sent_id
stringlengths
3
7
english
stringlengths
3
1.06k
chichewa
stringlengths
4
3.03k
topic
stringclasses
8 values
source
stringclasses
17 values
en2302
However no one food supplies all the nutrients the body needs.
palibe chakudya chimene chimapereka michere yonse yofunikila nthupi
agriculture
agriculture document
en2303
They are also required for control of body processes and for protection against diseases and infections
amaloledwanso kugwira ntchito zochitika nthupi ndi kuteteza kumatenda ndi tizirombo
agriculture
agriculture document
en2304
Root/Stem vegetables such as carrots, garlic, ginger, onions
mizu/tsinde zamasamba monga kaloti, adyo, jinja, anyezi
agriculture
agriculture document
en2305
Fruits are a source of many essential nutrients
zipatso ndi gwero la michere yazakudya yofunikila nthupi
agriculture
agriculture document
en2306
Deliberate effort should be made to plant trees that mature faster and produce in different seasons
Khama liyenera kuchitidwa dala kubzala mitengo yomwe imakhwima mwachangu ndi kutulutsa munyengo zosiyanasiyana
agriculture
agriculture document
en2307
Poultry include chickens, ducks, guinea fowls, and pigeons as they are commonly found and easy to rear.
mbalame zopezeka kwambiri komanso zosavuta kuweta ndi monga nkhuku, abakha, nkhanga komanso nkhunda
agriculture
agriculture document
en2308
small stock animals that can be reared around the homestead include poultry, rabbits/guinea pigs and goats.
mitundu ya ziweto zazing'ono zimene zikhonza kuwetedwe pakhomo ndi monga nkhuku, akalulu/nkhumba ndi mbuzi
agriculture
agriculture document
en2309
Other small stock such as pigs are also possible to manage for households that have adequate labour and feed.
mitundu ina ya ziweto zazing'ono ngati nkhumba ndizosavuta kusamala kwa amene ali ndi antchito ndi zokudya zokwanila
agriculture
agriculture document
en2310
It creates awareness among stakeholders on new and available technologies
zimapereka chidziwitso cha ukadaulo watsopano womwe ulipo kwa onse okhudzidwa
agriculture
agriculture document
en2311
It stimulates the need in smallholder farmers to seek for information about the new technology
zimalimbikitsa alimo ang'onoang'ono kusaka uthenga olondola okhuzana ndi ukadaulo watsopano
agriculture
agriculture document
en2312
A field day is an event organized for a group of participants to see improved technologies being practiced on one or more farms, demonstration plots, or research stations
tsiku lowona kumunda ndi njira imodzi yomwe alimi amatha kukaona ukadaulo wamakono umene ukuchitidwa ndi pamunda kapena minda, minda ya zionetselo kapena minda kafukufuku
agriculture
agriculture document
en2313
A lead farmer handles technologies that he/she has already adopted and is practicing
mlimi wotsogolela amaphunzitsa ukadauolo womwe iye wayamba kuchita kale
agriculture
agriculture document
en2314
A lead farmer is an individual farmer who has been selected by the village to voluntarily assist in the delivery of a maximum of three good agricultural practices/technologies that are enterprise specific and is trained in those technologies
Mlimi wotsogolera ndi mlimi payekha yemwe wasankhidwa ndi mudzi kuti athandize modzifunira popereka njira zitatu zabwino zaulimi / matekinoloje omwe ali okhudzana ndi mabizinesi ndipo amaphunzitsidwa umisiriwo.
agriculture
agriculture document
en2315
This requires a seed rate of 8 kg per hectare and the expected plant population is 37,000 and 44,444 plants per hectare at 90 cm and 75 cm ridge spacing respectively
Izi zimafuna mbeu yokwana makilogalamu 8 pa hekitala ndipo chiwerengero cha zomera ndi 37,000 ndi 44,444 pa hekitala pa 90 cm ndi 75 cm motalikirana ndi mitsetse.
agriculture
agriculture document
en2316
The rate for leafroller control are for army worm.
njira yothanilana ndi ma leafroller ndi chimodzimodzi ndi ya ma arym worm
agriculture
agriculture document
en2317
The most important insect pest for groundnuts is aphids transmit the Rosette virus.
Tizilombo tofunika kwambiri ku mtedza ndi nsabwe za m'masamba zomwe zimafalitsa kachilombo ka khate.
agriculture
agriculture document
en2318
Aphids can be controlled by early planting and planting at correct spacing
Nsabwe za m'masamba zimatha pewedwa ndi kubzala msanga ndikubzala pamalo oyenera.
agriculture
agriculture document
en2319
However potential yields are 2000kg/ha for large seeded varieties and 2500kg for small seeded varieties
Komabe zokolola zomwe zingatheke ndi 2000kg/ha kwa mitundu ikuluikulu yambewu ndi 2500kg ya mbeu zazing'ono.
agriculture
agriculture document
en2320
Pearl millet is an important food crop mostly grown in the Shire Valley
mapira ndi mbewu yofunikira kwambiri yomwe imabzalidwa ku Shire Valley
agriculture
agriculture document
en2321
Farmers should be encouraged to grow pearl millet due to its tolerance to drought
alimi alimbikitsidwe ulimi wa mapiri chifukwa cha kulolela kwake nyengo ya chilala
agriculture
agriculture document
en2322
Farmers should be encouraged to grow improved varieties which are high yielding.
alimi akuyenera alimbikistidwe kulima mbewu zamakono zoika kwambiri
agriculture
agriculture document
en2323
Nyankhombo (Okashana–1) is a variety currently recommended for the Shire Valley
Nyankhombo (Okashana–1) ndi mtundu womwe ukulimbikitsidwa pakali pano ku Shire Valley
agriculture
agriculture document
en2324
It matures very early (75 to 80 days) and has a plant height of 1.9 to 2.3m.
imacha msanga (masiku 75 mpaka 80) amatalika mpakana ma mita 1.9 kufikila 2.3
agriculture
agriculture document
en2325
It has a yield potential of 2,500kg per hectare.
Ili ndi kuthekera kokolola 2,500kg pa hekitala.
agriculture
agriculture document
en2326
SDMV 90031 is a high yielding variety, yielding above 2800 kgha-1.
SDMV 90031 ndi yobereka kwambiri, yopatsa kuposa 2800 kkha-1.
agriculture
agriculture document
en2327
It is resistant to drought, diseases and insect pests such as Stem borer
imagonjetsa chilala, matenda ndi tizilombo monga stem borer
agriculture
agriculture document
en2328
Farmers can also use unimproved pearl millet varieties grown in their areas
alimi akhonza kugwiritsa ntchito mbewu yakale ya mapira a pearl yomwe amalima m'dera mwao.
agriculture
agriculture document
en2329
Since pearl millet is an out crossing crop, farmers must use fresh seed each season
popeza mbewu ya mapila a pearl ndiyochokela maiko ena, alimi akuyenera kubzala mbewu yatsopano yosabwereza chanka chilichonse
agriculture
agriculture document
en2330
Ridges for improved varieties should be prepared at 75 cm and 90 cm for those unimproved
mizere ya mbewu zamakono isiyane 75 sentimita ndipo ya mbewu zakale iziyane 90 sentimita
agriculture
agriculture document
en2331
Pearl millet must be planted with first planting rains when 25mm rainfall has fallen.
mapira a pearl abzalidwe ndi mvula yoyambilira pamene yagwa ma milimita 25
agriculture
agriculture document
en2332
The seed rate is 4kg per hectare.
mbewu yoyenela kubzala pa hekitala ikhale yokwana 4kg
agriculture
agriculture document
en2333
Either use 200kg of 23:10:5+6S+1Zn per hectare at the time of planting.
mukhonza kugwiritsa ntchito 200kg ya 23:20:5+6s+1Zn pa hekitala pamene mukubzala
agriculture
agriculture document
en2334
Apply using drilling method 18g per meter of ridge using two and half cupfuls of cup No.8
gwiritsani ntchito pobowola njira 18g pa mita ya mzere uliwonse pogwiritsa ntchito makapu awiri ndi theka la chikho nambala 8
agriculture
agriculture document
en2335
Timely weeding during the first 6 weeks is recommended and should be followed by banking
onetsetsani kuti kupalira koyamba kwachitika mu nthawi yake pasanathe masabata asanu ndi limodzi kutsogozedwa ndi kubandila
agriculture
agriculture document
en2336
Birds are most important pests of pearl millet and they should be scared right from head formation to harvesting.
mbalame zimaononga kwmabiri mapira kotelo zikuyenera kuthamangisidwa mapila akangoyamba kumene kubereka
agriculture
agriculture document
en2337
The Disease of economic importance is Downy mildew and can be controlled by use of improved varieties and early planting.
nthenda yovuta kwmabiri ndi downy mildew ndipo tingathane nayo pogwiritsa ntchito pobzala mbewu zamakono ndi kubzala mwachangu
agriculture
agriculture document
en2338
Timely harvesting minimises weevil attack in the field, grain damage and shattering
kukolola mu nthawi yoyenera kumathandiza kuti zokolola zathu zisagwidwe ndi anankafumbwe mmunda ndi mu nkhokwe
agriculture
agriculture document
en2339
Treat the grain with Wivokil Super Dust or Actelic Super Grain Dust at the rate of 25g per 50kg bag
thirani ufa wa Wivokil Super Dust or Actelic Super Grainku mbewu yanu pa mlingo wa 25g pa thumba lilolonse la 50kg
agriculture
agriculture document
en2340
The slash and burn (Visoso) as practiced in Chitipa and Karonga and Mzimba destroys vegetation and land productivity and should therefore be discouraged
monga momwe amachitila ku chitipa ndi karonga ndi mzuzu, visoso imaononga zomela komaso nthaka ndipo ikuyenela kuletsedwa
agriculture
agriculture document
en2341
For all finger millet cultivars apply 200kg of 23:10:5+6S+1.0Zn per hectare
thirani 200kg ya 23:10:5+6S+1.0Zn pa hekita ku mbewu iliyonse ya mapira
agriculture
agriculture document
en2342
Plant improved cultivars such as Dopalopa and Mavoli which are red and white grained
bzalani mbewu za makono monga dopalopa ndi mavoli zomwe zimakhala mbewu zofiila ndi zoyera
agriculture
agriculture document
en2343
Plant 2 to 4 weeks after first rains to allow Rapoko grass (Eleusine indica), a weed which looks like millet to emerge so that it can be controlled before millet is sown
bzalani pakatha masabata awiri moaka anayi mvula yoyamba ikagwa ndi cholinga chikuti mulore udzu wa rapoko (eleusine indica) womwe umafanana ndi mapira umele ndipo uchotsedwe
agriculture
agriculture document
en2344
Harvest the crop when the heads are dry and store whole heads in dry structures such as nkhokwes
kololani mbewu zonse zikawuma ndikusunga mbewu yonse mu nkhokwe zopanda chinyezi
agriculture
agriculture document
en2345
It performs well in these areas when the main rains are tailing off and the cool season is setting in.
zimachita bwino mmadera amene mvula ikusiya ndipo nyengo yozizila ikuyamba
agriculture
agriculture document
en2346
Jupateco 73 It is a semi-dwarf wheat variety adapted for production under irrigation in upland areas and matures in 90 to 120 days
Jupateco 73 ndi mtundu wa tirigu wamfupi womwe umabzalidwa ndi ulimi wanthirira mmalo okwera ndipo umakhwima pakati pa masiku 90 ndi 120
agriculture
agriculture document
en2347
Make a fine tilt seedbed to ensure good seedling emergence and establishment.
pangani bedi la dothi lofewa bwino kuti muonetsese kuti mbewu zamera bwino komanso zakhazikika
agriculture
agriculture document
en2348
In Phoka Hills, Viphya plateau and Misuku Hills, wheat planting should start from mid-April to mid-May.
ku mapiri a phoka, viphya ndi misuku, yambani kulima tirigu kuchokela pakati pa mwezi wa April mpaka pakati pa mwezi wa May
agriculture
agriculture document
en2349
Birds are the most important pests of wheat especially Quelea spp(mpheta) and should be controlled by scaring from grain setting period to harvesting
mbalame ndi mbewu zimene zimawononga kwambiri tirigu makamka mpheta (quelea spp) ndipo zikuyenera kuthamangisidwa pamene titigu wayamba kubereka
agriculture
agriculture document
en2350
Drill seed in rows 30cm apart and 5cm deep.
kumbilani mbewu pansi kwa 5cm ndikusiyanisa mizere kwa 30cm
agriculture
agriculture document
en2351
All types of fertilizers applied in wheat should be drilled 10cm deep and 10cm away from the rows.
mitundu yonse ya fetereza itjiriodwe ku tirigu pokumba 10cm ndi 10cm kutali ndi phando
agriculture
agriculture document
en2352
Apply 12g per 4 meters of row length using 3 cup full of cup No.5 for each type of fertilizer
thirani 24g pa 4mita ya mzere pogwiritsa ntchitp kapu namba 5 ya fetereza aliyense
agriculture
agriculture document
en2353
Threshing should be done on clean surfaces to avoid grain mixing with sand, stones and trash
punthani mbewu pa malo woyela kupewa kuti zingasakanizike ndi mchenga, miyala ndi zinyalala zina
agriculture
agriculture document
en2354
All shriveled and off type seed, stones and any trash should be removed
mphwephwa ndi mbewu zonse zongogweramo, miyala ndi zinyalala zonse zichotsedwe
agriculture
agriculture document
en2355
An application of Grain Dust at the rate of 25g per 50kg bag of grain will prevent weevil attack
kuthila mankhwala a ufa pa mlingo wa 25g pa 50kg ya chimanga zimateteza ku anankafumbwe
agriculture
agriculture document
en2356
Sunflower is commonly grown in areas such as South Mzimba, Kasungu North, Lilongwe to Mchinji plateau areas, Balaka and Phalombe as well as Lake Chilwa plain
mpendadzuwa amalimidwa kwambiri mmadera a kumwera kwa Mzimba, Kumpoto kwa Kasungu, Lilongwe mpaka mapiri a Mchinji, Balaka ndi phalombe komanso m'mbali mwa lake chira
agriculture
agriculture document
en2357
PAN 7351 Recently released variety is well adapted to midaltitude
PAN 7351 ndi mbewu yomwe yatulutsidw apompano ndipo ikulimidwa kwambiri ku madera osakwera
agriculture
agriculture document
en2358
It has a yield potential of 4,000kg per hectare
ili ndi kuthekera kokolola ma kilogilamu 4000 pa hekitala
agriculture
agriculture document
en2359
The seed colour is black.
mbewu yake imakhala ya mtundu wakuda
agriculture
agriculture document
en2360
Super 530 is a medium maturing variety
super 530 ndi mbewu imene imakhwima chapakatikati
agriculture
agriculture document
en2361
Matures in 112 to 131 days.
imachapakatha masiku 112 mpaka 131
agriculture
agriculture document
en2362
Seed rate for unimproved cultivars is 8 kg per hectare and 3.5kg per hectare for improved varieties.
mbewu yakale yoyenera kubzala ndi 8kg pa hekita ndi 3.5kg pa hekita ya mbewu yamakono
agriculture
agriculture document
en2363
Planting sunflower 4 to 6 weeks after the onset of effective planting rains produces the best yields
kubzala mpendadzuwa pakati pa masabata anayi ndi asanu ndi limodzi mvula yoyambilira ikagwa kumathandiza kuti zichite bwino
agriculture
agriculture document
en2364
This will also let the crop escape diseases, since physiological maturity stage will occur under conditions of low relative humidity after the rainy season.
Izi zimapangitsa kuti mbewu isagwidwe ndi matenda, chifukwa zimakhwima mu nyengo yozizila
agriculture
agriculture document
en2365
Ridges should be spaced at 75cm or 90cm apart and planting stations should be 50cm apart.
mizere isiyane ma sentimita okwana 75 kapena 90 ndipo siyanisani 50 sentimita pakati pa mapando
agriculture
agriculture document
en2366
Plant 2 seeds per station for improved varieties
bzalani mbewu ziwiri pa phondo lililonse podzala mbewu yamakono
agriculture
agriculture document
en2367
Higher yields can be obtained when ridges are spaced at 75cm.
mukasiyanisa mizere ma sentimita 75 mumapeza zokolola zochuluka
agriculture
agriculture document
en2368
Weeding during the first 5 weeks after emergence is crucial.
kupalira masabata asanu oyambilila nkofunika kwambiri
agriculture
agriculture document
en2369
Sunflower is an important catch crop for witchweed (Striga asiatica),It should be used in rotation with maize to reduce witchweed infestation
mpendadzuwa ndi mbewu yofunikila kuthan ndi udzu wa kaufiti, ikuyenera kulimidwa mosintha ndi chimanga kuli muchepetse chiwerengero cha kaufiti
agriculture
agriculture document
en2370
Black seeded varieties fetch a higher price on the local market and it is advisable to grade the seed properly prior to marketing
mbewu yamaonekedwe akuda imagulitsidwa pa mtengo waukulu ku msika ndipo ndikofunikila kusankha mbewu yoyenera kugulitsa
agriculture
agriculture document
en2371
Sesame (Chitowe) is grown in Malawi either for food or cash.
chitowe chimalimidwa ngati chakudya kapena cha malonda malawi muno
agriculture
agriculture document
en2372
It is tolerant to drought and grown where other crops fail
imalolera ku nyengo ya chilala ndi kulimidwa pamene mbewu zina sizinachite bwino
agriculture
agriculture document
en2373
Sesame oil extracted from seeds is used for cooking and soap making
mafuta a chitowe amachokela ku nthanga zake zimene zimagwiritsidwa ntchito pophika komanso kupangila sopo
agriculture
agriculture document
en2374
Average yields range from 300 to 400 kg per hectare
zokolola zimatha kukhala 300 mpaka 400kg pa hekitala
agriculture
agriculture document
en2375
Sesame thrives best on soils which are well drained.
chitowe chimachita bwino pa nthaka yomwa madzi bwino
agriculture
agriculture document
en2376
Planting should be done between mid-January to mid-February so that the crop matures under dry days
mukuyenera kubzala pakati pa mwezi wa January ndi pakati pa mwezi wa February kuti mbewu zizakhwime nyengo ya mvula itatha
agriculture
agriculture document
en2377
Sesame is ready for harvest when one third to two thirds of the lower plant parts turn yellow
chitowe chimakololedwa mbali imodzi kapena ziwiri mwa zitatu za nthambi ya pansi zikachita chikasu
agriculture
agriculture document
en2378
Plant 2 seeds per planting station, 15cm apart on ridges spaced at 90cm
bzalani mbewu ziwiri pa phando, mizere isiyane 15cm
agriculture
agriculture document
en2379
Early weeding protects the crop from intensive competition with weeds until the crop produces sufficient canopy to suppress further weed growth.
kupalila msanga kumateteza mbewu ku mpikisano ndi udzu mpakana mbewu yanu iyange masamba obweretsa nthuzi
agriculture
agriculture document
en2380
The critical period is within the first 4 to 6 weeks of crop establishment.
nyengo yovutisitsa kwambiri ndi masabata anayi mpaka asanu ndi limodzi mbewu zikangobzalidwa
agriculture
agriculture document
en2381
When completely dry, thresh by gently and carefully beating the bundles turned upside down into a container
zikawuma bwinowbino, punthani mosamala zitayang'ana pansi
agriculture
agriculture document
en2382
Bacterial blight is the most serious disease when the crop is planted early
bacterial blight ndi nthenda imene imavutisa kwambiri mbewu zikabzalidwa mwachangu
agriculture
agriculture document
en2383
Leafspot is a serious problem in sesame as it causes premature defoliation of the leaves.
leafspot ndi matenda ovuta kwambiri amene amadzesa kugwa kwa masamba mbewu zisanache
agriculture
agriculture document
en2384
Suitable areas for castor growing are the Shire Valley, Phalombe Plain, Lakeshore Plain in Lilongwe and Chitipa
malo abiwno olimapo msatsi ndi Shire Valley, phalombe, mbali mwa nyanja ku Lilongwe ndi Chitipa
agriculture
agriculture document
en2385
To achieve high yields, plant with the first rains in areas such as the Shire Valley, Phalombe Plain and the Lakeshore Plain to allow the fruit to mature as the rains tail off
kuti mukolole zochuluka, bzalani ndi mvula yoyambilira mmadera aku shire valley, phalombe ndi ku lakeshore ndicholinga kuti mvula ikamatha zikhale zitakhwima
agriculture
agriculture document
en2386
Keep the field weed free throughout the growing season
munda onse ukhale opanda tchire mu nyengo yolima
agriculture
agriculture document
en2387
Plant castor on ridges spaced at 75cm or 90cm.
mizere yolimapo castor italikane 75 mpaka 90cm
agriculture
agriculture document
en2388
Sow one seed at 60cm between planting stations on the ridge
bzalani mbewu imodzi 60cm pakati paphando lililonse
agriculture
agriculture document
en2389
The seed rate is 10 to 12kg per hectare
mbewu yoyenera kubzala pa hekitala ikhale yokwana 10 mpaka 12kg
agriculture
agriculture document
en2390
The most common disease of castor is Botritis mould–Recem (Botrytis cinerea)
nthenda yodziwika kwambiri ya castor ndi Botritis mould–Recem (Botrytis cinerea)
agriculture
agriculture document
en2391
It is not economical to control the disease with fungicide.
palibe phindu lothandilana ndi matendawo pothila mankhwala (fungicides)
agriculture
agriculture document
en2392
The pods are ready for harvesting when they turn grey and the pods shows cracks
mbewu zikhonza kukololedwa zikasintha mtundu kukhla mbuu komanso ngati zayamba kuthetheka
agriculture
agriculture document
en2393
The giant local variety produces the first ripe pods suitable for picking approximately 140 days after planting
mtundu waukulu wa mbewu umatulutsa zipatso zakupsa zoyambilira zokuti zithyoledwe pakatha masiku 140
agriculture
agriculture document
en2394
Dry the pods on a clean dry ground in the sun for a few days before shelling.
yanikani makoko pansi poyera padzuwa kwa masiku angapo musanaswe
agriculture
agriculture document
en2395
Cassava stem storage technique is encouraged among smallholder farmers who store the harvested cassava stems until there is enough rains for planning in the next season
njira yosunga nthambi za chinangwa za mbewu kumalimbikitsidwa pkati pa alimi ang'onoang'ono amen amasunga mbewu zozabzala mvula ikazayamba
agriculture
agriculture document
en2396
Planting material should be free from insect pests such as cassava mealy bug and cassava scales;
zipangizo zodzalira sizakhale zogwidwa ndi tizizlombo monga cassava mealy bug ndi cassava scales
agriculture
agriculture document
en2397
Cuttings should be obtained from the base to the middle portions of well matured plants of older than 9 months
mitengo ya mbewu ikuyenera kudulidwa pa nthambi zapakati zokhwima bwino
agriculture
agriculture document
en2398
Farmers should not plant cassava late
alimi asamabzale chinangwa mochedwa
agriculture
agriculture document
en2399
Cassava does well on well drained soils
chinangwa chimachita bwino pa nthaka yolowa madzi bwino
agriculture
agriculture document
en2400
These are sucking insects and their feeding habit is not very destructive.
iti ndi tizirombo toyamba madzi komanso kadyedwe kake sikakhala kowononga
agriculture
agriculture document
en2401
Control is aimed at the disease and not the insect pest
vuto lofunika kuthana nalo ndi matenda osati tizilombo
agriculture
agriculture document