sent_id
stringlengths
3
7
english
stringlengths
3
1.06k
chichewa
stringlengths
4
3.03k
topic
stringclasses
8 values
source
stringclasses
17 values
en2602
Drought occurs in Malawi when rainfall is less than 75% of normal
Chilala chimabwera kuno ku Malawi pomwe mvula imagwa pansi pa 75% yanthawi zonse
agriculture
agriculture document
en2603
Riverine flood: Occurs when excessive rainfall over an extended period of time causes a river to exceed its capacity
Kusefukira kwa Mtsinje: Kumachitika pamene mvula yadzaoneni kwa nthawi yaitali ipangitsa kuti mtsinjewo upitirire mphamvu yake
agriculture
agriculture document
en2604
Droughts and floods are the most severe of hazards experienced and the most serious obstacles to agricultural productivity and food security in Malawi.
Chilala ndi kusefukira kwa madzi ndi zoopsa kwambiri zomwe anthu akukumana nazo komanso zolepheretsa kukula kwaulimi komanso kupezeka kwa chakudya Malawi.
agriculture
agriculture document
en2605
Climate change has resulted in shifting planting dates of maize
nyengo yobzalila chimanga inasinthaso malingana ndi kusintha kwa nyengo.
agriculture
agriculture document
en2606
Changes in the maize varieties grown (from medium to late maturing to short maturing varieties).
kusintha kwa mbeu zobzala za chimanga ( kuchoka ku mbeu zokucha mochedwa kufikila ku mbeu zokucha msanga)
agriculture
agriculture document
en2607
Important predictions of future impacts of climate change on crop productivity
Zonenedweratu zokhuza mtsogolo zakusintha kwanyengo pa zokolola
agriculture
agriculture document
en2608
Livestock production in Malawi is seriously affected by climate change.
Kuweta kwa ziweto m’Malawi muno kwakhudzidwa kwambiri ndi kusintha kwa nyengo.
agriculture
agriculture document
en2609
The animals reduce their food intake because of the higher temperatures;
Nyamazo zimachepetsa kudya chifukwa cha kutentha kwambiri;
agriculture
agriculture document
en2610
Areas suitable for grazing and availability of forage have declined due to dry spells and droughts, leading to reduction in livestock production and deaths;
Malo odyetserako ziweto achepa chifukwa cha mvula ndi chilala, zomwe zachititsa kuchepa kwa ziweto ndi kufa;
agriculture
agriculture document
en2611
Inadequate availability of feed and water due to droughts are causing decreased milk production (GFDRR, 2016
Kusapezeka kokwanira kwa chakudya ndi madzi chifukwa cha chilala kumapangitsa kuti mkaka ukhale wochepa (GFDRR, 2016
agriculture
agriculture document
en2612
Effects of climate change on pests and diseases
zotsatira za kusintha kwa nyengo pa tizirombo ndi matenda
agriculture
agriculture document
en2613
Pests and diseases are major constraints to farm productivity in Malawi.
Tizilombo ndi matenda ndizomwe zimalepheretsa ntchito zaulimi Malawi.
agriculture
agriculture document
en2614
Drying up of lakes and temperature changes, which have affected aquatic life and resulted in declining fish stocks and fish catches (Msiska et al. 2017, MoECCM, 2013);
kuuma kwa nyanga ndi kusintha kwa nyengo kwakhudza zamoyo za mmadzi, zomwe zachepetsa chiwerengero cha nsomba ndi kawezedwe komwe.
agriculture
agriculture document
en2615
Food insecurity
kusowa chakudya
agriculture
agriculture document
en2616
Extreme hunger
njala yoopsa
agriculture
agriculture document
en2617
Malnutrition
kunyentchera
agriculture
agriculture document
en2618
Improve management of croplands
Kupititsa patsogolo kasamalidwe ka minda
agriculture
agriculture document
en2619
Plant adaptive crop varieties
kubzala mbeu zopilira ku nyengo zosiyanasiyana
agriculture
agriculture document
en2620
Use improved storage facilities for the harvest;
kugwiritsa ntchito nyumba za makono zosungilamo zokolola
agriculture
agriculture document
en2621
Improve pasture management
kupititsa pastogolo kasamalidwe ka malo odyetsera ziweto
agriculture
agriculture document
en2622
Practice sustainable forest management
Kusamalira nkhalango mokhazikika
agriculture
agriculture document
en2623
Use weather and early warning information;
Gwiritsani ntchito zidziwitso zanyengo ndi chenjezo loyambirira;
agriculture
agriculture document
en2624
Use fish species that are tolerant of changing climatic conditions;
Gwiritsani ntchito mitundu ya nsomba zomwe zimalolera kusintha kwa nyengo;
agriculture
agriculture document
en2625
Increase the resilience of smallholder fish farming households to climate change impacts;
kupangisa alimi ang'onoang'ono amene akupanga ulimi wa nsomba akhale opilira ndi kusintha kwa nyengo
agriculture
agriculture document
en2626
Make the farmers more food secure compared to those who do not practice integrated fish-crop-livestock farming.
kupangisa alimi kukhale ndi chakudya chokwanira kusiyana ndi amene sapanga nawo ulimi wa nsomba, zakumunda ndi ziweto pakamodzi.
agriculture
agriculture document
en2627
In areas prone to drought famers must cultivate staple crops like sorghum, cassava, and pearl millet which are tolerant to drought
ku malo ovuta mvula alimi akuyenera kubzala mbeu zopirira ndi kuuma kwa nthaka monga mapira, chinangwa, mawere.
agriculture
agriculture document
en2628
farmer must: • Plant late maturing maize varieties such as: SC 719 which takes 158 days to maturity or local maize.
alimi akuyenera kubzala mbeu zochedwa kucha monga SC 719 yomwe imacha pakatha masiku 158 kuti chikhwime
agriculture
agriculture document
en2629
Swales for water harvesting
maswale ngati njira yokolela madzi
agriculture
agriculture document
en2630
Plant the crops early to benefit from the available rain
Bzalani mbewu msanga kuti mupindule ndi mvula yomwe ilipo
agriculture
agriculture document
en2631
A swale is a technology used to harvest rainwater in a farm located on a slope and allow the water to seep through the farm over time.
swale ndi ukadaulo umene umagwiritsidwa ntchito pokolola madzi a mvula pa munda umene uli malo otsetseleka ndikulola madzi kuti alowelele mkati mwa munda
agriculture
agriculture document
en2632
The length of the swales must be equivalent to the length of the ridges
kutalika kwa swale kukhale kofanana ndi kutalika kwa zitunda/mizere
agriculture
agriculture document
en2633
A swale is a soil and water conservation technology
Swale ndi luso lomwe limathandiza kusunga nthaka ndi madzi
agriculture
agriculture document
en2634
It holds rain water and reduces effects of surface runoff
Imasunga madzi amvula ndikuchepetsa zotsatira za kusefukira kwamadzi
agriculture
agriculture document
en2635
Reduces nitrate leaching because of minimal mechanical disturbance of soil;
zimachepetsa kukokoloka kwa nitirati chifukwa chosasokoneza nthaka
agriculture
agriculture document
en2636
Planting crops under Msangusangu trees;
Kubzala mbewu pansi pa mitengo ya Msangusangu;
agriculture
agriculture document
en2637
Increased water infiltration into the soil
kuchuluka kwa madzi olowa nthaka
agriculture
agriculture document
en2638
Beekeeping is a profitable enterprise that is undertaken by subsistence farmers as well as commercial farmers in Malawi.
ulimi wa njuchi ndi wopindulisa umene umapangidwa ndi alimi ang'onoang'o komanso alimi akuluakulu
agriculture
agriculture document
en2639
Provide clean drinking water near the beehives, for bees to drink
kumasiya madzi oyera bwino pafupi ndi kuti njuchi zizimwa.
agriculture
agriculture document
en2640
Hang the beehives within the farm and/or surrounding vegetation
Ponyani ming'oma ya njuchi pafamu ndi/kapena zomera zozungulira
agriculture
agriculture document
en2641
Large quantities of crop yield are destroyed by storage pests and diseases, resulting in food insecurity among farming families.
chakudya chambiri chikakololedwa chimaonongeka ndi tizilomba posunga zomwe zimabweretsa kusowa kwa chakudya pamaanja
agriculture
agriculture document
en2642
Post-harvest challenges faced by farmers in Malawi tend to be given limited attention by farmers and the agricultural sector as a whole, compared to pre-harvest operations
ziphinjo zimene alimi amakumana nazo akakolola mbewu ku munda sizipatsidwa chidwi kwmabirir kusiyana ndi ziphinja zomwe makumana nazo asanabzale
agriculture
agriculture document
en2643
There are limited technologies developed and limited extension services provided for post-harvest than for field operations.
pali ukadaulo ndi ulangizi ochepa umene umaperekedwa kwa alimi okhudza kasamalidwe ka mbewu zikakololedwa kusiyana ndi ulangizi wapamunda
agriculture
agriculture document
en2644
Post-harvest handling is about preparing the harvest into a most suitable form for consumers and industry
Kusamalira pambuyo pokolola ndikukonzekera zokolola kuti zikhale zoyenera kwa ogula ndi mafakitale
agriculture
agriculture document
en2645
For a long time, post-harvest losses were mostly regarded as only those occurring in storage.
kwa nthawi yaitali kuluzazidwa kwa zokolola kumatengedwa ngati kumadza pamen zokolola zili mu nkhokwe
agriculture
agriculture document
en2646
Winnow and clean the grain
petani ndi kuyeretsa mbewuyo
agriculture
agriculture document
en2647
The harvest is guarded from animals and birds.
zokolola zimatetezedwa ku mbalame ndi zilombo
agriculture
agriculture document
en2648
Clean and fumigate the grain store before storage of the new harvest
konzani ndi kuthila mankhawala mu nkhokwe yanu musanasungemo zokolola zatsopano
agriculture
agriculture document
en2649
The ideal storage facilities are those that provide maximum possible protection and suitable conditions to the harvest
nkhokwe zabwino ndi zimene zimateteza mbewu zathu komanso kupereka zofunika zoyenera zomwe mbewu zathu zimafunikila
agriculture
agriculture document
en2650
Torn sacks are not used to store grain.
musagwiritse ntchito matumba obooka
agriculture
agriculture document
en2651
Create aeration in the store to reduce the temperature
pangani motulukila mpweya
agriculture
agriculture document
en2652
Never mix old and fresh harvest in the same store;
osaphatikiza zokolola zakale ndi zatsopano
agriculture
agriculture document
en2653
Establish product-buying points within easy reach of farming communities
khazikitsani misika pafupi ndi midzi
agriculture
agriculture document
en2654
Establish demonstration plots
khazikitsani minda yochitila zionetselo
agriculture
agriculture document
en2655
Planting crops under Msangusangu trees;
bzalani zakumunda zanu pansi pa mitengo ya msangusangu
agriculture
agriculture document
en2656
The steeper the slopes, the closer the trenches to one another
maenje afupikane pa malo otsetseleke kwambiri
agriculture
agriculture document
en2657
Agriculture plays an important role in the national economy of Malawi, and plays a key role in ensuring food security.
ulimi umagwira ntchito yaikulu kwambirir pankhani zachuma malawi ndi kuonetsetsa kupezeka kwa chakudya chokwanira
agriculture
agriculture document
en2658
Adopt crop rotation
kutengela ulimi wa kasinthasintha
agriculture
agriculture document
en2659
Increase adoption of Climate smart agriculture practices by farmers;
Kuonjezera kutsata njira za ulimi wanzeru kwa nyengo ndi alimi;
agriculture
agriculture document
en2660
In recent years, the total daily, monthly or annual rainfall has varied from year to year, thus, there have been wet years and dry years
mu zaka zaposachedwa, mvula yatsiku ndi tsiku, mwezi uliwonse kapena pachaka yakhala ikusiyana chaka ndi chaka, motero, pakhala zaka zamvula ndi zopanda mvula
agriculture
agriculture document
en2661
The rainfall pattern has been erratic; and has had adverse impact on farming activities.
Kugwa kwamvula kwakhala kosasinthasintha; ndipo zasokoneza ntchito zaulimi.
agriculture
agriculture document
en2662
Maize is the dominant crop in Malawi
chimanga ndi mbeu yomwe imalimidwa kwambiri m'Malawi
agriculture
agriculture document
en2663
Unfortunately, most farmers in Malawi have inadequate access to pest, weed and disease control services because veterinary and crop protection services are severely under-resourced
Tsoka ilo, alimi ambiri Malawi muno alibe mwayi wopeza chithandizo chothana ndi tizirombo, udzu ndi matenda chifukwa ntchito zachiweto ndi zoteteza mbeu ndi zoperewera kwambiri.
agriculture
agriculture document
en2664
Effects of climate change on lake fisheries in Malawi
zotsatila za kusintha kwa nyengo pa ulimi wa nsomba mu nyanja ya malawi
agriculture
agriculture document
en2665
The smaller and faster breeding sardine type Angraulicypris sardella (locally called Usipa) has replaced Chambo as the dominant species.
usipa waung'ono omwe umakula mwachangu unalowa mmalo mwa chambo ngati nsomba zodyedwa kwambiri
agriculture
agriculture document
en2666
Farmers are abandoning fish farming activities because of water shortages
Alimi akusiya ntchito yoweta nsomba chifukwa cha kusowa kwa madzi
agriculture
agriculture document
en2667
Use improved storage facilities for the harvest
kugwiritsa ntchito nkhokwe za makono
agriculture
agriculture document
en2668
Practice agroforestry
kuyesela ulimi wophatitikiza zakumunda ndi mitengo
agriculture
agriculture document
en2669
Certified improved seeds
mbweu yabwino yotsimikizika
agriculture
agriculture document
en2670
Grow disease tolerant cowpea varieties: Sudan 1 (Nseula) and IT82E-16 (Khobwe);
Kulima mbeu za Nandolo zopilira ku matenda monga Sudan 1 (Nseula) and IT82E-16 (Khobwe)
agriculture
agriculture document
en2671
Grow the early maturing and disease tolerant soya bean variety:
kulima mbeu ya soya yosachedwa kucha msanga komanso yopilira ku matenda
agriculture
agriculture document
en2672
Grow the drought tolerant ground nut variety:
kulima mbeu ya mtedza yopilila ku nyengo youma/yosowa mvula
agriculture
agriculture document
en2673
Production and use of compost
kapangidwe ndi kagwiritsidwe ntchito ka manyowa a kompositi
agriculture
agriculture document
en2674
Water harvesting and conservation technologies
njira zamakono zokololela ndi kusamala madzi
agriculture
agriculture document
en2675
Pit-planting is a rain water harvesting technology;
kubzala mbeu mmaenje ndi njira imodzi yokololera madzi a mvula
agriculture
agriculture document
en2676
Integrate livestock with crop production
ulimi ophatikiza ziweto ndi zakumunda
agriculture
agriculture document
en2677
Beekeeping is a profitable enterprise that is undertaken by subsistence farmers as well as commercial farmers in Malawi.
Kuweta njuchi ndi bizinesi yopindulitsa pakati pa alimi ang'onoang'ono komanso alimi amalonda Malawi muno.
agriculture
agriculture document
en2678
Use traditional hives; transitional hives or the more advanced modern hive (depending on available resources);
gwiritsani ntchito mng'oma zalokolo kapena zamakono malingana ndi zipangizo zomwe muli nazo
agriculture
agriculture document
en2679
The harvest is dried on canvas or on mats
zokolola zanu ziyanikidwe pa thandala kapena pa mkeka/mphasa
agriculture
agriculture document
en2680
Be dry, cool and well ventilated
mukhale mowuma, mozizilila ndi molowa bwino mpweya
agriculture
agriculture document
en2681
Be affordable to the farmer
zikhale zosavuta kupeza kwa mlimi
agriculture
agriculture document
en2682
New sacks (if possible) are used to store the new harvest
ngati kuli kotheka, gwiritsani ntchito matumba atsopano posunga zokolola kumene
agriculture
agriculture document
en2683
Rodents consume almost everything that a farm house homestead can have (apart from metal objects)
makoswe amadya ndi kuonoka chilichonse mu nkhokwe kupatula zinthu za chitsulo
agriculture
agriculture document
en2684
Use rodenticides available in the market.
gwiritsani ntchito mankhwala a makoswe amene amapezeka ku misika
agriculture
agriculture document
en2685
Use cats (a biological control method)
gwiritsani ntchito amphaka (ngati njira imodzi ya chilengedwe)
agriculture
agriculture document
en2686
A key limiting factor to increased production of the high value crops by smallholder farmers is access to produce markets in the remote, rural communities
vuto limodzi lalikulu lomwe limachititsa alimi ang'onoang'ono kuti asamalime mbewu zopindulitsa ndi kusowa kwa misika mmadera oyandikana ndi midzi
agriculture
agriculture document
en2687
A majority of farmers in Malawi are experienced in production of kidney beans, soya beans and groundnuts.
alimi ambiri mmalawi ali ndi ukadaulo ochuluka wa nyemba, soya ndi mtedza
agriculture
agriculture document
en2688
Alleviating poverty in rural households
kuchepetsa umphawi mmakomo akumidzi
agriculture
agriculture document
en2689
Women actively be involved in processing and marketing processes to lift them from low-skilled positions and also be provided with the necessary training
Azimayi amatenga nawo gawo pakukonza ndi kutsatsa malonda kuti awachotse pamaudindo otsika komanso kupatsidwa maphunziro ofunikira.
agriculture
agriculture document
en2690
Women must be included in all decision making structures at all levels of society
azimayi akuyenera kutenga nawo mbali popanga ziganizo mmagulu onse a mu dera
agriculture
agriculture document
en2691
Gender discrimination in employment opportunities
Kusalana pakati pa amuna ndi akazi mu mwayi wa ntchito
agriculture
agriculture document
en2692
Shift from crop varieties and livestock breeds that are highly susceptible to drought and heat to crop and livestock varieties/breeds that have greater drought and heat tolerance
Siyani ku mitundu ya mbewu ndi ziweto zomwe zimakhudzidwa kwambiri ndi chilala ndi kutentha kupita ku mbewu ndi mitundu ya ziweto zomwe zimapilira ndi chilala komanso kutentha kwambiri.
agriculture
agriculture document
en2693
Use climate forecast advice from extension services when implementing farm activities
Gwiritsani ntchito upangiri wolosera zanyengo kuchokera ku mautumiki a ulangizi pokhazikitsa ntchito zaulimi
agriculture
agriculture document
en2694
Change timing of farm operations
Kusintha nthawi ya ntchito zaulimi
agriculture
agriculture document
en2695
Adjust sowing dates to offset (avoid) moisture stress during warm periods
Sinthani masiku obzala kuti muchepetse (kupewa) kupanda chinyontho nthawi yofunda
agriculture
agriculture document
en2696
Use mulch stubble and straw
Gwiritsani ntchito chiputu ndi udzu
agriculture
agriculture document
en2697
Develop effective planning processes
Konzani njira zokonzekera bwino
agriculture
agriculture document
en2698
To control moulds the farmer must
Kuwongolera nkhungu mlimi ayenera
agriculture
agriculture document
en2699
Insect pests can cause 100% grain loss in storage.
Tizilombo toyambitsa matenda titha kuwononga mbewu zonse mosungira.
agriculture
agriculture document
en2700
They contaminate the stored produce by urinating on the produce and through their droppings (faecal material) which get mixed with the stored grain, rendering the produce unusable
amayipitsa zomwe zasungidwa pokodza pa zokolola komanso kudzera mu ndowe zawo (zinthu zakunja) zomwe zimakasakanizidwa ndi tirigu wosungidwa, zomwe zimaangitsa kuti zokololazo zisagwiritsidwe ntchito
agriculture
agriculture document
en2701
A gender friendly technology to men, women and youth
ukadaulo ogwirizana ndi abambo, amyi komanso achinyamata
agriculture
agriculture document