moyang'anilidwa ndi alangizi otsata za mbewu ya khofi
agriculture
agriculture document
en2588
Coconut can grow well even in low rainfall areas, especially when ground water conditions are favourable
coconut amakula bwino ngakhale ku malo otentha, makamaka kumene madzi a mu nthaka akupezeka
agriculture
agriculture document
en2589
Pluck mushrooms when fully grown
thyolani bowa akamalidza kukula
agriculture
agriculture document
en2590
Avoid storing nuts on the farm for longer than 2 months as quality will be reduced.
pewani kusunga mtedza pa munda kwa nthawi yaitali yopitilila miyezi iwiri chifukwa zimawononga mtedza
agriculture
agriculture document
en2591
Roots are ready for harvesting when they are 3months old from sowing
misitsi ikhonza kukololedwa ikakwana miyezi itatu
agriculture
agriculture document
en2592
Cucumbers are relatively shallowrooted and require irrigation in most parts of the country.
nkhaka zili ndi miistsi yaifupi kotero imafunika izizthililidwa madera ambiri mdziko muno
agriculture
agriculture document
en2593
Mulch around the basin with grass, dried leaves or maize stover
kwililani maenje ndi udzu, masamba owuma kapena mapesi a chimanga
agriculture
agriculture document
en2594
Keep the plants in a cool place, under shade and water daily
sungani mbewu pa malo ozizila, pansi pa dzuwa ndikumathirira tsiku ndi tsiku
agriculture
agriculture document
en2595
Mix the compost with the top soil and fill in the hole
sakanizani komposti ndi dothi lapamwamba ndikuthira mudzenje
agriculture
agriculture document
en2596
Keep watering this compost heap every day.
pitilizani kuthirira muli wa komposti tsiku ndi tsiku
agriculture
agriculture document
en2597
Coffee suffers attacks from a number of pests which severely limit production
khofi amagwidwa ndi tizilombo tambiri tomwe timapititsa pansi zokolola
agriculture
agriculture document
en2598
The most serious weather conditions that have negatively affected agricultural productivity in Malawi are dry spells, seasonal droughts, intense rainfall, riverine floods and flash floods
Nyengo yovuta kwambiri yomwe yasokoneza ntchito zaulimi Malawi muno ndi chilimwe, chilala, mvula yamkuntho, kusefukira kwamadzi komanso kusefukira kwamadzi.
agriculture
agriculture document
en2599
Dry spell is a period of dryness that has little or no effect on soil moisture or water levels.
Dry spell ndi nthawi yowuma yomwe ilibe mphamvu pang'ono kapena yopanda mphamvu ya chinyontho mu nthaka kapena madzi.
agriculture
agriculture document
en2600
Dry spells turn into droughts when they last 3 to 4 months.
nyengo youma zimasanduka chilala zikatha miyezi itatu kapena inayi.
agriculture
agriculture document
en2601
Drought is a result of a prolonged deficiency of precipitation over an extended period of time usually over a season or more.
Chilala chimabwera chifukwa cha kuchepa kwa mvula kwa nthawi yayitali nthawi zambiri pakapita nyengo kapena kuposerapo.
agriculture
agriculture document