sent_id
stringlengths
3
7
english
stringlengths
3
1.06k
chichewa
stringlengths
4
3.03k
topic
stringclasses
8 values
source
stringclasses
17 values
en2402
s. Their feeding activity results into yellowing and defoliation of leaves
kadyedwe kawo kamapangisa chikasu ndi kuthothoka kwa masamba
agriculture
agriculture document
en2403
Cassava green mite feeds on young leaves and tender shoots.
chiswe chamu chunangwa chimadya masamba aang'ono komanso ofewa
agriculture
agriculture document
en2404
It is characterized by mottled and curled leaves and transmitted by white flies.
zizindikilo ndi masamba akuda komanso okwinyika ndipo amabweretsedw andi tintchentche toyera mtundu
agriculture
agriculture document
en2405
Farmers should be advised to be on the lookout for any insect pest and disease outbreaks
alimi akulangizidwa kukhala atcheru podziwa tizilombo ndi matenda amene akuvta nthawi imeneyo
agriculture
agriculture document
en2406
After the cassava crop has reached maturity, the quality of roots of most varieties often deteriorates after 15 months of growth.
chinangwa chikafika pokhwima, kawonekedwe ka mitsisi ya mbewu zambiri kamawonongeka pakatha miyezi khumi ndi isanu
agriculture
agriculture document
en2407
Cassava Brown Streak Disease is caused by a virus and transmitted by White flies
nthenda ya chinangwa ya brown streak imayamba chifukwa cha tincthenthce ta mtundu oyera
agriculture
agriculture document
en2408
On the leaves the disease appears as patches of yellow areas mixed with normal green colour.
nthendayi imaoneka ngati madontho ofiila pa masamba obiliwira
agriculture
agriculture document
en2409
The damaged leaves do not become distorted in shape as in cassava mosaic disease
masamba owownongeka samasintha maonekedwe ngati momwe imapangitsila nthenda ya chinangwa ya mosaic
agriculture
agriculture document
en2410
Farmers using sweet varieties should process their cassava roots using the cassava chip (makaka) methods if the end product is to be used for human consumption.
alimi amene amalima mbewu yosekemela akuyenera kusunga chinangwa ngati makaka ngati chiyenera kugwiritsidwa ntchito ngati chakudya ch anthu
agriculture
agriculture document
en2411
Farmers are encouraged to store the cassava in flour or chip form
alimi amalimbikitsidwa kusunga chinangwa ngati ufa kapena makaka
agriculture
agriculture document
en2412
Farmers should store cassava chips (makaka) in cool dry places after packing them in gunny bags
alimi akuyenera kusunga makaka a chinangwa mmalo ozizila akalongeza mmasaka
agriculture
agriculture document
en2413
To avoid weevil damage apply 25 g of Actellic Super Dust to 50kg makaka or 25g of Super grain dust to 50kg of makaka
kupewa kuti zingawonongeke ndi anankafumbwe thirani 25g ya catelic super dust ku 50kg kapena 25g ya Super grain dust ku 50kg ya makaka
agriculture
agriculture document
en2414
Cassava can be sold as fresh roots, chips and flour
chinangwa chimagulitsidwa chachiwisi, makaka ndi ufa
agriculture
agriculture document
en2415
Orange fleshed varieties are a good source of vitamin A
mbatata zofiila ndi gwero labwino la vitamini A
agriculture
agriculture document
en2416
Leaves of Sweetpotato are used as relish (ndiwo) and are good source of vitamin A.
kholowa amagwiritsidwa ntchito ngati ndiwo ndipo ndi gwero la bwino la vitamin A
agriculture
agriculture document
en2417
Orange, very early maturity to allow for piece meal harvesting during lean times
mbewu yofiila imacha nsanga kuthandiza nathu kupeza chakudya mu nyengo yosowekela
agriculture
agriculture document
en2418
The vine should be cut 10-15 cm away from the base to reduce incidence of sweetpotato weevil
kholowa adulidwe 10-15cm kuchokela pansi kuti tipewe kupezeka kwa anankwfumbwe
agriculture
agriculture document
en2419
Where rainfall is not reliable, planting should be completed by mid-January
madera amene mvula simadalilika, kubzala kulekeze pakati pa mwezi wa January
agriculture
agriculture document
en2420
Farmers who plant their Sweetpotatoes in dimba gardens like in the Shire Valley flood plain should plant their crop as soon as water has receded
alimi amene amabzala mbatata mmadimba monga ngati ku shire valley akuyenera abzale madzi akaphwela
agriculture
agriculture document
en2421
Garlic does not tolerate excessive humidity or rainfall
adyo sapilira ku nyengo ya chinyezi kapena mvula yambiri
agriculture
agriculture document
en2422
Cuttings should be 25 to 30cm long.
zodula zanu zikhale zotalika 20 mpaka 30cm
agriculture
agriculture document
en2423
For root production, the ridges should be spaced at 90cm and planting stations at 30cm
kuti mizu ikule, talikisani mizere kwa 90cm ndi mapando kwa 30cm
agriculture
agriculture document
en2424
Where white grubs are a problem, do not plant on soils rich in organic matter
malo amene ma white grubs ndi vuto lalikulu, musabzale pamene pali manyowa azinyalala ambiri
agriculture
agriculture document
en2425
Soils which are water logged should be avoided.
pewani dothi lokumwa madzi ambiri
agriculture
agriculture document
en2426
Weed early particularly during the first 6 weeks of establishment
palirani mwachangu makamaka masambata asanu ndi imodzi oyambilila mukangobzala
agriculture
agriculture document
en2427
Where the crop cover is poor, hand weeding should continue as required.
pamene zomela zotchinga zili zosachita bwino mungota kuchotsa udzu ndi manja
agriculture
agriculture document
en2428
Sweetpotato weevil (Cylas formicarius) This is the most destructive insect pest of Sweetpotato
nankafumbwe wa mbatata ndi kachilombo kowonong akwmbiri mbatata
agriculture
agriculture document
en2429
Control is by practicing crop rotation, use of resistant varieties namely: Yoyera, Babache, Kenya, Kakoma, Semusa, Mugamba, Tainoni, filling cracks when the roots start bulking, and timely harvesting
njira yopewera ndi kupanga ulimi wakasinthasinthan ndipogwiritsa ntchito mbewu zololela monga; Yoyera, Babache, Kenya, Kakoma, Semusa, Mugamba, Tainoni, kukwilira ming'alu pamene mbatata zayamba kuphuka komanso kukolola nthawi yabwino
agriculture
agriculture document
en2430
White grubs cause serious damage to roots and tubers of Sweetpotato.
ma white grubs amaononga misitsi ndi mbatata
agriculture
agriculture document
en2431
About 370 bundles of sweetpotato vines are required to plant one hectare.
pa hekitala pamafunika mbewu ya kholowa mitolo 370 kuti mubzale
agriculture
agriculture document
en2432
Never leave the crop in the field for a longer time otherwise the sweetpotato weevils will heavily attack the tubers hence reducing the quality and quantity of usable tubers
osasiya zokolola zanu mmunda kw anthawi yaitali chifukwa zimagwidwa ndi anankafumbwe amene amaononga mbatata zabwino
agriculture
agriculture document
en2433
Potatoes locally known as Kachewere grow successfully in areas of high altitude, which have a cool climate and adequate rainfall.
kachewere amachita bwino mmadera okwera amene amakhala ndi nyengo yotentha bwino ndi mvula yokwanira
agriculture
agriculture document
en2434
Soils should be free-draining, deep and rich in organic matter with soil acidity of pH5.0 to 6.5
dothi lizikhala lolowa bwino madzi, komanso la manyowa okwanila bwino ndi asidi wa mu nthaka okwanila 0.5ph mpakana 6.5
agriculture
agriculture document
en2435
Plough deeply and break soil clods to make a fine tilth.
limani pansi kwambiri ndikuswa zigulumwa kuti mupange donthi lofewa bwino
agriculture
agriculture document
en2436
After ridging make grooves on top of ridges 15cm deep
mukapanga mizere, kumbani ngalande a 15cm pamwamba pa mzere
agriculture
agriculture document
en2437
Apply 200kg of D compound per hectare.
thirani 200kg ya D compound pa hekitala
agriculture
agriculture document
en2438
Three to four weeks after crop emergence, top dress with 200kg of CAN per hectare.
pakatha masabata atatu kapena anayi thirani fetereza wokulitsa wa CAN 00kg pa hekitala
agriculture
agriculture document
en2439
Apply 20g per meter of ridge length using 5 cupfuls of cup No.5.
thirani 20g pa mita ya mzere uliwonse pogwiritsa ntchito makapu 5 a cup no. 5
agriculture
agriculture document
en2440
A potato field should be weeded twice during the growing season.
munda wa kachewere uyenera kupalilidwa kawiri pa chaka
agriculture
agriculture document
en2441
Aphids are controlled by spraying with Malathion 25WP or Dimethoate 20WP
kuti muthane ndi nsabwe za mmasamba thirani mankhwala a Malathion 25W kapena Dimethoate 20WP
agriculture
agriculture document
en2442
Fortunately this disease in Malawi attacks the crop later in the season than Late Blight
mwa mwayi, nthendayi imakhudza mbewu kumapeto kwa nyengo yolima kusiyana ndi leaf blight
agriculture
agriculture document
en2443
Tuber Moth damage can be avoided by earthing up
agulugufe owononga mbewu akhonza kupewedwa pokwilira ndi dothi
agriculture
agriculture document
en2444
This should be done repeatedly at intervals of 10 to 14 days
chitani izi mobwwerezabwereza kwa masiku khumi mpaka khumi ndi anayi (masabata awiri)
agriculture
agriculture document
en2445
If the plants are infected in the later stages of development, when tubers are developing, the bacteria will get into the tubers and survive there.
ngati mbewu zagwidwa ndi matenda pamene zatsala pang'ono kukhwima, mbatata zikayamba, nthendayi imabisala mu mbatata ndikukhala m'menemo
agriculture
agriculture document
en2446
Seed tubers should further be protected by dusting them with one sachet (40g) of Pirimiphos- methyl (Actellic) per 90kg sack of potatoes
mbatata za mbewu zikuyenera kutetezedwa pothiridwa mankhwala a ufa sacheti limodzi lokwana 40g la Pirimiphos- methyl (Actellic) pa 90kgya thumba la mbatata
agriculture
agriculture document
en2447
There is no chemical control measure.
palibe njira yogwiritsa ntchito mankhwala
agriculture
agriculture document
en2448
Since the virus also spreads through seed, farmers are recommended to use clean seed only.
popeza mbewunso zimagwidwa ndi matenda, alimi akulangizidwa kuwgiritsa nthcito mbewu zomwe zilibe matenda
agriculture
agriculture document
en2449
The potato crop is mature when leaves turn naturally yellow or the top dies off.
mbewu ya mbatata imakwima masamba akachita chikasu or masamba apamwamba akayoyoka
agriculture
agriculture document
en2450
Leaves tend to be upright and are generally pale yellow.
masamba amakhaala oongoka ndipo nthawi zambiri amakahala otumbululuka achikasu
agriculture
agriculture document
en2451
It is best controlled through crop rotation and use of chemical Nematicides such as Furadan
imapewedwa bwino popanga ulimi wakasinthasintha ndi kugwiritsa ntchito mankhwala a nematicides monga furadan
agriculture
agriculture document
en2452
Potato for consumption should be stored in darkness
sungani kadyewere wa chakudya mu chipinda cha mdima
agriculture
agriculture document
en2453
Storage does not improve quality of the potatoes therefore best quality crop should be stored from the start
kusunga mbatat sikumawonjezela kawonekedwe kabwino ka mbatata kuteloko mbatata za mbewu zisungidwe kumayambiliro
agriculture
agriculture document
en2454
The shelf life of potatoes for consumption can be prolonged by keeping them at low temperatures less than 90C
nthawi imene mbatata ya chakudya ingasungidwe mopitilila ndi pamene yasungidwa pa ma dgili okwana 90
agriculture
agriculture document
en2455
Potato tubers for seed should be stored in Diffused Light Store
mbewu ya mbatata isungidwe muchipinda chowala
agriculture
agriculture document
en2456
Once green and under cool conditions, seed potato can store for 3 months
mbewu ya kachewere ikhonzi kusungidwa kwa miyezi itatu zikangobiliwila ndi kusongidwa malo ozizila
agriculture
agriculture document
en2457
Agricultural chemicals not normally used on tobacco should never be allowed to come in contact with tobacco during production, curing or in storage
mankhwala mbewu amene samathiridwa ku fodya sakuyenera kuyikidwa pafupi ndi fodya pa nthawi yolima, yoyanika ndikusunga
agriculture
agriculture document
en2458
Farmers are advised not to store any chemicals in tobacco barns and holding sheds
alimi amalangizidwa kuti asamasunge mankhwala mma balan a fodya
agriculture
agriculture document
en2459
The choice of tobacco type and/or variety depends on trade requirement, farmer preference and prevailing climatic and soil conditions
chisankho cha mtundu wa mbewu ya tobacco amene mukufuna kulima zimatengera ndi mmene msika ukufinila, kuufna kwa mlimi, nyengo ya dera ndi momwe nthaka ilili
agriculture
agriculture document
en2460
Growers who are interested to use introduced varieties should follow appropriate procedures for importation
alimi amene ali osangalatsidwa kugwiritsa ntchito mbewu yatsopano akuyenera atsatile ndondomeko zoyenera zogulira mbewu kuchokela dziko lina
agriculture
agriculture document
en2461
It is recommended that the length of seed beds should be 30m or any convenient length and 1m wide
mabedi a mbewu ovomelekeza amayenera akhale 30m mulitali ndi 1m mulifupi
agriculture
agriculture document
en2462
Nursery sites should be properly fenced to ensure protection from stray animals and other pests, strong wind and airborne diseases.
manazale akuyenera kumangilidwa mpanda kuti atetezeke ku nyama zoyendayenda ndi tizilombo, mphepo yamkuntho ndi matenda obwera ndi mphepo
agriculture
agriculture document
en2463
Nematodes should be controlled by using recommended pesticides such as Basamid or by burning
mukhonza kugonjetsa ma nematides pothira mankhwala monga basmid kapena powotcha mbewu zokhudzidwa
agriculture
agriculture document
en2464
On the14th day, apply the chemical using the above rate and thoroughly mix with soil to a depth of 20cm
pakatha masabata awiri (patsiku la 14), thirani mankhwala pogwiritsa ncthito ndondomeko zomwe zili mmwambamp ndikutsakaniza ndi dothi kwa 20cm
agriculture
agriculture document
en2465
On the 21st day plastic should be aerated in order to release some toxic gases that may injure the seed.
pakatha masabata atatu (patsiku la 21), boolani chipepala cha pulasitiki kuti mpweya woyipa otuluke womwe ungathe kuonnga mbewu
agriculture
agriculture document
en2466
Basamid does not leave any harmful residues after breaking down making it an ozone friendly chemical.
basamid samasiya zotsalila zoopsa zomwe akamaliza kusungunuka zomwe zimapangisa kuti asaownongwe chilengedwe
agriculture
agriculture document
en2467
Water is applied for 12 days before piling the stalks to activate soil organisms after which actual burning is done.
madzi athilidwe pakatha masiku khumi ndi awiri musawunjike mapesi kuti tizilombo ta mu nthaka tituluke pamene mukuotcha
agriculture
agriculture document
en2468
nematodes can be controlled by using the float tray system
mukhonza kupewa ma nematodes pobzala fodya mmathileyi oyandama mmadzi
agriculture
agriculture document
en2469
To maximize yield, tobacco should be water planted.
fodya ayenera kubzalidwa ndi madzi kuti zokolola zichuluke
agriculture
agriculture document
en2470
Farmers should follow a minimum rotation of 4 years to avoid build- up of pests and diseases, particularly nematodes.
alimi ayesele ulimi wakasinthasintha osachepera zaka zinayi kuti apewe kuchulukana kwa tizilombo ndi matenda makamaka nematode
agriculture
agriculture document
en2471
In areas where both tobacco and cotton are grown, great care is required to avoid insecticides used on cotton drifting onto tobacco
madera amene amalima fodya ndi thonje, akuyenela kusamala kwambiri kuti mankhwala othana ndi tizizlombo a thonje asafike mmunda wa fodya
agriculture
agriculture document
en2472
Pine bark is the common substrate used in float tray tobacco seedling production
khungwa la payini limagwiritsodwa ntchito pofesa mbewu ya fodya
agriculture
agriculture document
en2473
Farmers should aim at transplanting tobacco with the first planting rains so as to complete the operation before Christmas
alimi awokele nsamga fodya ndi mvula yoyambilila kuti ikamafika nyengo ya khisimisi azikhala atamlaiza kuwokela
agriculture
agriculture document
en2474
Where resources permit, famers should apply recommended pesticides
ngati pali zipangizo zokwanila, alimi athire mankhwala a tizolombo ovomelezeka
agriculture
agriculture document
en2475
It is therefore essential that tobacco should not be planted within 100m radius of any cotton crop
ndikofunika kuti munda wa fodya ukhale kutali ndi munda wa thonje kwa ma mita 100
agriculture
agriculture document
en2476
Always start with the clean lands or plants end up with diseased lands or plants.
kumayamba ndi nthaka yopanda matenda apo ayi mbewu zimagwidwa ndi matenda kapena kusiya matenda mu nthaka
agriculture
agriculture document
en2477
The disease also spreads by transplanting diseased seedlings into clean lands.
nthendayi imathanso kufala pamene tawokela mbewu zokhuzidwa pa malo abwinobwino
agriculture
agriculture document
en2478
Development of the diseases and severity of damage is enhanced by high soil moisture and high soil temperature
kukula kwa matenda komanso kaonongedwe kake kumadza chifukwa cha kuchuluka kwa chinyontho mu nthaka
agriculture
agriculture document
en2479
types of symptoms may occur if attacked by more virulent strains of the virus.
mitundu ya zizindikilo imaoneka ngati yakhudzidwa ndi tizilombo toopsa kwambiri
agriculture
agriculture document
en2480
Affected plants are stunted
mbewu zokhudziwa zimakula mopinimbila
agriculture
agriculture document
en2481
can lead to leaf degradation and loss of yield and quality
zikhodza kulowesa kawonekedwe kabwino ka masamba komanso kuchepetsa zokolola
agriculture
agriculture document
en2482
Control is by use of certified and disease free seed
pewani pogwiritsa ntchito mbewu zovomelezeka komanso zopanda matenda
agriculture
agriculture document
en2483
Harvesting or reaping, curing, bulking and preliminary pre-sale (farm) grading constitute some of the important aspects of post-harvest technology of tobacco.
kukolola, kuchiza, kulongeza ndi kasankha malingana ndi kaonekedwe ndi njira zofunika kutsatila posamalira fodya akakololedwa
agriculture
agriculture document
en2484
From the barn leaf is transferred to storage sheds.
kuchokela mma balani pititsani masamba mosungilamo
agriculture
agriculture document
en2485
The walls should be plastered and white washed.
khoma lizilidwe ndi kutsukidwa bwino
agriculture
agriculture document
en2486
Grouping is the arrangement of tobacco bales in such an order that bales of similar quality are sold together in runs of declining order of value.
magulu (grouping) ndi ndondomeko yoika fodya mmabelo mu ndondomeko yokuti mabelo owonek abwino amagulitsidwa pa mtengo waukulu kenako kumatsika malingana ndi mawonekedwe
agriculture
agriculture document
en2487
In the event that the disease appears in the lands, topping high and reaping earlier than normal may help to salvage the crop.
pamene nthendayi yatulukila msanga mudera, kubzala mwachangu ndi kukolola mwachangu kusiyana ndi nthawi zonse kumathandiza
agriculture
agriculture document
en2488
Symptoms of attack are stunting and yellowing of leaves
kupinimbila ndi kufiila kwa masamba ndi zizindikilo za kugwidwa ndi matenda
agriculture
agriculture document
en2489
The disease affects tobacco at any stage of growth in the seedbeds and can also develop on newly transplanted tobacco.
nthendayi imagwira fodya pa msinkhu uliwonse mukafesa ngakhaleso pamene mwangowokela kumene
agriculture
agriculture document
en2490
Sprays recommended for tobacco aphids and budworms will also control the aforementioned pests.
mankhwala amene mukhonza kthira ku fodya kuti muthane ndi nsabwe za mmasamba ndi mphutsi za mmaluwa mukhonzaso kuthira pothana ndi tizilombo tachulidwa mmwambamo
agriculture
agriculture document
en2491
Termites can be observed both in nurseries and in the lands, especially where there is lack of decomposed organic material during hot and dry weather.
chiswe chimawoneka kwambiri pa nazale kapena mmunda ngati manyowa sanawole bwino munyengo yotentha
agriculture
agriculture document
en2492
Control is by early ploughing to allow complete decomposition of the plant residues.
Kuthana nacho ndi kulima mwachangu kuti zinyalala za mbewu ziwole mokwanira
agriculture
agriculture document
en2493
Cutworms are active at night.
ma cutworm amachangamuka usiku
agriculture
agriculture document
en2494
The insect will curl up into a small thick lot when disturbed
Kachilomboka kamadzikulunga nkukhala kakang'ono kokhuthala kakasokonezedwa
agriculture
agriculture document
en2495
The tobacco aphid also known as the green peach aphid is the most severe insect pest of tobacco in Malawi
nsabwe za mmasamba a fodya zomwenso zimatchedwa nsabwe za mmasamba za mupichesi ndi tizilombo timene timawononga kwambiri fodya mmalawi muno
agriculture
agriculture document
en2496
Control is by hand picking under light infestations and chemical sprays of Steward 150 EC, Aryna 46EC, Belt Expert 480 SC etc
mutha kuthana nazo potola ndi manaj ngati zilipo zochepa ndi kuthira mankhwala monga Steward 150 EC, Aryna 46EC, Belt Expert 480 SC ndi ena ambiri
agriculture
agriculture document
en2497
As these leaves increase in size, the feeding holes increase proportionally, giving the leaves a raged distorted appearance.
pamene masamba akukula, mabowo odyera makulanso chimodzimodzi, kupangitsa kuti masamba akhale ndi kaonekedwe kodabwitsa
agriculture
agriculture document
en2498
Symptoms of ant damage are their observed presence in large numbers on the seedbeds and reduced seed germination because they carry the tiny newly sown seed off the seedbed.
zizindikilo za kuononga kwa chiswe kumaoneka ndikachulukidwe ka ka chiswe pa mabedi a mbewu komanso kuchewa kwa zomela kamba kakuti zimadya mbewu zikangomel
agriculture
agriculture document
en2499
In the Northern region, nursery destruction should be done before 1st January of each year
mchigawo chakumpoto, nazale limayenera liwonongedwe pa 1 January pasanafike chaka chilichonse
agriculture
agriculture document
en2500
Chemical control of aphids must be preventive, both in the seedbeds and in the lands.
mankhwala othana ndi nsabwe za m'masamba athitiridwe ngati kupewa nsabwezi mmalo obzala mbewu komanso minda
agriculture
agriculture document
en2501
In the Northern region, stalk uprooting should have been completed by 30th May each year.
Kuchigawo chakumpoto, kuzula mapesi kuyenera kumalizidwa pasanafike pa 30 May chaka chilichonse.
agriculture
agriculture document