sent_id
stringlengths
3
7
english
stringlengths
3
1.06k
chichewa
stringlengths
4
3.03k
topic
stringclasses
8 values
source
stringclasses
17 values
en2202
intercropping hinders some of the pest to locate the host crop in the system but also restrict the movement of pests and diseases from one crop to the other
kulima mbewu zosiyana mophatikiza kumathandiza kuti tizilombo tisagwire mbewu yofunika kwambiri pa ulimiwo komanso kumachepetsa kayendedwe ka tizilombo kupita ku mbewu zina
agriculture
agriculture document
en2203
For example, the fertilizer applied to maize will not be taken up by the pigeon pea crop in the farming system because it responds little to fertilizers
mwa chitsanzo, nandolo sagwiritsa ntchito fetereza amene wathilidwa ku chimanga chifukwa sagwiritsa ntchito
agriculture
agriculture document
en2204
Cowpea is aggressive when planted at the same time with maize
nandolo (cowpea) ndiwaukali akadzalidwa nthawi imodzi ndi chimanga
agriculture
agriculture document
en2205
Beating the plants should be gentle to avoid destroying the embryo which eventually may affect germination and overall seed quality.
punthani mosamala mbeu zanu kuti musawononge mtima wa mbeu kuti sizakhudze kameledwe ka mbeu
agriculture
agriculture document
en2206
Planting should be done with the first planting rains or soon after the main crop has emerged where inter-planting is practiced.
bzalani ndi mvula yoyamba kapena mbeu yodalilika ikangomela pamene mukupanga ulimi wakasakaniza
agriculture
agriculture document
en2207
Short duration pigeon peas are best produced as sole crop.
nandolo osachedwa kukhwima asankhwidwa ngati mbewu yoima payokha
agriculture
agriculture document
en2208
Aflatoxin management in Legumes and maize
kasamalidwe ka mbewu za nyemba nd chimanga ku chuku
agriculture
agriculture document
en2209
Aflatoxins are a major challenge in legumes and maize
chuku ndi vuto lalikulu kwmabiri pa mbewu za nyemba ndi chimanga
agriculture
agriculture document
en2210
Practice fermentation which reduces aflatoxins levels in food because lactic acid bacteria binds aflatoxin
yeserani kukundika komwe kumachepetsa kufala kwa chuku mu zakudya chifukwa cha tizilombo (lactic acid bacteria) timene ndimamata chuku
agriculture
agriculture document
en2211
The choice of vegetables to be planted in the homestead should be those that are nutrient dense.
mitundu ya masamba yomwe mukufuna kubzala pakhomo ikhale yoepeka michere ya nthupi yochuluka
agriculture
agriculture document
en2212
Vegetables have high nutritional value in terms of micronutrients and fibre and they also make meals more appealing in flavour, texture and colour.
zakudya zamasamba zimakhala zopasa thanzi chifukwa cha michere imene imakhala nayo komanso zimakhala zopasa mudyo nkaonekedwa ndi kakomedwe komwe
agriculture
agriculture document
en2213
Fruits do not require major preparation for somebody to eat.
zipatso zizitenga nthawi yambiri kuti zikonzedwa pokudya
agriculture
agriculture document
en2214
The choice of fruits to be planted in the homestead depends on the space available.
kusankha mitengo ya zipatso pakhomo zimatengela ndi mmene malo alili pakhomopo
agriculture
agriculture document
en2215
Where possible fish can be reared around the homestead where there are water sources
ngati kuli kotheka nsomba zikhonza kuwetedwa pakhomo ngati pali magwero a madzi
agriculture
agriculture document
en2216
Poultry production should be incorporated into small farming systems such as homestead farming.
ulimi wa ziweto za mbalame ukuyenera kuphatikizidwa mu mitundu ya ulimi waung'ono monga ulimi wapakhomo
agriculture
agriculture document
en2217
Gross margin refers to the remaining income from an enterprise after the variable costs are deducted
kupindula phindu kumathanthauza kuti ndalama yomwe yatsala mukagulitsa katund wanu komanso mukachotsela zimene munalowetsa
agriculture
agriculture document
en2218
The gross margin budget includes all costs involved in producing the enterprise.
ndondomeko yopindulira phindu timaphatikiza ndalama zonse zomwe zinalowetsedwa pa ulimi wa zokolola zathu
agriculture
agriculture document
en2219
It helps farmers to compare the performance of a single enterprise using different farming practices and technologies
zimathandiza alimi kusiyanisa mmene mbewu yachitila bwino pogwiritsa mtchito zipangizo ndi ukadaulo osiyanasiya
agriculture
agriculture document
en2220
Helps to find out what products people want and reasons for their preferences
zimathandiza kudziwa zinthu zimene anthu akuzifuna ndi zifukwa zimene akuzifunila
agriculture
agriculture document
en2221
Farmers should then decide whether to go on with their farm plan of producing for the possible identified buyers.
alimi akuyenera kuanga chiganizo chopitiliza ndi pulani yawo yolima mbewu zimene apeza kale misika yake
agriculture
agriculture document
en2222
Limited access to markets by vulnerable gender categories especially when the markets are located far away from the village
kufikila kochepa ku miskika kwa magulu ophinjika pakati a amayi ndi abamabo makamaka ngati misika ili kutalai ndi mudzi
agriculture
agriculture document
en2223
Diversion of income meant for agriculture production to provision of from to care, treatment and support for sick family members.
kugawa kwa ndalama zokhudza ulimi kupititsa ku gawo la chisamaliro, chithandizo ku matenda ndikuthandizila odwala m'banja
agriculture
agriculture document
en2224
Improving access to agricultural input and market information amongst farmers
kutukula kapezedwe ka zipangizo za ulimi ndi ma uthenga a misika pakati pa alimi
agriculture
agriculture document
en2225
Promotion of production of high value crops/livestock amongst women
kutukula ulimi wa mbewu zopindulitsa kapena ziweto pakati pa amayi
agriculture
agriculture document
en2226
It causes yellowing between the veins of cowpea leaves, resulting in the death of infested plants.
zimayambitsa chikasu pakati pa misempha ya masamba a nandolo, zomwe zimapangitsa kufa kwa mbewu zomwe zakhudzidwa
agriculture
agriculture document
en2227
The seeds of these parasites can survive in soil for many years (more than 20 years) until a susceptible variety is planted
mbewu ya tizilomboti imatha kukhala mu nthaka kwa zaka zochuluka osafa (kupitilila zaka 20) pokhapokha padzalidwe mbewu yomwe ikhonza kutengela
agriculture
agriculture document
en2228
Cultural control measures that are affordable to farmers include cowpea–cereal rotation and the use of resistant cowpea varieties
njira za chikhalidwe zomwe alimi amatsatila ndi kulima kwa kasinthasintha kw ambewu monga nandolo ndi chimanga ndi kugwiritsa ntchito mitundu ya nandolo yopilira
agriculture
agriculture document
en2229
Ensure good hygiene in the store and check every 2 weeks for any change in storage conditions
onetsetsani ukhondo wabwino mosungila mbewu ndi kumayang'anamo pamasabata awiri aliwonse ngati pali kusintha kwa zinthu mosungilamo
agriculture
agriculture document
en2230
This is one of the serious pests on maize causing considerable damage in high altitude areas and to the late planted crop
aka ndi kachilombo kovuta kwambiri kamene kamakhudza chimanga koyambitsa kuwonongeka mmadera okwera ndi madera obzala mochedwa
agriculture
agriculture document
en2231
The larvae infest the leaves, rolling them longitudinally together and live inside the rolled leaf.
kachilomboka kamadya masamba ndi kuzungulidza pamodzi iko ndikumakhala mkati mwa tsambo lozungulilalo
agriculture
agriculture document
en2232
The insect is also called African boll worm or tobacco bud worm depending on the crop attacked.
kachilomboka kamatchedwa african boll worm kapena tobacco bud worm malingana ndi mbewu imene yakhudzidwa
agriculture
agriculture document
en2233
Clean and sort 8 parts of maize grains, 1 part of ground nuts and 1 part of pulses (cowpeas or pigeon peas or beans or ground beans)
konzani ndi kusakha magawo 8 a chimanga, gawo limodzi la mtedza ndi gawo limodzi la zanyemba (nandolo kapen nyemba)
agriculture
agriculture document
en2234
Mill with maize or mill the beans alone if the quantity is reasonable enough to go through the grinding mill to make flour
gaitsani ndi chimanga kapena gaitsani nyemba zokha ngati zilipo zochuluka bwino zokuti zikhonza kugaitsidwa nkupanga ufa
agriculture
agriculture document
en2235
small livestock raising
ulimi wa ziweto zing'onozing'ono
agriculture
agriculture document
en2236
promotion of improved preservation and storage of fruits and vegetables to reduce waste, post-harvest losses and effects of seasonality
kutukula kasungidwe kamakono ndi kasungidwe ka zipatso ndi zamasamba kuti tichepetse kuwononga zakudya, zotayika pa nthawi yokolola ndi zosatsila za zanyengo
agriculture
agriculture document
en2237
promotion of underexploited traditional foods and home gardens
kutukula zakudya zachikhalidwe zosagwiritsidwa ntchito bwino ndi minda yapakhomo
agriculture
agriculture document
en2238
It is therefore important to ensure that a variety of foods are sustainably available and accessible in adequate amounts and quality; and properly utilised.
chomwecho, ndikofunika kuwonetsetsa kuti zakudya zamagulu osiyanasiyana zikupezeka nthawi zonse ndi kwa anthu onse pa mlingo okwanila komanso zikugwiritsidwa ntchito moyenerera
agriculture
agriculture document
en2239
Promoting Income Generating Projects for vulnerable gender groups
Kupititsa patsogolo ntchito zobweretsa ndalama kumagulu ophinjika
agriculture
agriculture document
en2240
Always ensure that extension meetings are organized during times when women and other vulnerable categories can be able to participate
onetsetsani kuti mkumano wa zaulangizi ukukhazikitsidwa nthawi imene amayi komanso magulu ena ophinjika akhonza kukwanitsa kutenga nawo mbali
agriculture
agriculture document
en2241
Soil fertility improvement and fodder
kutukula nthaka ndi zakudya za ziweto
agriculture
agriculture document
en2242
Maize grain for storage should be well treated with storage pesticides such as Actellic upon recommendations on safe use and correct application rates.
chimanga chosungidwa chikuyenera kuthiridwa mankhwala oyenera monga actelic malingana ndi ndondomeko za kathilidwe koyenerera ngakhalenso mlingo oyenerera
agriculture
agriculture document
en2243
Ensuring that all crop residuals are fully decomposed before planting
kuonetsetsa kuti zosalila mmunda zonse zaololena bwino musanadzale
agriculture
agriculture document
en2244
Observing good crop husbandry practices such as early land preparation, early planting, burying all diseased plants and others
kuonetsetsa kuti ndondomeko zoyenera kuchita pa ulimi zikutsatilidwa monga, kusosa mwachnagu, kubzala msanga, kukwilira mbewu zonse zamatenda ndi zina zambiri
agriculture
agriculture document
en2245
Groundnuts and soybean are planted in rows spaced at 37.5 cm and 10-15cm and 5cm apart between plant stations.
mtedza ndi soya zimadzalidwa mmizere yotalikilana 37.5cm ndi10 mpaka 5cm komanso 5cm pa phando ndi phando
agriculture
agriculture document
en2246
cannot run a big risk, especially not when the technology is not known
sizingatheke kukhala pa chiopsezo kwambiri, makamaka ngati tekinolojeyo siyikudziwika bwino
agriculture
agriculture document
en2247
need a learning-by-doing environment
pakufunika malo ophunzilira mwakuchita
agriculture
agriculture document
en2248
A diet is the total foods and drink eaten by an individual or a group of people at a given time.
chakudya choyenera kudya ndi zakudya zonse ndi zakumwa zimene munthu amadya kapena magulu a anthu pa nthawi yoikika
agriculture
agriculture document
en2249
Food and nutrition helps in the prevention of malnutrition
chakudya cha thanzi chimathandizira kupewa kuperewera kwa zakudya mthupi
agriculture
agriculture document
en2250
Enables easy transportation of food materials
zimathandizila kayendedwe ka zakudya mthupi
agriculture
agriculture document
en2251
It Increases seasonal availability of many foods.
zimachulutsa kupezeka kwa zakudya zambiri mu nyengo zosankhika
agriculture
agriculture document
en2252
most foods are seasonal so processing them into other products makes them available all year round.
zakudya zambiri zimatengela nyengo kotelo kuzikonza mu mtundu wina kumapangitsa kuti zikhale zopezekelatu mu chaka chonse
agriculture
agriculture document
en2253
Methods of food processing
njira zokonzela chakudya
agriculture
agriculture document
en2254
Biological methods
njira za chilengedwe
agriculture
agriculture document
en2255
Water conservation is ensuring there is increased infiltration of water in the soil so as to reduce erosion caused by runoff
kasungidwe ka madzi ndi kuonetsetsa kuti madzi akulowa kwambiri pansi pa nthaka zomwe zimachepetsa kukokoloka kwa nthaka ndi madzi
agriculture
agriculture document
en2256
Processed products are easy to transport and lessen the cost of transportation
zakudya zopangidwa sizimavuta kunyamula ndipo zimachepetsa ndalama yonyamulila katundu
agriculture
agriculture document
en2257
Reduces siltation and flooding
zimacheetsa kusefukila kwa madzi
agriculture
agriculture document
en2258
Soil and water conservation entails a number of technologies.
pali ukadaulo wochuluka okhudza kasamalidwe ka nthaka ndi madzi
agriculture
agriculture document
en2259
Reduces water runoff and soil erosion
zimachepetsa kukokoloka kwa nthaka
agriculture
agriculture document
en2260
Benefits of Soil and Water Conservation
ubwino wosamala nthaka ndi madzi
agriculture
agriculture document
en2261
Conserves soil moisture for plant growth and development
zimasunga chinyezi nthaka kuti mbewu zizikula bwino
agriculture
agriculture document
en2262
Not understanding the technology
kusamvetsetse kwa ukadaulo
agriculture
agriculture document
en2263
Soils or crops are not adequate and need to be adjusted
nthaka ndi mbewu sizokwanira ndipo ziyenera kusinthidwa
agriculture
agriculture document
en2264
need a learning-by-doing environment
pamafunika malo ophunzira mwakuchita
agriculture
agriculture document
en2265
do not have the capital to invest
alibe mpamba oyambila
agriculture
agriculture document
en2266
Steps to follow when establishing a conservation agriculture demo plot
ndondomeko zoyenmera kutsatila pokhazikitsa puloti yachiwonetselo ya ulimi wosunga nthaka
agriculture
agriculture document
en2267
After the demarcation, start preparing the plots as per the agreed design layout
mukamaliza kupanga malire, yambani kukonzekela malngana ndi dongosolo lomwe mwangwirizana
agriculture
agriculture document
en2268
Soil and water conservation.
kasungidwe/kasamalidwe ka nthaka ndi madzi
agriculture
agriculture document
en2269
Soil Conservation is the protection, maintenance, rehabilitation, restoration and enhancement of soil resources and includes the management and use of soil resources to ensure the sustainability of such use
kusamala nthaka ndiko kuteteza, kusamala, kuchiritsa, kubwenzeretsa ndi kutukula nthaka, iziz zimaphatikiza lasamalidwe ndi kagwiritsidwe ntchito ka nthaka kuti ikhale ikugwirabe nthcito kwa nthawi yaitali
agriculture
agriculture document
en2270
Improves crop and pasture fields;
zimatukula minmda komanso malo odyetsela ziweto
agriculture
agriculture document
en2271
In order to control runoff and soil loss, ridges should be cultivated along the contour
kuti muthane ndi kukukoloka kwa madzi ndi nthaka, bzalani mizere molekani ndi mtunda
agriculture
agriculture document
en2272
Legumes are Very important in the diet as they supplement cereals, roots and tubers by providing plant protein
mbewu za nyemba ndizofunikila mu zakudya chifukwa zimathandizila mbewu za chimanga, za mitsitsi ndi zobala pansi popereka mapulotini ku mbewuzo
agriculture
agriculture document
en2273
Legume Processing
kakonzedwe ka mbewu za nyemba
agriculture
agriculture document
en2274
Pre-treated legume flour
ufa okonzedweratu wa magulu a nyemba
agriculture
agriculture document
en2275
Farmer Field School is a group training approach that focusses on adult non formal education through hands on field discovery learning.
maphunziro a alimi apamunda ndi uphunzitsi wapagulu umene umayang'na kwambiri za maphunziro a akuluakalu ndi kuchita bwino pamunda
agriculture
agriculture document
en2276
The approach is a school without walls for improving decision making capacity of farmers and stimulating innovativeness for agricultural sustainability and can be done on both crops and livestock
njirayi ndi sukulu yopanda malire imene imathandiza alimi kupanga ziganizo zabwino komanos kulimbikitsa ukadaulo watsopano wotukula ulimi wa zakumunda ndi ziweto
agriculture
agriculture document
en2277
Improve adoption of knowledge intensive technologies and practices
zimatukula kutengela kwa nzeru za matekinoloje woonjeza ndi kuchita
agriculture
agriculture document
en2278
The approach focusses on learning of experienced farmers usually in the same locality or village who learn with hands on especially when the subject matter is related to their experiences
njirayi imayang'ana kwmabiri alimi amene anakumanapo nazo mu dera kapena mudzi omwewo komanso amachita nzinthunzo ndi alimi amene akukhudzidwa kwenikweni ndi nkhani yokambidwayo
agriculture
agriculture document
en2279
Capacity building and farmer empowerment
sukulu ya bizinesi ya alimi
agriculture
agriculture document
en2280
Promotes lead farmer concept which enhances farmer to farmer extension
zimalimbikitsa ndondomeko ya alimi wotsogolela alimi anzawo yomwe imalimbikitsa ulangizi wa pakati pa alimi
agriculture
agriculture document
en2281
Enhance Farmer Led Research
kulimbikitsa kafukufuku otsogozedwa ndi alimi
agriculture
agriculture document
en2282
Promote collective problem identification, analysis and solving
limbikitsani kuzindikiritsa mavuto onse, kusanthuka ndi kuthesa
agriculture
agriculture document
en2283
Principles of Farmer Field Schools
mfundo za sukulu ya mlimi
agriculture
agriculture document
en2284
Based on agro-enterprise cycle and time specific because you have to start with a crop at planting up to harvesting
kutengela ndi mabizinesi ozungulila a zaulimi ndi nthawi yoikika chifukwa mukuyenra kuyamab ndi kubzala mbewu mpakana kukolola
agriculture
agriculture document
en2285
Identify and select most promising farm enterprises to increase profitability and farm income.
dziwani ndikusankha ma bizinesi omwe akupereka chiyambekezo kuti muonjezere phindu komanso ndalama zaulimi
agriculture
agriculture document
en2286
Farmer Business School
sukulu ya bizinesi ya alimi
agriculture
agriculture document
en2287
Plan and cost the production process
konzani ndi kuwerengetsa ndamala zomwe zikufunika pa ntchito ya ulimi
agriculture
agriculture document
en2288
Acquire the fundamentals of how to grow crops and raise livestock in a business manner
pezani zofunika za momwe mungakulire mbewu ndi kuweta ziweto mwa bizinesi
agriculture
agriculture document
en2289
Make a plan for marketing of their farm produce
kukonzelatu mmene angagulitsile zakumunda
agriculture
agriculture document
en2290
Find out what the market wants and produce what the market wants.
dziwani zomwe zikufunika pa ndikupanga zimene msika ukufuna
agriculture
agriculture document
en2291
It involves awareness creation among local or community leaders, farmers and farmer organizations on farmer business school through a meeting
zimafunikila mauthenga a chidziwitso pakati pa adindo a mmudzi, alimi ndi magulu a alimi a sukulu ya ulimi wa buzinesi
agriculture
agriculture document
en2292
Sensitization of Local Leaders and Farmer Organizations
kulimbikitsa atsogoleri a m'mudzi koamnso ma bungwe azaulimi
agriculture
agriculture document
en2293
Interested and supporting farmers are mobilized.
alimi onse amane ali ndi chidwi komanso amaitanidwa mapodzi
agriculture
agriculture document
en2294
They should be active and practicing farmers, willing to participate regularly, farmers with a common interest, farmers from the same locality and are willing to share experiences
akuyenera akhale alimi olimbikila ndi kuchita zimene aphunzira, wololera kutenga nawo gawo nthawi zonse, alimi amene ali ndi chidwi chimodzi, alimi a dera limodzi komanso wololera kugawira anzawo zimene akudziwa
agriculture
agriculture document
en2295
Benefits to Integrated Homestead Farming
kufumikila kwa ulimi wophatikiza wa pakhomo
agriculture
agriculture document
en2296
It promotes sustainable utilization of resources at household level.
zimalimbikitsa kagwiritsidwe ntchito zipangizo kokhazikika pakhomo
agriculture
agriculture document
en2297
It increases utilization of vegetables, fruits and animal sources at household level.
zimalimbikitsa kagwiritsidwe ntchito ka zakudya za masamba, zipatso ndi zanyama
agriculture
agriculture document
en2298
It increases household income.
zimachulikitsa malipiro a pakhomo
agriculture
agriculture document
en2299
It increases consumption of nutrient rich plant and animal foods.
zimachulukitsa kadyedwe ka zakudya za thanzi
agriculture
agriculture document
en2300
Components of Integrated Homestead Farming
Zigawo za Ulimi Wophatikiza Pakhomo 
agriculture
agriculture document
en2301
The nutrients play various important roles in the body.
Zakudyazi zimagwira ntchito zosiyanasiyana thupi.
agriculture
agriculture document