sent_id
stringlengths
3
7
english
stringlengths
3
1.06k
chichewa
stringlengths
4
3.03k
topic
stringclasses
8 values
source
stringclasses
17 values
en2001
If stored in bags, stack them on wooden planks or poles to avoid damage from dampness from the wall and the floor.
ngati wasungidwa mmasaka/matumba, sanjani matumba anu mamwamba pa matabwa kapena mitengo kuopesa kuonongeka ndi chinyezi cha mmakoma komanso pansi
agriculture
agriculture document
en2002
Groundnuts are usually shelled prior to sowing or selling, with the majority of farmers shelling by hand.
mtedza umaswedwa pa nthawi imene ukufuna kubzalidwa kapena kugulitsidwa, ndipo alimi ambiri amaswa ndi manja
agriculture
agriculture document
en2003
Termites can also attack soybean plants at any stage of development from the seed to the mature soybean plant particularly when there is prolonged dry spells
Chiswe chimaononga mbewu ya soya pemene yayamba kukula kumene mpakana itayamba kukhwima
agriculture
agriculture document
en2004
Legumes are very important crops that contribute to improving household food security, nutrition, and soil health and soil fertility.
mbewu za magulu anyemba ndizofunika kwambiri popeza zimathandizila kupezeka kwa chakudya pakhomo, nthazi komanso kuonjezela chonde nthaka
agriculture
agriculture document
en2005
Soils that easily compact and form a crust must be avoided for growing soybean
pewani kubzala mbewu ya soya pa nthaka imene siimachedwa kugwirana pamodzi
agriculture
agriculture document
en2006
A farm business plan is a plan that records the most important decisions and actions affecting the operation of the farm business.
pulani ya bizinesi ya kumunda ndi pulani yomwe imasunga zinthu zofunika kwambiri ndi zochitika zomwe zimakhudza ulimi wa biziznesi
agriculture
agriculture document
en2007
Market research helps farmers to produce what they can sell rather than produce then hunt for a buyer.
kuchita kafukufuku wa msika kumathandiza alimi kuti alime zinthu zimene akhonza kugulitsa osati kulima zinthu zimene azilephere kupeza msika ogulitsila
agriculture
agriculture document
en2008
There are two types of farm records namely: Physical records and financial records.
pali mitundu iwiri ya ma rekodi: ya pa manja komanso ya za chuma
agriculture
agriculture document
en2009
Plant 2 seeds per station spaced at 60 cm on ridges of either 75 or 90 cm apart.
bzalani mbewu ziwiri pa phando motalika 60cm pa mizere yotalikana 75 mpaka 90 cm
agriculture
agriculture document
en2010
Avoiding planting seeds obtained from mosaic-affected plants
pewani kubzala mbewu zomwe zinagwidwapo ndi nthenda ya mosaic
agriculture
agriculture document
en2011
Piling soybean plants on tarpaulin or putting dry soybean pods in sacks and beating them with a stick.
kusanzula soya pa tarpaulin kapen akumuika mmatumba ndikumaputha ndi chimtengo
agriculture
agriculture document
en2012
Avoid poor sandy soils with low content of organic matter.
pewani dothi la mchenga lomwe lili ndi manyowa achilenge ochepa
agriculture
agriculture document
en2013
Maggots can be controlled by adjusting time of planting
mutha kuthana ndi mbozi posintha nthawi yobzalila
agriculture
agriculture document
en2014
Aphids can be controlled by spraying Dimethoate(WP or EC)
popelani dimethoate( WP akpena EC) kuti muthane ndi nsabwe
agriculture
agriculture document
en2015
Plant dwarf varieties in rows 45 cm apart
mizere ya mbewu yaifupi isiyane 45cm
agriculture
agriculture document
en2016
Post emergence herbicides are applied after weeds and the crop have emerged and the target specific weed type
mankhwala a udzu amathiridwa udzi ndi mbewu zikamela ndi pa mtundu wa udzu oyenera kuthilidwawo
agriculture
agriculture document
en2017
Weeding can be done manually or using herbicides
mukhonza kupalira udzu kapena kuthila kuthira mankhwala
agriculture
agriculture document
en2018
Dig groundnuts and dry using Mandela cock system
kumbani ndi kuyanika mtedza pogwiritsa ntchito njira ya mandela cock
agriculture
agriculture document
en2019
Apply phosphorus using 2×50 kg bags of 23:21:0 +4S compound fertilizer available in Malawi.
thirani phosphorus pothira matumba awiri a 5okg a fetereza wa 23:21:0+4s opezeka M'malawi
agriculture
agriculture document
en2020
The field should be weed free especially in the initial stages of establishment.
munda ukuyenera ukhale opanda udzi makamaka nthawi yobzala
agriculture
agriculture document
en2021
Without exception, all early maturing pigeon pea varieties have to be sprayed twice between 50% and full flowering and twice between 50% and full pod to control insect pests
mukachotsa mtedza wanu ukuyenera kukhala kuti wauma bwino musanausunge
agriculture
agriculture document
en2022
The young leaves and immature pods are eaten as vegetables.
masamba aang'ono ndi mbewu zosakhwima zimadyedwa ngati ndiwo zamasamba
agriculture
agriculture document
en2023
It is tolerant of drought and well adapted to sandy and poor soils
ndiyopilira ku chilala ndi kuchita bwino pa dothi la mchenga khangaleso dothi lopanda chonde
agriculture
agriculture document
en2024
Proper site selection is very important
kazankhidwe ka malo abwino ndikofunikila
agriculture
agriculture document
en2025
Plant one seed in rows/ridges per stations spaced at 25cm apart
bzalani bzalani mbewu imodziimodzi pa mzere uliwonse ndipo mapando atalikilane kwa 25cm
agriculture
agriculture document
en2026
2 bags of NPK (23:21:0+4S) are sufficient for one hectare
matumba awiri a fetereza wa NPK (23:21:0+4S) ndiwokwanila pa hekitala
agriculture
agriculture document
en2027
The rows /ridges should be spaced at 75 cm apart
mizere ikuyenera kutalikilana kwa 75cm
agriculture
agriculture document
en2028
Top dress with UREA fertilizer after 3 to 4 weeks from basal dressing fertilizer application
thirani fetereza wa UREA pakangotha masabata atatu kapena anayi mutangothila fetereza obzalila
agriculture
agriculture document
en2029
Keep the maize field as free from weeds as possible
onetsetsani kuti munda wa chimanga ulibe udzu
agriculture
agriculture document
en2030
Weeding can be done manually or using herbicides
mutha kupalila pamanja kapena kugwiritsa ntchito mankhwala
agriculture
agriculture document
en2031
Application rates and modalities are indicated on the label for the mentioned type of herbicide
kathiridwe kamankhwala ndi zina zoyenera kutsatila zimalembedwa pachipepala cha mankwalawo
agriculture
agriculture document
en2032
Crop rotation can also be used to control some weeds such as witch weed
kulima kwa kasinthasintha kumathandiza kuchepetsa udzu monga kaufiti
agriculture
agriculture document
en2033
Late planted crops are mostly attacked
mbewu zomwe zabzalidwa mochedwa ndizomwe zimakhudzidwa kwambiri
agriculture
agriculture document
en2034
Hand picking is most practical and should be encouraged
kutola ndikothandiza kwmabiri ndipo kuzilimbikitsidwa
agriculture
agriculture document
en2035
The insect pest can also be controlled by spraying with Endosulfan35 EC and pyrethroids
mutha kuthana ndi tizilomboti pothira mankhwala a Endosulfan35 EC ndi pyrethroids
agriculture
agriculture document
en2036
It also occurs in high altitude when maize is planted late
zimachitika malo okwera chimanga chikadzalidwa mochedwa
agriculture
agriculture document
en2037
The maize planted during off season in dimbas using residual moisture acts as a reservoir of both leafhoppers and the virus
chimanga chimene chimadzalidwa nthawi yopanda mvula mmadimba chimakhala chipangizo chosungilamo mazila a zitete komanso tizilombo (virus)
agriculture
agriculture document
en2038
Dissemination is mostly by wind borne spores (wind dispersed)
kufalitsa kumachitika kwambiri ndi ma spores ofala ndi mphepo (ofalitsidwa ndi mphepo)
agriculture
agriculture document
en2039
Ensuring that all crop residuals are fully decomposed before planting
kuonetsetsa kuti zosalila mmunda zonse zaololena bwino musanadzale
agriculture
agriculture document
en2040
Harvesting and storage in maize
kakololedwe ndi kasungidwe ka chimanga
agriculture
agriculture document
en2041
Legumes are very important crops that contribute to improving household food security, nutrition, and soil health and soil fertility.
mbewu za nyemba ndizofunika kwmabiri chifukwa zimathanditha kuonjezera chakudya chokwanira pakhomo, thanzi la anthu ndi nthaka ya bwino komanso yachonde
agriculture
agriculture document
en2042
Soil fertility improvement and fodder
kutukula chonde mnthaka komanso chakudya cha ziweto
agriculture
agriculture document
en2043
Groundnuts Production
ulimi wa mtedza
agriculture
agriculture document
en2044
Legumes are vital supplement to the largely maize-based diets and are readily available sources of vegetable protein, vitamins and vegetable oil.
mbewu za nyemba zimaonjezela kwambiri ku zakudya za chimanga komanso ndi nsanamilo wopezekelatu zamasama za mapuloteni, mavitamini ndi zasamamba zamafuta
agriculture
agriculture document
en2045
Legumes provide cash farmers thereby contributing to their livelihoods.
mbewu za nyemba zimabweretsa ndalama kwa alimi kotelo kutukula miyoyo yawo
agriculture
agriculture document
en2046
Farmers should always use certified seed for higher yields.
alimi akuyenera kugwiritsa ntchito mbewu yovomelezeka kuti akolole zochuluka
agriculture
agriculture document
en2047
Plant with the first effective rains (approximately 25-30 mm).
bzalani ndi mvula yoyambilila ( ikagwa pafupifupi 25-30 mm)
agriculture
agriculture document
en2048
Cover the groove firmly to ensure rapid and uniform emergence
kwililani maenje kuti zimele mofulumila komanso mofanana
agriculture
agriculture document
en2049
There is need to treat groundnuts kernels with appropriate fungicides such as Thiram or Fernasan D.
ndikofunika kuwaza mankhwala monga Thiram kapena Fernasan D mungale za mtedza kuti zisawonongeke
agriculture
agriculture document
en2050
Weed control
kuthana ndi udzu
agriculture
agriculture document
en2051
Weed at least twice during this critical period is imperative, thus within 20 and 45 days after sowing.
kupalila kosachepera kawiri mu nyengo yovuta ndikofunika kwambiri, kotero chitani izi pakati ma pa masiku 20 mpaka 45 mukabzala
agriculture
agriculture document
en2052
the most important and widespread are: Rosette, Early and Late leaf spots and rusts
matenda amene amafala kwambiri ndi: khate, early ndi late leaf spot ndi dzimbiri
agriculture
agriculture document
en2053
It is common to find pods of different ages on the same plant at any one time the groundnut crop is scouted.
ndizosadabwisa kupeza mbewu zosiyana kakulidwe pa mtengo umodzi wa mtedza pamene mukuyendera mbewu
agriculture
agriculture document
en2054
Ground nuts should be timely harvested to avoid bleaching and discolouration of nuts, sprouting and pods remaining in the ground, and aflatoxin contamination.
mtedza ukuyenera kukololedwa mu nthawi yoyenera kuti mupewe kusuluka kwa mtundu, kumela komanso kusalila kwa makoko mu nthaka ndi kuyamba chuku
agriculture
agriculture document
en2055
The falling of leaves is not necessarily a sign of maturity
kugwa kwa masamba sikukutanthauza kukhwima kwa mbewu
agriculture
agriculture document
en2056
Dry pods produce rattling sound when shaken
makoko owuma amasokosela akakhuchumulidwa
agriculture
agriculture document
en2057
Ventilated stacking or Mandela Cock is a modern way of curing the nuts.
kuunjika pamodzi kapena kupanga mandela cock ndi njira imodzi yochilitsa/kuumitsa mtedza
agriculture
agriculture document
en2058
Remove groundnuts from the straws.
chotsani mtedza ku mitengo yake
agriculture
agriculture document
en2059
Store their groundnuts in pods and in well ventilated containers and structures to avoid mould development and aflatoxin contamination
kusunga mtedza wawo mu makoko ndi zosungilamo zopita bwino mpweya ndi nkhokwe kuopesa chinyezi komanso chuku
agriculture
agriculture document
en2060
Store under dry conditions.
sungani malo owuma bwino
agriculture
agriculture document
en2061
Ensure that the bags allow good circulation of air so as to maintain seed vigour and viability
onetsani kuti matumba akhale olowa bwino mpweya kuti mtedza usaonongeke
agriculture
agriculture document
en2062
Do not wet pods to prior to shelling as this may lead to development of moulds and aflatoxin
osanyowetsa mtedza pamene ukuswanyidwa kuopetsa nkhungu komanso ndi chuku
agriculture
agriculture document
en2063
All mouldy nuts should be discarded and not fed to livestock.
mtedza wa nkhungu utayidwe ndipo usadyetse ziweto
agriculture
agriculture document
en2064
Grade properly, taking out shriveled, rotten, mouldy and split nuts.
sankhani bwino, pochotsa mbewu zonyala, zowola, za nkhungu ndi zosweka
agriculture
agriculture document
en2065
If using a mechanical shellers sort your pods according sieve sizes.
ngati mukugwiritsa ntchito zipangizo zosolela, sankhani mbewu zanu malingana ndi mtundu wamasefa
agriculture
agriculture document
en2066
it is grown throughout the country mostly in cool plateau areas.
zimalimidwe mmadera mabiri dziko muno makamaka madera azitunda ozizila
agriculture
agriculture document
en2067
The bean yields are around 300 to 800kg per hectare.
nyemba zikakololedwa zimatha kufika 300 mpaka 800kg pa hekitala
agriculture
agriculture document
en2068
Land should be prepared by the end of November for the southern region and by the end of December for the central and Northern regions
maboma akumwera ayenera kusosa mwezi wa novembala usanathe pamene pakati ndi kumpoto ayenera kusosa mwezi wa desembala usanathe
agriculture
agriculture document
en2069
Recommended Cultural Practices in Bean Production
zoyenera kutsatila pa ulimi wa nyemba
agriculture
agriculture document
en2070
This requires a seed rate of 80 and 70 kgs per hectare
zimafunika mbewu zokwana 80 ndi 70kg pa hekitala
agriculture
agriculture document
en2071
This requires a seed rate of 75 to 90kgs per hectare
zimafunika mbewu zokwana 75 mpaka 90kg pa hekitala
agriculture
agriculture document
en2072
In relay cropping planting should be done during the months of February and March.
pa ulimi odalirana kubzala kudzikhala pakati pa mwezi wa february ndi march
agriculture
agriculture document
en2073
Beans should be planted from mid-December to mid-January in southern region and in the month of January in central and Northern regions.
nyemba zidzalidwe kuyambila pakati pa mwezi wa December mpaka pakati pa mwezi wa January madera a kumwera ndi mwe wa January madera a pakati ndi kumpoto
agriculture
agriculture document
en2074
Climbing beans should be planted on 1 row, 1 seed per station at 15cm apart.
bzalani nyemba zoyanga mzere umodzi, mbewu imodzi pa phando zitalikilane 15cm
agriculture
agriculture document
en2075
Dimba crop
mbewu zaku dimba
agriculture
agriculture document
en2076
Irrigated crop
mbewu zanthirila
agriculture
agriculture document
en2077
Fertilizer Application
kuthira fetereza
agriculture
agriculture document
en2078
Plant beans on flat as this assists in moisture conservation.
bzalani nyemba zanu pa malo olingana bwino pakuti izi zimathandiza kusunga chinyontho
agriculture
agriculture document
en2079
plant 1 seed per station spaced at 20cm
bzala mbewu imodzi pa phando pa 20cm
agriculture
agriculture document
en2080
Fertilizer is needed for root development.
fetereza ndi ofunikila kuti mizu ikule bwino
agriculture
agriculture document
en2081
Apply 18g per 2metres of ridge length using two and half cupful of cup number 8
thirani 18g pa 2 mita ya mzere pogwiritsa ntchito makapu awiri ozadza a kapu namba 8
agriculture
agriculture document
en2082
Hand weeding is applicable when weeds are observed during flowering
kudzula udzu ndi manja ndi kotheka pamene mbewu zayamba kutulutsa maluwa
agriculture
agriculture document
en2083
Avoid weeding during flowering to avoid flower shedding
pewani kupalira pamene mbewu zanu zayamba maluwa kuopesa kuthothoka kwa maluwa
agriculture
agriculture document
en2084
Practice a 3 year rotation with cereals
yeselani kasinthasintha ka mbewu za chimanga
agriculture
agriculture document
en2085
Bury crop residues
kwililani zotsalira za mbewu yanu (mapesi)
agriculture
agriculture document
en2086
Spray Daconil at same rate as with Anthracnose
thirani mankhwala a Daconil mmene mumathirila mankhwala a Anthracnose
agriculture
agriculture document
en2087
Bean common mosaic virus Symptoms include dark green sector on leaves and curling of leaves
zizindikilo za nthenda ya mosaic virus za nyemba ndi monga kubiliwila ndi kukwinyana kwa masamba
agriculture
agriculture document
en2088
Pests in beans include Bean Stem Maggot, bean beetle and bean aphids
tizilombo tomwe timagwira nyemba ndi monga mbozi, zitete ndi nsabwe za mmasamba
agriculture
agriculture document
en2089
Beetles can be controlled by spraying carbaryl at the rate of 85g in 14 litre of water or 1litre of water in ULV Sprayer.
tizilombo (beetle) muthane nazo powazila mankhwala a carbaryl pa mlingo wa 85g mu 14 lita ya madzi mu sipuleya ya ULV
agriculture
agriculture document
en2090
Do hand threshing to avoid damage
nsanzulani ndi manja kuopa kuononga
agriculture
agriculture document
en2091
Do not store cowpea treated with Phostoxin in a living room or animal house.
osasunga nandolo amene anathiridwa phostoxin mu chipinda chopezeka anthu kapena mosungila ziweto
agriculture
agriculture document
en2092
Do not use Phostoxin directly without wrapping it or in a container that is not airtight
osagwiritsa ntchito phostoxin ngati sanasungidwe mu kontena yovindikila bwino yosalowa mpweya
agriculture
agriculture document
en2093
Do not use or sell cowpea grains that have been mixed with storage chemical until after 6 months of storage.
osagwiritsa ncthito kapena kugulitsa nandolo amene ngati miyezi isanu ndi umodzi siinathe chithilireni mankhwala
agriculture
agriculture document
en2094
Ensure good hygiene in the store and check every 2 weeks for any change in storage conditions
onetsetsani kuti mosungila mwanu ndi mwaukhondo komanso kumayang'anamo pakatha masabata awiri aliwonse kuti muzikhala mokonza bwino
agriculture
agriculture document
en2095
Keep rodents away.
sungani kutali ndi makoswe
agriculture
agriculture document
en2096
Conduct the second spraying 10 days after the first spraying when the crop is in full flowering and podding
thiraniso mankhwala pakatha masiku khumi chithirireni mankhwala ena pamene mbewu zanu zamaliza kupanga maluwa komanso kuyamba kubereka
agriculture
agriculture document
en2097
Conduct the first spraying between 30 and 35 days (4–5 weeks) after planting when flower bud initiation has started. T
thirani mankhwala oyambilira pakati ma masiku 30 ndi 35 (masabata 4-5) mukabzala pamene maluwa ayamba kumasula kumene
agriculture
agriculture document
en2098
For varieties susceptible to aphids, one spraying may be needed at seedling stage, 14–21days after planting.
kwa mitundu yosachedwa kugwidwa ndi nsabwe za mmasamba, kupopera mankhwala kamodzi zikangomela ndi kofunika, masiku 14 mpaka 21 zikangobzalidwa
agriculture
agriculture document
en2099
Clean up haulms from previous crops, as these insects may survive over season in such rubbish.
chotsani mapesi a mbewu zakale kuti mbewu zatsopano zisagwidwe ndi tizilombo timene timabitsala mmapesimo
agriculture
agriculture document
en2100
Late-maturing varieties require more sprays than early maturing varieties because of the staggered flowering period
mbewu zochedwa kucha zimafunika kuthiridwa mankhwala kwa nthawi yaitali kamaba kakuti maluwa ake amatulukaso mochedwa kusiyana ndi mbewu zokucha msanga
agriculture
agriculture document