sent_id
stringlengths
3
7
english
stringlengths
3
1.06k
chichewa
stringlengths
4
3.03k
topic
stringclasses
8 values
source
stringclasses
17 values
en2902
During brooding period the chicks are given starter marsh.
nthawi yofungatira ana, anapiye amapatsidwa zakudya zoyambilira zokulitsa
agriculture
agriculture document
en2903
Chicks should be placed in the brooder as soon as they arrive.
anapiye akuyenera ayikidwe mu khola lotenthera akangofika
agriculture
agriculture document
en2904
The litter works as an insulator and help absorb moisture from droppings
zinyalala zoyika pansi zimagwira ntchito ngati chotenthetsera ndi kuthandiza kuyamwa chinyontho chochokela ku zitosi za nkhuku
agriculture
agriculture document
en2905
Deep litter rearing of chicks is by far the most prevalent
makola a zinyalala zakuya ndi njira yotchuka kwambiri yowetela nkhuku
agriculture
agriculture document
en2906
A farmer needs to develop a business plan before engaging into egg production enterprise.
mlimi akuyenera kusanja pulani asanayambe malonda ogulitsa mazira
agriculture
agriculture document
en2907
On average water requirement from day old to slaughter age is about 12 litres/chicken
mongoyerekeza madzi amene amafunikila kuyambila tsiku loyamba mpakana tsiku lophedwwa ndi ma lita 12 pa nkhuku iliyonse
agriculture
agriculture document
en2908
Fresh and clean water should be offered daily
madzi oyenera akuyenra kuperekedwa tsiku lililonse
agriculture
agriculture document
en2909
Growing birds have different nutritional requirements throughout the growing period
pamene mbalame zikukula zimakhala ndi zosowekera zosiyanasiyana pa thanzi lawo pa nyengo yomwe zikukula
agriculture
agriculture document
en2910
The feeding space can be determined by using a trough with 40cm diameter for every 30 birds
malo odyera angayezedwe pogwiritsa ntchito malo odyera otambalala 40cm pa mbalame makumi atatu alisonse
agriculture
agriculture document
en2911
On average feed intake for broilers from day old to slaughter age of 6 – 8 weeks is about 4kg/bird
chikatikati cha chakudya chimene nkhuku ya nyama imayenera kudya kuyambila tsiku loyamba mpaka tsiku lophedwa pakati pa masabata asanu ndi limodzi mpaka asanu ndi atatu ndi 4kg pa nkhuku iliyonse
agriculture
agriculture document
en2912
Controlling litter moisture is the most important step in avoiding ammonia
kuthana ndi chinyontho mu khola ndikofunika kwambiri chifukwa kumathandiza kupewa mpweya wa ammonia
agriculture
agriculture document
en2913
Too dry and dusty litter causes dehydration of young chicks, respiratory diseases and increases condemnations.
zinyalala zouma komanso zafumbi kwambiri zimayambitsa kusowa kwa madzi kmthupi mwa anapiye, matenda ammapapo ndi kuchulukitsa anapiye akufa
agriculture
agriculture document
en2914
A cow should be bred again around 60 days
ng'ombe ikuyenera kukwatitsidwanso pakatha masiku 60
agriculture
agriculture document
en2915
Protect the calf from predators.
kuteteza mwana wa ng'ombe ku zilombo
agriculture
agriculture document
en2916
Overstocking will restrict movement causing leg problems, bruising and death
kuchulutsa ziweto mkhola kumakanikisa mayendedwe omwe amayambisa mavuto a miyendo, kusupuka komanso kufa
agriculture
agriculture document
en2917
Stocking density depending on the breed
kuchulukwa kwa ziweto nkhola kumatengela ndi mtundu wake
agriculture
agriculture document
en2918
20 to 25 chicks/m for day old chicks
anapiye 20 mpaka 25 pa mita kwa nkhuku za tsiku limodzi
agriculture
agriculture document
en2919
10 to 12 chicks/m for 21 to 25 day old chicks
anapiye 10 mpaka 12 pa mita iliyonse za nkhuku za masiku 21 mpka 25
agriculture
agriculture document
en2920
Goat and sheep farmers need to know age of their animals in order make informed decisions of breeding stock selection
alimi a mbuzi ndi nkhosa akuyenera kuziwa zaka za ziweto zawo ndi cholinga chokuti azipanga ziganizo zabwino pamene akusanga ziweto zobeleka
agriculture
agriculture document
en2921
It utilizes natural vegetation at no cost
zimagwiritsa ntchito zomela mwachilengegwe opanda kulowetsa ndalama
agriculture
agriculture document
en2922
Sufficient time for animals to select their preferred herbage.
nthawi yokwanila kuti nyma zisankhe zakudya zimene zikuufuna
agriculture
agriculture document
en2923
Nutritional satisfaction depends on quality and density of fodder, Nutritive value change with season.
kukhutila ndi thanzi kumatenegla ndi kuchuluka kwa zakudya, thanzi limasintha malingana ndi nyengo
agriculture
agriculture document
en2924
Animals damage field crops and household items.
nyama zimawononga mbewu zakumunda ngakhaleso zinthu zapakhomo
agriculture
agriculture document
en2925
Animals are subjected to theft, predation and loss
nyama zimatha kubedwa, kudyedwa ndi nyama zina ndi kusowa
agriculture
agriculture document
en2926
Overgrazing is controlled
kumachepetsa kudyetsa ziweto kwmabiri
agriculture
agriculture document
en2927
Sick animals can be easily identified
nyama zomwe zikudwala ndizosavuta kuzizindikila
agriculture
agriculture document
en2928
People handling infected animals should wear protective gloves at all times.
anthu amene akuthandiza nymama zomwe zili ndi matenda avale ma gulovo ozitetezela nthawi zonse
agriculture
agriculture document
en2929
Pneumonia is common in later stages.
chibayo chimavuta pamene zikukula
agriculture
agriculture document
en2930
One animal cannot catch heart water directly from another.
ziweto sizingapatsilane nthenda ya heart water
agriculture
agriculture document
en2931
Animals can be run over by vehicles as they cross roads
nyama zimathanso kugundidwa ndi magalimoto pamene zikuwoloka pa nseu
agriculture
agriculture document
en2932
If chicks have been transported for a long distance and period, provide them with water for the first 2-3 hours prior to providing them feed.
ngati mukusamusa nkhuku kupita dera lakutali, zipatseni madzi okumwa pakatha ma ola awiri kapena atatu musanazipatse chakudya
agriculture
agriculture document
en2933
To boost the chicks, add vitamin supplement to drinking water for the first 3 days
kuti nkhuku zikule, zipateseni ma vitamini m'madzi masiku atatu oyambilira
agriculture
agriculture document
en2934
The most important requirement is that they are provided with a suitable environment and receive the proper diet
chinthu chofunikila kwambiri ndichowonetsetsa kuti zikukhala malo abwino komanso zikudya zakudya zabwino
agriculture
agriculture document
en2935
The house can be constructed using bricks or earth or planks for the walls depending on prevailing situation.
nyumba ikhonza kumangidwa ndi njewra, kuphomedwa ndi dothi kapena matabwa mmakoma malinga ndi nyengo zimene zilipo
agriculture
agriculture document
en2936
There is no limit in the length of the house as it depends upon the number of chickens to be kept
kulibe mlingo weniweni wa kukula kwa nyumba pakuti zimatengera ndi chiwerengero cha nkhuku zimene muzisunga
agriculture
agriculture document
en2937
The width of a deep litter open sided house should not be more than 9 meters.
mulifupi wa khola usakhale opyolera ma mita 9
agriculture
agriculture document
en2938
The height should be about 3 meters
nyumba italike kupita mwamba mita atatu
agriculture
agriculture document
en2939
Preparation for arrival of chicks
zoyenera kuchita pokonzekela kubwera kwa anapiye
agriculture
agriculture document
en2940
Birds that are growing very fat.
nkhuku zimene zikunenepa kwmabiri
agriculture
agriculture document
en2941
Hens that have dry and scaly cloaca
thazi amene ali ndi chinyomphilo chouma
agriculture
agriculture document
en2942
Collect eggs frequently (at least 3 times a day)
kumakolola mazira pafupipafupi (katatu pa tsiku)
agriculture
agriculture document
en2943
Handle the eggs carefully to avoid breakages
samalani mazira moyenera popewa kusweka
agriculture
agriculture document
en2944
Keep the eggs cool and at right humidity immediately after collecting them
sungani mazira pa malo ozizira komanso achinyezi choyenera mukangotha kutolera
agriculture
agriculture document
en2945
Keep eggs away from strong scented substances
sungani mazira patali ndi zinthu za fungo
agriculture
agriculture document
en2946
Pack the eggs in clean packing materials
longezani mazira oyera mu zipangaizo zolongezela
agriculture
agriculture document
en2947
Pack clean eggs separately from dirty ones
longezani mazira abwino ndi akuda mosiyana
agriculture
agriculture document
en2948
If there is premium for large eggs then the eggs will need to be graded
ngati pali mwai wa mazira akuluakulu pakufunika kusankha mazira
agriculture
agriculture document
en2949
The layers are left in lay for 52 weeks after which it might no longer be economical in terms of costs and returns.
nkhuku za mazira zimasungidwa masabata 52 zikuyikira mazira ndipo pambuyo pake sidzingabweretse phindu lokwanira
agriculture
agriculture document
en2950
At that stage the hens are sold for meat
pa nthawi imeneyo zimagulitsidwa ngati nyama
agriculture
agriculture document
en2951
It is advisable that when they are 35 weeks old or earlier the farmer should start raising a replacement flock which shall start laying just when the old flock is being disposed of
zikafika masabata 35 alimi amalangizidwa kuti pa nthawi imeneyo ayambe kusunga nkhuku zina za mazira ndi cholinga chakuti zizidzabweretsa phindu pamene zina zikugulitsidwa
agriculture
agriculture document
en2952
The disease usually affects birds between 3 and 8 weeks of age, occasionally older birds suffer.
nthendayi imagwira nkhuku za masabata atatu ndi asanu ndi atatu, koma zomwe zimadwala kwambiri ndi zazikulu
agriculture
agriculture document
en2953
Depression, stops eating and may drink excessively.
kukhumudwa, kusiya kudya ndi kumwa madzi kwamabiri
agriculture
agriculture document
en2954
Blood in droppings,
magazi mu zitosi
agriculture
agriculture document
en2955
Some commercial feeds in Malawi contain a drug to control coccidiosis
zakudya za nkhuku zina zogula zimakhala kale ndi mankhwala a coccidiosis
agriculture
agriculture document
en2956
Do not vaccinate laying birds
osapereka katemela kwa nkhuku zoyikila
agriculture
agriculture document
en2957
If you have less than 1,000 birds it is possible to share the vaccine with a neighbour
ngati muli ndi nkhuku zosakwana 1000 mukhonza kuwagailako anzanu
agriculture
agriculture document
en2958
mortality often increases rapidly
chiwerengero cha nkhuku zakufa chimachuluka kwambiri
agriculture
agriculture document
en2959
All vaccines should be applied as recommended by the manufacturer.
katemera yense aperekedwe motsatila malangizo amene anapereka opanga katemera
agriculture
agriculture document
en2960
The following records should be kept; Number of live chickens sold
sungani kaundula wa zochitika pa ulimi wanu monga; nkhuku zomwe zagulitsidwa zamoyo
agriculture
agriculture document
en2961
Number of chickens slaughtered
nkhuku zomwe zaphedwa
agriculture
agriculture document
en2962
Number of chicks bought
anapiye omwe agulidwa
agriculture
agriculture document
en2963
Number of chickens used for home consumption
nkhuku zomwe zadyedwa pakhomo
agriculture
agriculture document
en2964
Water and feed intake
kamwedwe ka madzi ndi kadyedwe ka chakudya
agriculture
agriculture document
en2965
Number of chickens died
nkhuku zimene zafa
agriculture
agriculture document
en2966
Vaccinations and treatments offered
katemela ndi chithandizo chomwe chaperekedwa
agriculture
agriculture document
en2967
Rodents, wild birds, pets, and other animals that may be carriers of the bacteria must be excluded from poultry houses.
makoswe, mbalame zamtchire, ziweto zapakhomo ndi nyama zina zikhonza kukhala zosungila tizilombo toyambitsa matenda ndipo zikuyenera kukhala kutali ndi makola a nkhuku
agriculture
agriculture document
en2968
High milk production
zimatulutsa mkaka wachuluka
agriculture
agriculture document
en2969
They are docile and easy to handle
ndizomvera komanso zosavuta kusamala
agriculture
agriculture document
en2970
This is where a bull is used to mate with the cow/heifer.
apa ndi pamene ng'ombe yayimuna imagwiritsidwa ntchito kukwerana ndi ng'ombe yayikazi
agriculture
agriculture document
en2971
Sexually transmitted diseases are prevented
zimapewa matenda opatsilana pogonana
agriculture
agriculture document
en2972
Protect the calf from predators.
tetezani mwana wa ng'ombe ku zilombo zolusa
agriculture
agriculture document
en2973
The amount of water required at different physiological stages varies and therefore provide water as much as the animal takes (80 to 100 litres).
mlingo wa madzi wofunikira panthawi zosiyanasiyana pamakulidwe kamasiyana ndipo nkoyenera kupeleka madzi mmene nyamazo zingafunire (80 kufika 100 litres)
agriculture
agriculture document
en2974
Use weigh bands or scales to weigh calves.
gwiritsani ntchito malamba kapena masikelo oyezela kulemela kwa ana ng'ombe
agriculture
agriculture document
en2975
Animal goes off food, milk yield falls, it has a mild FEVER.
chiweto chimasiya kudya, mkaka umatuluka ochepa, imatenthaso thupi
agriculture
agriculture document
en2976
Ensure that utensils are thoroughly scrubbed with a hot detergent solution
onetsetsani kuti ziwiya zatsukidwa bwino ndi madzi asopo otentha
agriculture
agriculture document
en2977
After thorough cleaning, the utensils should be put inverted on the drying rack in the direct sunlight.
mukamaliza kutsuka, ziwiya mudziike chogadamitsa pa thandala padzuwa
agriculture
agriculture document
en2978
It is absolutely necessary to filter the milk
ndikofunila kusefa mkaka
agriculture
agriculture document
en2979
The cloths used for this purpose should be washed with soap after each use.
ka nsalu kamene mutagwiritse ntchito kakuyenera kuchapidwa ndi sopo mukamaliza kugwiritsa ntchito
agriculture
agriculture document
en2980
Animals may easily die due to too much fluid loss from the body
nyama zimatha kufa msanga chifukwa chotaya madzi nthupi
agriculture
agriculture document
en2981
Ensure that a calf consumes adequate colostrum and that it suckles all the time for energy and nutrients.
onetsetsani kuti kamwana ka ng'ombe kayamwa mkaka woyambilira wokwanira ndipo kakuyamwa nthawi zonse kuti kadzikhala ndi mphamvu komanso michere yokwanira
agriculture
agriculture document
en2982
Becomes thin and constipated
imawonda ndi kudzimbidwa
agriculture
agriculture document
en2983
By bulking the milk farmers are able to sell the milk to a processor;
alimi amakwanitsa kugulitsa mkaka kwa ogaya mkaka akasokhetsa mkaka pamodzi
agriculture
agriculture document
en2984
Members for a bulking group are supposed to come from within eight kilometers radius from the cooling center.
alimi a gulu lowonkhetsa mkaka amayenera akhale ochokela dera losapitilila makilomita 8 kuchokela pa malo osiyila mkaka
agriculture
agriculture document
en2985
The cow should be health and clean
ng'ombe ikhale yathanzi komanso ya unkhondo
agriculture
agriculture document
en2986
Milk starts to lose its quality as soon as it has been milked and this can be minimized through the use of clean utensils
mkaka ukangokamidwa umayamba kuonongeka ndipo mukhonza kuchepetsa izi pogwiritsa ntchito zipangizo zotsukidwa bwino
agriculture
agriculture document
en2987
Do not mix the milk milked in the morning and that was milked in the afternoon.
osaphatikiza mkaka omwe wakamidwa mamawa ndi mkaka omwe wakamidwa masana
agriculture
agriculture document
en2988
Dentition is used to know the age of an animal
kuona mano kumathandiza kudziwa msinkhu wa nyama
agriculture
agriculture document
en2989
Easy to collect manure
kosavuta kotolela manyowa
agriculture
agriculture document
en2990
Reduces risk of predation and theft
zimachepetsa kudyedwa ndi kubedwa
agriculture
agriculture document
en2991
Disease prevention and control is an important aspect in goats and sheep production, therefore farmers must know the clinical signs of diseases for early detection and reporting to relevant authorities.
kupewa ndi kuthana ndi matenda ndikofunika pa ulimi wa mbuzi ndi nkhosa, kotero alimi akuyenera kudziwa zizindikilo zosiyanasiyana za matenda mwachangu ndikuwawudza adindo oyenera
agriculture
agriculture document
en2992
The eyes may also become infected, causing eyelids to mat together with discharge.
maso akhonza kugwidwa ndi matenda, ndikuyambitsa kuti zikope zizimatana kwia zikutulutsa manthongo
agriculture
agriculture document
en2993
Drench the whole flock (excluding sucking animals which are not yet grazing)
bidzani ziweto zonse (kupatula zimene zimene zikuyamba zomwe sizinayambekusaka chakudya)
agriculture
agriculture document
en2994
They transmit important human diseases
zimafalitsa matenda oopsa kwa anthu
agriculture
agriculture document
en2995
This time around, Weah is quite aware that his popularity has dwindled and that he has no chance in this election
Padakali pano, Weah akuzindikira kuti chikoka chake chatsika ndipo alibe mwayi wosankhidwanso
politics
Online sources
en2996
Incumbent President George Weah, a decorated former football star, is seeking reelection for a second six-year term after a tumultuous first tenure tainted by corruption scandals and allegations of mismanagement
Mtsogoleri wolamula Geaorge Weah, yemwe ankasewera mpira wa miyendo mwachikoka, akufunanso kusankhidwa pampando kachiwiri kuti alamule zaka zina zisanu ndi chimodzi potsatira kulamula kwake koyamba komwe kwayipa ndi katangale komanso kusayendetsa bwino zinthu
politics
Online sources
en2997
More than 60% of Liberia’s 5.4 million people are below the age of 25, but unemployment is widespread among the country’s youth, some of whom were former child soldiers in the civil war
Anthu 60 pa 100 aliwonse mwa anthu 5,400,000 mdziko la Liberia sanakwanitse zaka makumi awiri ndi zisanu (25), koma vuto lakusowa kwa ntchito ndilalikulu pakati pa achinyamata, omwe ena mwa iwo anali asirikali pamene anali ana munthawi yanhkondo yapachiweniweni
politics
Online sources
en2998
Tensions flared between supporters of the two parties ahead of the polls, Liberia’s police said . This led to a “loss of lives and the destruction of properties,” the country’s electoral commission stated
Kusamvana kunakula pakati pa otsatira zipani ziwirizi pokonzekera masankho, apolisi aku Liberia anatero. Izi zinadzetsa imfa komanso kuonongeka kwa katundu, oyendetsa chisankho anafotokoza
politics
Online sources
en2999
Liberians want a change. The youths on the street are telling me they made a mistake and want to correct the mistake. They are saying everywhere I go, ‘forgive us, we made a mistake,’” he said.
Mzika za dziko la Liberia zikufuna kusintha. Achinyamata omwe ndawapeza mmiseu andiuza kuti analakwitsa ndipo akufuna akonze kulakwitsako. Kulikonse komwe ndapita iwo akuti "tikhululukireni", tinalakwitsa, iye anatero
politics
Online sources
en3000
A spokesperson for the UN Human Rights Office in Liberia said at least two people died and 20 others were injured in the clashes
Mneneri wa nthambi yoona za ufulu wa anthu ya mgwirizano wa mayiko onse (United Nations) ku Liberia yanena kuti anthu awiri anafa pamene ena makumi awiri anavulala pakukangana komwe kunabuka
politics
Online sources
en3001
Supporters of both main parties have accused each other of instigating the violence. Videos circulating on social media depict scenes of chaos, with rival groups engaged in altercations and hurling objects at each other, sending shockwaves through the community
Otsatira zipani ziwiri zikuluzikulu akulozana zala poyambitsa zipolowe. Makanema omwe ali pamasmba a mchezo (social media) akuonetsa kubuka kwa zipwirikiti, pomwe magulu osamvana akumenyana, kuponyerana zinthu zomwe zadzetsa kukhumudwa mmadera osiyanasiyana
politics
Online sources