sent_id
stringlengths
3
7
english
stringlengths
3
1.06k
chichewa
stringlengths
4
3.03k
topic
stringclasses
8 values
source
stringclasses
17 values
en2702
A technology that is consistent with commitment to actions on gender sensitivity
ukadaulo womwe umagwirizana ndi kudzipereka kwa zinthu zokhudzana ndi kukhudzidwa kwa amuna ndi akazi
agriculture
agriculture document
en2703
A technology that has minimum labour input requirements
ukadaulo umene umafunika zogwirira ntchito zochepa
agriculture
agriculture document
en2704
Why beekeeping is a climate smart practice
mbweu yabwino yotsimikizika
agriculture
agriculture document
en2705
Less variability in yields
kusasiyana kwenikweni muzokolola
agriculture
agriculture document
en2706
Alternative source of firewood and construction timber; medicines; livestock fodder/feeds and thus new source of income;
gwero lopezekelatu la nkhuni ndi matabwa, mankhwala, zakudya za ziweto ndi njira yopezela ndalama
agriculture
agriculture document
en2707
Diminished effects of extreme weather events, such as heavy rains, drought and storms on the agro-ecosystem;
zotsatila za kusintha kwa nyengo monga mvula yamkuntho, chilala ndi mphepo pa ulimi ndi zachilengedwe
agriculture
agriculture document
en2708
Cover crops take up nitrogen from the soil and reduce its loss from the soil into the atmosphere
mbewu zophimba zimatenga nitrogen kuchoka mu nthaka komanso kuchepesa kuuluka kwa nitrogen kupita mmalele
agriculture
agriculture document
en2709
Replenishes soil nutrients through use of leguminous species in cereallegume intercropping practices
imabwenzeretsa michere yamunthaka pobzala mbewu za magulu a nyemba pamodzi ndi za magulu a chimanga
agriculture
agriculture document
en2710
If a farm is located in an area that is prone to crop failure due to unpredictable rains the farmer must:
ngati munda uli dera limene mbewu sizichita bwino chifukwa cha kusagwa kwa mvula, alimi akuyenera:
agriculture
agriculture document
en2711
Grow well under frequently changing climatic conditions and/or under drought conditions
zimakula bwino munyengo yosinthasintha ngakhaleso nyengo yopanda mvula/chilala
agriculture
agriculture document
en2712
Diversify farmers’ sources of income by selling fish as well as crop and livestock products
kusiyanitsa njira zopezela ndalama pogulitsa nsomba, zakumuda komanso zoweta
agriculture
agriculture document
en2713
Malawi has reported a 93% decline in catches of Oreochromis species (locally called Chambo) from Lake Malawi due to a combination of overfishing and adverse effects of climate change since 1990
malawi yanena za kustika kwa kawezedwe ka nsomba ya chambo ndi 93% chifukwa cha kuweza opyola muyezo komanos kusintha kwa nyengo kuchokela mu chaka cha 1990
agriculture
agriculture document
en2714
The average number of HOT NIGHTS per year increased by 41.0 days
avereji ya masiku otentha idakwera ndi masiku 41 pa chaka
agriculture
agriculture document
en2715
Climate variability involves short term variations (daily, seasonal, inter-annual or over several years) around a mean
kusintha kwa nyengo kumakhudza nyengo yaifupi (tsiku ndi tsiku, panyengo,pakati pa chaka kapena pazaka zambiri)
agriculture
agriculture document
en2716
Most fish ponds are drying up for long periods in a year, leading to premature and unscheduled harvesting of the fish;
maiwe ambiri a nsomba amauma kwa nthawi yaitali m'chaka, zomwe zimachititsa kuti akolole msanga komanso musakonzekela
agriculture
agriculture document
en2717
effects of climate change on aquaculture
zotsatila za nyengo oa ulimi wa m'madzi
agriculture
agriculture document
en2718
The animals reduce their food intake because of the higher temperatures
nyamazi zimachepetsa kudya kwambir chifukwa cha kutentha kwambiri
agriculture
agriculture document
en2719
The onset of rains has become more unpredictable with the changing climate.
kuyamba kwa mvula kwakhla kosadziwikiratu ndi kusintha kwa nyengo
agriculture
agriculture document
en2720
Some years have been wetter than others
zaka zina zimakhala za chinyezi kwambiri kusiyana ndi zina
agriculture
agriculture document
en2721
The risks climate change poses to agriculture in Malawi
kuopsa kwa kusintha kwa nyengo komwe kumadzetsa pa ulimi m'Malawi
agriculture
agriculture document
en2722
The onset of rains has become more unpredictable with the changing climate.
kayambidwe ka mvula kakhala kosinthasintha malingana ndi kusintha kwa nyengo
agriculture
agriculture document
en2723
This has determined the types of crops grown by farmers.
izi zimatsikimika mtundu wa mbewu zimene angadzale mlimi
agriculture
agriculture document
en2724
Area along the Shire river in the Shire valley of Malawi are prone to frequent riverine flooding.
mmbali mwa shire river ku shire valley kumakhudzidwa kwambiri ndi kusefukila kwa mitsinje
agriculture
agriculture document
en2725
Decrease use of fish meal and fish feeds;
chepetsani kagwiritsidwe ntchito ka zakudya za nsomba
agriculture
agriculture document
en2726
Apart from the species of fish that are being cultured, fish farming in Malawi tends to be sensitive to availability of water
kupatula mitundu ya nsomba imene ikuwetedwa, ulimi wa nsomba malawi muno umakhudziwanso ndi kapezedwe ka madzi
agriculture
agriculture document
en2727
Improve energy efficiency;
kutukula kasamalidwe ka mphamvu
agriculture
agriculture document
en2728
Buy risk insurance against effects of extreme weather events.
gulani ishulansi yoteteza zinthu mu nyengo yovuta kwmabiri
agriculture
agriculture document
en2729
Reduce variability in yields
kucheptsa kasiyanitsidwe eka zokolola
agriculture
agriculture document
en2730
Improved human nutrition
kutukula thanzi la anthu
agriculture
agriculture document
en2731
Increased animal feed (resilience/adaptation, mitigation and food security)
kuchukula kwa zakudya za ziweto (kupilira/kutengela, kuthetselati ndi kupezeka kwa chaudya)
agriculture
agriculture document
en2732
Alternate grazing with rest periods for the land
kudyestsa msipu mwakasinthasintha ndikupereka nthawi yopuma ku malo
agriculture
agriculture document
en2733
ensure that the farmer has transporting equipment such as wheelbarrows, baskets etc that minimise losses in transit
onesetsani kuti mlimi ali ndi zipangizo zoyenerera zonyamulila katundu monga ma wilibala, mabasiketi ndi izina kuchepesa kutayika kwa zokolola
agriculture
agriculture document
en2734
The drying grains are not allowed to get wet
mbewu zimene zawuma sizololedwa kunyowa
agriculture
agriculture document
en2735
Protect the harvest from extremes of temperature and, moisture;
tetezani mbewu ku nyengo yotentha kwambiri ndi chinyontho
agriculture
agriculture document
en2736
Harvest the crop at the right time of maturity of the grains
kololani mbewu zanu mu nthawi yoyenerera zikakhwima
agriculture
agriculture document
en2737
Dry the grain to the required moisture level before storage;
wumitsani mbewu mpaka ifike pa mlingo oyenerera zisanasungidwe
agriculture
agriculture document
en2738
An explicit gender strategy of empowering women along the whole agricultural value chain of a commodity must be developed and adopted.
khanzikitsani njira zolimbikitsila azimayi kuti azitenga nawo gawo mu zonse zochitika pa ulimi
agriculture
agriculture document
en2739
Implementation strategies should be developed with “local women and local researchers” that are familiar with the cultural contexts regarding gender norms.
njira zoyenera kutatila zipangidwe ndi azimayi komanso alangizi amene akudziwa bwino mavuto amene alipo okhudza chikhalidwe
agriculture
agriculture document
en2740
Cultural and legal barriers to womens’ rights to land must be identified and removed
kufufuza ndi kuchotsa chikhalidwe ndi malamulo ophinja ufulu wokhala ndi malo wa azimayi
agriculture
agriculture document
en2741
Women face more barriers in accessing extension services than men.
amayi amakuma ndi ziphinjo zochuluka kuti apeze ulangizi kusiyana ndi abambo
agriculture
agriculture document
en2742
Shift from crops and livestock types that are highly susceptible to drought and heat to crops and livestock types that are drought and heat tolerant
sinthani kuchoka ku mbewu ndi ziweto zosapilila ku chilala ndi kutentha ndikulima ndi kuweta ziweto zopilila ku chilala ndi kutentha
agriculture
agriculture document
en2743
Shift from crops and livestock types that are highly susceptible to pests and diseases to crops and livestock types that are pest and disease resistant/ tolerant;
sinthani kuchoka ku mbewu ndi ziweto zosapilira ku tizirombo ndi matenda ndi kulima ndi kuweta ziweto zopilira ku tizirombo ndi matenda
agriculture
agriculture document
en2744
Use climate forecast advice from extension services when implementing farm activities
kugwiritsa ntchito zolosela za nyengo pamene mukutsatila zochitika pamunda
agriculture
agriculture document
en2745
Buy weather-related crop and livestock insurance (where available and affordable)
gulani ishulansi ya zakumunda ndi ziweto (ngati zilipo komanso ngati mungakwanitse)
agriculture
agriculture document
en2746
Participate in initiatives that transfer income or assets to the poor
tengani nawo gawo mu zochitika zopititsa chuma kapena katundu kwa anthu osauka
agriculture
agriculture document
en2747
Develop efficient communication systems;
tukulani njira zofalitsila mauthenga zodalilika
agriculture
agriculture document
en2748
Use low planting densities
bzalani mbewu zochepa pa malo
agriculture
agriculture document
en2749
Reduce deforestation and forest degradation
zimachepetsa kudula mitengo mwachisawawa ndi kuononga mkhalango
agriculture
agriculture document
en2750
Convert land from non-forest to forest land use
sinthani malo omwe palibe mitengo ndikubzalapo mitengo
agriculture
agriculture document
en2751
Replant suitable aquatic plants in the aquaculture areas.
bzalaninso mbewu za mmadzi zabwino ku malo a ulimi wa nsomba
agriculture
agriculture document
en2752
Long lactation period
zimatulutsa mkaka kwa nthawi yaitali
agriculture
agriculture document
en2753
Withstand diseases better than exotic breeds
zimapilira ku matenda kusiyana ndizachikunja
agriculture
agriculture document
en2754
Higher growth rate and live weight
zimakula komanso nyama yake ilemela kwambiri
agriculture
agriculture document
en2755
The farmer is at liberty to choose semen from the bull preferred
mlimi ali mdi ufulu osankha umuna wa ng'ombe yomwe wafuna
agriculture
agriculture document
en2756
Requires well trained personnel in AI.
zimafunika akatswiri odziwa za tekinilloje
agriculture
agriculture document
en2757
Farmer should have knowledge in detecting heat.
mlimi akuyenera kukhala ndi nzeru zoziwira pamene ng'ombe ili mu nyengo yotentha
agriculture
agriculture document
en2758
Farmers should always record the subsequent expected date/dates of heat.
mlimi akuyenra kusunga masiku amane ng'ombe ingakhale itayamba kutentha
agriculture
agriculture document
en2759
Gestation period for cattle is 280 days (nine months)
masiku amene ng'ombe imakahala ndi bere ndi 280 (miyezi isanu ndi inayi)
agriculture
agriculture document
en2760
Fast and health growth of the fetus
kukula ndi thanzi la mwana osabadwa
agriculture
agriculture document
en2761
The cow is restless.
ng'ombe imasowa mtendere
agriculture
agriculture document
en2762
Two days before calving the udder swells if the teats are squeezed milk would come out
masiku awiri isanabereke, bere la ng'ombe limatupa ndipo mawereakae akafinyidwa mkaka umatuluka
agriculture
agriculture document
en2763
Birth weight should be recorded.
lembani ndi kusunga kulemela kwa ng'ombe yobadwa kumene
agriculture
agriculture document
en2764
Highly nutritious and contain anti-bodies
ndiyopasa thanzi kwambiri komanso imakhala ndi asilikali omenya nkhondo nthupi
agriculture
agriculture document
en2765
The calf should fully be allowed to suckle first milk produced (known as colostrum) for the first 4 days
kamwna aka ng'ombe kakuyenra kuloledwa kuyamwa mkaka oyambirira wa mmawere omwe umatuluka masiku anayi oyambilira
agriculture
agriculture document
en2766
If the calf fails to properly suckle, it should be bottle fed
ngati mwana wa ng'ommbe akulephera kukama wbino mkaka, akuyenera kumwetsedwa mkaka wa m'botolo
agriculture
agriculture document
en2767
If the dam dies before the calf has received colostrum, colostrum should be acquired and given to the calf especially where another cow is available.
ngati ng'ombe yayikazi yafa mwana asanakame mkaka oyambilila, mkakawu ukuyenera kukamidwa ndikumwetsedwa kwa kamwana ka ng'ombe ngati pali ng'ombe ina
agriculture
agriculture document
en2768
After 3 days the calf can be kept separate from the dam and artificially fed
pakatha masiku atatu mwana wa ng'ombe akhonza kusiyanisidwa nd ng'ombe yayikazi ndikumadyetsedwa
agriculture
agriculture document
en2769
The calf should by then be slowly introduced to roughages and be adjusted to appetite
nthawi imeneyo kamwana ka ng'ombe kakuyenela kuyambitsidwa kudya zolimbitsa
agriculture
agriculture document
en2770
At 12 weeks of age, the calf should be eating sufficient roughages and madeya in order to harden them in preparation to weaning.
kakakwanitsa masabata 12, kamwan aka ng'ombe kakhonza kuyamba kupatsidwa zkaudya zolimba ndi madeya cholinga zipilile pamene zikukonsekera kusiya kuyamwa
agriculture
agriculture document
en2771
The animal should be dewormed and dipped accordingly
nyamazi zipatsidwe mankhwal a nyongolotso komanso kusamba mu madzi a mankhwala
agriculture
agriculture document
en2772
wearners stage
nyengo yosiyisa kuyamwisa
agriculture
agriculture document
en2773
Provide a feed trough.
perekani modyera
agriculture
agriculture document
en2774
The crush is used for restraining the animal during treatments, spraying and other management procedures.
chipangizocho chimathandiza kukhala malo amodzi pamenezikulandila chithandizo, mankhwala ofaila ndi chisamaliro china mundondomeko
agriculture
agriculture document
en2775
The floor should be made of rough concrete cement if possible or burnt bricks
pansi pakuyenera pakhale pozilidwa ndi simenti ngati kuli kotheka kapena pakahle pa njewra zootcha
agriculture
agriculture document
en2776
The khola should be built on well-drained ground and floor to be at a slope to allow drainage
khola limagwidwe pa nthawi yolowa bwino madzi komanso likhale lopendama kuti madzi aziyenda bwino
agriculture
agriculture document
en2777
Drains to be made around the khola.
ngalande zikumbidwe kuzungulira khola
agriculture
agriculture document
en2778
Bedding should be clean, comfortable especially where the cow sleeps and/or can rest.
zogonela zokhale zoyera, makamaka pamene ng'ombe zimangona kapena kupumilapo
agriculture
agriculture document
en2779
A Dairy animal requires good nutrition for maintenance, growth, production and reproduction
nyama ya mkaka imayenera ikhale yathanzi.
agriculture
agriculture document
en2780
Provision of enough and sufficient quantity and quality roughages is the basis for high milk production.
kupereka zakudya zokwanira komanso zabwino ndi nsanamilo wa ulimi wa mkaka wochuluka
agriculture
agriculture document
en2781
Farmers can also buy commercially produced concentrates such as calf meal and dairy mash.
alimi akhonza kugula zakudya zopangidwa kale ngati zakudya za mwana wa ng'ombe komanso zakudya za mkaka
agriculture
agriculture document
en2782
For a lactating cow the rule of thumb is 5 litres of water for each litre of milk produced
kwa ng'ombe ya mkaka lamulo kale ndilokuti lipatsidwe ma lita 5 a madzi pa 1 lita iliyonse ya mkaka omwe wakamidwa
agriculture
agriculture document
en2783
Animals with high productivity need mineral supplementation.
nyama zimene zimaswana kwabiri zimafunika zakudya zoonjezera
agriculture
agriculture document
en2784
At six months, a heifer can be raised on pastures as long as it is good quality pasture.
pa miyezi isanu ndi umodzi, ng'ombe ikhonza kuwetedwa ku msipe pokhapokha ngati msipu wake ndi wabwino
agriculture
agriculture document
en2785
2 months before calving the cow/heifer should be steamed up
miyezi iwiri isanabereke mwana ng'ombe iyenera kutenthedwa
agriculture
agriculture document
en2786
During the first three days feed cows moderate amounts of dairy mash or concentrates plus high quality roughages adlibitum.
masiku atatu oyambilila ipatseni ng'ombe zakudya za mkaka kapena zolimbitsa thupi ngati adlibitum
agriculture
agriculture document
en2787
Plenty of cool clean drinking water should be provided all the time.
madzi ozozila okumwa amabiri akuyenera kuperekedwa nthawi zonse
agriculture
agriculture document
en2788
If a dry cow is in good condition it can maintain its health on good quality forage only
mwadzi aukhondo okumwa akuyenera kuperekedwa nthawi zonse
agriculture
agriculture document
en2789
Again rinse with cold clean water
kachikenanso tsukani ndi madzi ozizila oyera
agriculture
agriculture document
en2790
Ensure that utensils are thoroughly scrubbed with a hot detergent solution.
onetsetsani kuti zipangizo ndizotsukidwa bwino ndi madzi otentha
agriculture
agriculture document
en2791
Deliver the milk promptly to the milk bulking group.
kaperekeni mkaka ku gulu osonkhetsa mkaka
agriculture
agriculture document
en2792
Keep the milk as cool as possible
onesetsani kuti mkaka ukumakhala ozizila
agriculture
agriculture document
en2793
Those relating to production performance of the dairy cows.
zokhuza kasamalidwe ka ng'ombe za mkaka
agriculture
agriculture document
en2794
All farmers involved in dairy production are grouped into Bulking Groups.
alimi onse opanga ulimi wa mkaka amaikidwa mmagulu osokhetsa mkaka pamodzi
agriculture
agriculture document
en2795
The milk is tested and cooled at the centre.
mkaka umayezedwa ndikuzizilitsidwa ku likulu
agriculture
agriculture document
en2796
By bulking the milk farmers are able to sell the milk to a processor; they also bargain as a group and can buy inputs in bulk at a reduced price.
posonkhanitsa mkaka pamodzi, ali amatha kugulitsa kwa ogaya mkaka, amathanso kunenelela mitengo ngati gulu ndikugula zipangizo zochuluka pa mtengo otsika
agriculture
agriculture document
en2797
Develop program to prevent the spread of bacteria at milking time
tukulani mchitidwe opewa kafalidwe ka tizilombo nthawi yokama mkaka
agriculture
agriculture document
en2798
Give 2.5mg/kg into muscle
ibayeni 2.5mg/kg mu mnofu
agriculture
agriculture document
en2799
Sickness lasts for about 1 week; the animal dies or slowly recovers.
matenda amakhala mpakana sabata imodzi; nyama imafa kapena kuchila pang'onopang'ono
agriculture
agriculture document
en2800
It is best to vaccinate calves.
ndikabwino kupereka katemera kwa ng'ombe
agriculture
agriculture document
en2801
Heartwater can affect cattle, sheep and goats.
madzi a mu mtima amakhudza ng'ombe, nkhosa ndi mbuzi
agriculture
agriculture document