sent_id
stringlengths
3
7
english
stringlengths
3
1.06k
chichewa
stringlengths
4
3.03k
topic
stringclasses
8 values
source
stringclasses
17 values
en3502
The party is very supportive of improving voting rights as well as election accuracy and accessibility
Chipanichi chikuthandizira kwambiri kukonza ufulu wovota komanso kulondola kwa chisankho ndi kapezekedwe kakae
politics
Online/Wikipedia
en3503
They support extensions of voting time, including making election day a holiday. They support reforming the electoral system to eliminate gerrymandering, abolishing the electoral college, as well as passing comprehensive campaign finance reform
Amathandizira kuwonjezera nthawi yovota, kuphatikiza kupanga tsiku lachisankho kukhala tchuthi. Amathandizira kukonzanso dongosolo la zisankho kuti athetse nkhanza, kuthetseratu koleji ya zisankho, komanso kupititsa patsogolo kusintha kaperekedwe ka chuma chothandizira kukopa anthu.
politics
Online/Wikipedia
en3504
The present platform states that all women should have access to birth control and supports public funding of contraception for poor women
Ndondomekoyi ikuti amayi onse akuyenera kukhala ndi mwayi opeza njra zakulera komanso kuthandizirakapezekedwe ka njira za kulera kwa amayi osauka
politics
Online/Wikipedia
en3505
As a matter of the right to privacy and of gender equality, many Democrats believe all women should have the ability to choose to abort without governmental interference
Pankhani ya ufulu wachinsinsi komanso kufanana pakati pa amuna ndi akazi, ma Democrat ambiri amakhulupirira kuti azimayi onse ayenera kusankha kuchotsa mimba popanda kusokonezedwa ndi boma
politics
Online/Wikipedia
en3506
They believe that each woman, conferring with her conscience, has the right to choose for herself whether abortion is morally correct
Amakhulupirira kuti mkazi aliyense, mogwirizana ndi chikumbumtima chake, ali ndi ufulu wodzisankhira yekha ngati kuchotsa mimba kuli kolondola kapena ayi
politics
Online/Wikipedia
en3507
Support for same-sex marriage has steadily increased among the general public, including voters in both major parties, since the start of the 21st century
Kuvomereza maukwati a amuna kapena akazi okhaokha kwawonjezeka mochuluka pakati pa anthu onse, kuphatikizapo ovota m'magulu akuluakulu onse, kuyambira chiyambi cha zaka za mmazana makumi awiri ndi chimodzi
politics
Online/Wikipedia
en3508
On May 9, 2012, Barack Obama became the first sitting president to say he supports same-sex marriage
Pa May 9, chaka cha 2012, Barack Obama adakhala mtsogoleri woyamba kunena kuti amavomereza maukwati a amuna kapena akazi okhaokha
politics
Online/Wikipedia
en3509
Many Democrats are opposed to the use of torture against individuals apprehended and held prisoner by the United States military and hold that categorizing such prisoners as unlawful combatants does not release the United States from its obligations under the Geneva Conventions
Ma Democrat ambiri amatsutsana ndi kugwiritsa ntchito kuzunza anthu omwe amangidwa ndikumangidwa ndi asirikali aku United States ndipo amati kugawa akaidi ngati omenyera nkhondo osaloledwa sikumasula dziko la United States kuudindo wake pamisonkhano ya Geneva
politics
Online/Wikipedia
en3510
Democrats contend that torture is inhumane, damages the United States' moral standing in the world, and produces questionable results. Democrats are largely against waterboarding
Ma Democrats amatsutsa kuti kuzunzidwa ndi nkhanza, kumawononga chikhalidwe cha United States padziko lapansi, ndipo kumabweretsa zotsatira zokayikitsa. Ma Democrat amatsutsana kwambiri ndi ukamberembere
politics
Online/Wikipedia
en3511
The United States is doing too much in other countries around the world, and it is time to do less around the world and focus more on our own problems here at home
Dziko la United States likuchita zochuluka kwambiri m'maiko ena padziko lonse lapansi, ndipo nthawi yakwana yoti tichite zochepa padziko lonse lapansi ndikungoyang'ana kwambiri mavuto athu pano kwathu
politics
Online/Wikipedia
en3512
The United States must continue to push forward to promote democracy and freedom in other countries worldwide because these efforts make our own country more secure
Dziko la United States liyenera kupitiliza kulimbikitsa utsogoleri wa mphamvu kwaanthu ndi ufulu m'maiko ena padziko lonse lapansi chifukwa izi zimapangitsa dziko lathu kukhala lotetezeka
politics
Online/Wikipedia
en3513
As a candidate for president, I made clear my support for a timeline of 16 months to carry out this drawdown, while pledging to consult closely with our military commanders upon taking office to ensure that we preserve the gains we've made and protect our troops
Monga opikisana nawo pa mpando wa mtsogoleri wa dziko, ndidafotokoza momveka bwino kuti ndikuchirikiza kwa miyezi khumi ndiisanu ndiumodzi kuti tichite izi, ndikulonjeza kuti tidzakambirana ndi akuluakulu athu ankhondo potenga udindowu kuti tiwonetsetse kuti tikusunga zomwe tapeza ndikuteteza asilikali athu.
politics
Online/Wikipedia
en3514
Those consultations are now complete, and I have chosen a timeline that will remove our combat brigades over the next 18 months
Kukambirana kumeneku kwatha, ndipo ndasankha nthawi yomwe idzachotse magulu ankhondo athu m'miyezi khumi ndiitatu ikubwerayi
politics
Online/Wikipedia
en3515
He stated that both the speed of withdrawal and the number of troops left over would be "entirely conditions-based
Ananenanso kuti liwiro lochoka komanso kuchuluka kwa asirikali omwe atsala zikhala zotengera mmene zinthu zikhalire
politics
Online/Wikipedia
en3516
Support for the war among the American people diminished over time. Many Democrats changed their opinion over the course of the war, coming to oppose continuation of the conflict
Thandizo la nkhondo pakati pa anthu aku America linachepa pakapita nthawi. Ma Democrat ambiri adasintha malingaliro awo panthawi yankhondo, akubwera kudzatsutsa kupitiriza kwa mkangano
politics
Online/Wikipedia
en3517
Recently, the party has significantly increased support among affluent, college-educated whites and dramatically lost support among voters with lower incomes or lacking a college degree, particularly from Asian Americans
Posachedwapa, chipanichi chawonjezera chithandizo pakati pa azungu olemera, ophunzira ku sukulu zaukachenjede komanso kutaya chithandizo pakati pa ovota omwe amapeza ndalama zochepa kapena opanda digiri ya koleji, makamaka ochokera kwa Mzika za ku America-Asia
politics
Online/Wikipedia
en3518
Historically, the party has represented farmers, laborers, and religious and ethnic minorities as it has opposed unregulated business and finance and favored progressive income taxes
M'mbiri, chipanichi chidayimilira alimi, ogwira ntchito, azipembedzo ndi mafuko ang'onoang'ono chifukwa chimatsutsa mabizinesi osayendetsedwa ndi ndalama komanso kukondera misonkho yopita patsogolo
politics
Online/Wikipedia
en3519
A large majority of liberals favor moving toward universal health care, with many supporting an eventual gradual transition to a single-payer system in particular
Ambiri omasuka amakonda kupita ku chisamaliro chaumoyo wapadziko lonse, ndipo ambiri amathandizira kusintha kwapang'onopang'ono kunjira yolipira m'modzi makamaka
politics
Online/Wikipedia
en3520
A majority also favor diplomacy over military action; stem cell research, same-sex marriage, stricter gun control, environmental protection laws, as well as the preservation of abortion rights
Ambiri amakondanso zokambirana m'malo mwa nkhondo; kafukufuku wa maselo a tsinde, maukwati a amuna kapena akazi okhaokha, kukhwimitsa mfuti, malamulo oteteza chilengedwe, komanso kusunga ufulu wochotsa mimba
politics
Online/Wikipedia
en3521
Immigration and cultural diversity are deemed positive as liberals favor cultural pluralism, a system in which immigrants retain their native culture in addition to adopting their new culture
Kusamuka komanso kusiyanasiyana kwa zikhalidwe kumawonedwa kukhala kwabwino popeza omasuka amakonda kusiyanasiyana kwa chikhalidwe, njira yomwe olowa m'mayiko ena amasunga chikhalidwe chawo komanso kutengera chikhalidwe chawo chatsopano
politics
Online/Wikipedia
en3522
Most liberals oppose increased military spending and the mixing of church and state. Recently, many have made combating economic inequality their top priority
Ambiri omasuka amatsutsa kuchuluka kwa ndalama zankhondo komanso kusakanikirana kwa mpingo ndi boma. Posachedwapa, ambiri aona kuti kulimbana ndi kusalingana pazachuma kukhala chinthu chofunika kwambiri
politics
Online/Wikipedia
en3523
The relationship between income, class, and partisan support has changed significantly in recent years
Ubale pakati pa ndalama, kalasi, ndi chithandizo chamagulu azachipani chasintha kwambiri m'zaka zaposachedwa
politics
Online/Wikipedia
en3524
Beginning in the 1980s to 1990s, there has been a significant decline in support for the Democratic Party among white working class voters
Kuyambira m'zaka za m'ma 1980 mpaka 1990, pakhala kuchepa kwakukulu kwa chithandizo cha Democratic Party pakati pa ovotera azungu
politics
Online/Wikipedia
en3525
Although the gender gap has varied over the years, women of all ages as a whole are more likely than men to identify as Democrats
Ngakhale kusiyana pakati pa amuna ndi akazi kwakhala kosiyana kwa zaka zambiri, amayi azaka zonse ali ndi mwayi wodziŵika kuti ndi a Democrats kuposa amuna
politics
Online/Wikipedia
en3526
White women are the only group of female voters who support Republican Party candidates for president. They have done so by a majority in all but 2 of the last 18 elections
Azimayi achizungu ndi gulu lokhalo la ovota achikazi omwe amathandizira ofuna kukhala mtsogoleri wa dziko wa chipani cha Republican. Achita izi ndi anthu ambiri kusiyapo 2 mwa zisankho 18 zapitazi
politics
Online/Wikipedia
en3527
Americans that identify as single, living with a domestic partner, divorced, separated, or widowed are more likely to vote Democratic in contrast to married Americans who split about equally between Democrats and Republicans
Pali chiyembekezo chachikulu kuti anthu aku America omwe amadziwika kuti ndi osakwatiwa, okhala ndi mnzawo wapakhomo, osudzulidwa, opatukana, kapena wamasiye adzavotera ma Democrat kusiyana ndi anthu apabanja aku America omwe amagawanika mofanana pakati pa ma Democrat ndi ma Republican
politics
Online/Wikipedia
en3528
However, there is a significant difference in fertility rates between the two related groups, liberals and conservatives, with liberals reproducing at a much lower rate than conservatives
Komabe, pali kusiyana kwakukulu kwa chiwerengero cha kuberekana pakati pa magulu awiri ogwirizana, omasuka ndi osunga malamulo, omwe ali omasuka akubereka pamlingo wocheperapo kusiyana ndi osunga malamulo
politics
Online/Wikipedia
en3529
Catholic Americans were once a stronghold for the Democratic Party, but in recent years they have become more divided between the two major parties
Akatolika ochokera ku dziko la America poyamba anali dera la mphamvu la chipani cha Democratic, koma m’zaka zaposachedwapa agaŵikana kwambiri pakati pa zipani zazikulu ziŵirizo
politics
Online/Wikipedia
en3530
All adult citizens were required to be party members. They had to carry "party cards" in their wallets at all times
Nzika zonse zachikulire zimafunikira kuti akhale mamembala achipani. Anayenera kunyamula 'makhadi achipani' m'matumba mwawo nthawi zonse.
politics
Online/Wikipedia
en3531
The party lost its monopoly on power in a 1993 referendum and was roundly defeated in the country's first free elections the next year
Chipanichi chidataya mphamvu zake pa chisankho chomwe chidachita mu 1993 ndipo chidagonja pazisankho zoyambirira zaulere mdziko muno chaka chamawa
politics
Online/Wikipedia
en3532
It remains a major force in Malawian politics. It is strongest in the central region, populated by ethnic Chewa and Nyanja people
Ndilo chilimbikitso chachikulu pa ndale za Malawi. Ndiwolimba kwambiri m’chigawo chapakati, komwe kumakhala A Chewa ndi a Nyanja
politics
Online/Wikipedia
en3533
The administration of F.W. de Klerk lifted the ban on the ANC in 1990, and its leaders were released from prison or allowed to return to South Africa and conduct peaceful political activities
Ulamuliro wa F.W. de Klerk unachotsa chiletso cha ANC mu 1990, ndipo atsogoleri ake adatulutsidwa m'ndende kapena kuloledwa kubwerera ku South Africa ndikuchita ndale zamtendere
politics
Online/Wikipedia
en3534
Nelson Mandela, the most important of the ANC’s leaders, succeeded Oliver Tambo as president in 1991
Nelson Mandela, nkulu wa atsogoleli wa ANC, anapambana a Oliver Tambo ngati mtsogoleri wa dziko mu 1991
politics
Online/Wikipedia
en3535
Mandela led the ANC in negotiations (1992–93) with the government over transition to a government elected by universal suffrage
Mandela adatsogolera ANC mu zokambirana (1992-93) ndi boma pa kusintha kwa boma losankhidwa ndi ufulu wa anthu onse
politics
Online/Wikipedia
en3536
In April 1994 the party swept to power in the country’s first such election, winning more than 60 percent of the vote for seats in the new National Assembly
Mu mwezi wa April 1994 chipanichi chidatenga mphamvu pachisankho choyamba choterechi, ndipo chidapeza mavoti opitilira 60 peresenti ya mipando mu nyumba yamalamulo
politics
Online/Wikipedia
en3537
Mandela, who headed a government of national unity, was inaugurated as South Africa’s first Black president on May 10, 1994
Mandela, yemwe adatsogolera boma la mgwirizano wa dziko, adakhazikitsidwa kukhala mtsogoleri wa dziko oyamba wakuda wa South Africa pa May 10, 1994
politics
Online/Wikipedia
en3538
After the withdrawal of the National Party from the government in 1996, the ANC entered into an alliance with its previous rival, the Inkatha Freedom Party, led by Mangosuthu Buthelezi
Chipani cha National chitatuluka m’boma m’chaka cha 1996, chipani cha ANC chinachita mgwirizano ndi chipani cha Inkatha Freedom chotsogoleredwa ndi Mangosuthu Buthelezi
politics
Online/Wikipedia
en3539
Mandela stepped down as ANC president in 1997, and in June 1999 his successor, Thabo Mbeki, became the second Black president of South Africa
Mandela adachoka ngati mtsogoleri wa dziko wa ANC mu 1997, ndipo mu June 1999 wolowa m'malo mwake, Thabo Mbeki, adakhala mtsogoleri wachikuda wa South Africa
politics
Online/Wikipedia
en3540
The party celebrated its 90th anniversary in 2002 and continued its domination of South African politics
Chipanichi chinachita chikondwerero cha zaka 90 chikhazikitsire mchaka cha 2002 ndipo chinapitirizabe kulamulira ndale ku South Africa
politics
Online/Wikipedia
en3541
Signs of dissent began to appear within the ANC leading up to the party’s 2007 national conference, where the next president of the ANC—and, most likely, the next president of the country—was to be selected
Zizindikiro za kusagwirizana zinayamba kuonekera mkati mwa chipani cha ANC pokonzekera msonkhano wa chipanichi mu 200, pomwe mtsogoleri wotsatira wa ANC—ndipo mwinanso mtsogoleri wotsatira wa dziko—anayenera kusankhidwa
politics
Online/Wikipedia
en3542
Although Mbeki was barred by South Africa’s constitution from serving a third term as president of the country, securing a third term as party president would have guaranteed him considerable influence in choosing the country’s next president in 2009
Ngakhale a Mbeki analetsedwa ndi malamulo a dziko la South Africa kuti akhale mtsogoleri wa dzikolo kwa nthawi yachitatu, kudzakhala mtsogolerio wa chipani chachitatu kukanamupatsa mphamvu zambiri posankha mtsogoleri wotsatira wa dzikolo mu 2009
politics
Online/Wikipedia
en3543
His bid for leadership of the party was challenged by Jacob Zuma, the former deputy president whom he had dismissed in 2005 amid charges of corruption; the next year Zuma also stood trial for an unrelated charge of rape
Kufuna kwake kukhala mtsogoleri wachipanichi kudatsutsidwa ndi Jacob Zuma, yemwe anali wachiwiri kwa mtsogoleri yemwe adamuchotsa mchaka cha 2005 pamilandu yakatangale; chaka chotsatiracho Zuma adazemngedwanso mlandu wokhudza kugwiririra
politics
Online/Wikipedia
en3544
He was acquitted of rape in May 2006, and the corruption charges were dropped later that year
Anatulutsidwa pamlandu wogwiririra mu May 2006, ndipo milandu ya katangale inathetsedwa chakumapeto kwa chaka chimenecho
politics
Online/Wikipedia
en3545
Despite repeated allegations of wrongdoing—which his supporters claimed were politically motivated—Zuma remained a popular figure within the ANC and, in what was one of the most contentious leadership battles in the party’s history, was selected over Mbeki in December 2007 to be party president
Ngakhale ankanena zolakwa zambiri zomwe omutsatira ake ankanena kuti zinali zokomera ndale, Zuma anakhalabe munthu wotchuka mu chipani cha ANC ndipo, mu umodzi mwa mikangano ya utsogoleri m'mbiri ya chipanichi, anasankhidwa pa Mbeki mu December 2007 kukhala mtsogoleri wachipani.
politics
Online/Wikipedia
en3546
The request for Mbeki’s resignation angered part of the ANC membership base, and several high-ranking ANC officials resigned from their government positions in protest
Pempho loti a Mbeki atule pansi udindo lidakwiyitsa mbali ina ya umembala wa chipani cha ANC, ndipo akuluakulu angapo achipani cha ANC adatula pansi udindo wawo m’boma potsutsa
politics
Online/Wikipedia
en3547
Another source of tension within the party was Zuma’s close ties to the South African Communist Party and to the Congress of South African Trade Unions
Chinanso chomwe chidayambitsa kusamvana mchipanichi ndi ubale wa Zuma ndi chipani cha South Africa Communist Party komanso Congress of South African Trade Unions
politics
Online/Wikipedia
en3548
Although both organizations had long been allies of the ANC, there was growing concern among many ANC members that those groups were exerting too much influence on the ANC under Zuma’s leadership
Ngakhale mabungwe onsewa adagwirizana kwa nthawi yayitali ndi chipani cha ANC, kuda nkhawa kudakulirakulira pakati pa mamembala ambiri a ANC kuti maguluwa akukakamiza kwambiri chipani cha ANC motsogozedwa ndi Zuma
politics
Online/Wikipedia
en3549
The discord in the ANC proved to be too great to overcome. High-ranking members and Mbeki supporters broke away from the ANC and established a new party, Congress of the People (COPE)
Mkangano mu ANC unakhala waukulu kwambiri kuti ugonjetse. Mamembala akuluakulu komanso otsatira a Mbeki adatuluka mu ANC ndikukhazikitsa chipani chatsopano cha Congress of the People (COPE)
politics
Online/Wikipedia
en3550
The new party, which pledged to reach out to minorities and women, was officially launched in December 2008 and attracted members from the ANC as well as other organizations
Chipani chatsopanochi, chomwe chidalonjeza kuti chidzafikira anthu ochepa komanso amayi, chidakhazikitsidwa mwalamulo mu December 2008 ndipo chidakopa mamembala a ANC komanso mabungwe ena
politics
Online/Wikipedia
en3551
Despite the challenge from COPE and other parties, the ANC was victorious in the 2009 general election, finishing far ahead of its competitors, with almost 66 percent of the national vote
Ngakhale zipani za COPE ndi zipani zina zidakumana nazo, chipani cha ANC chidapambana pachisankho cha 2009, ndikumaliza kuposa omwe adapikisana nawo, ndi pafupifupi 66 peresenti ya mavoti adziko lonse
politics
Online/Wikipedia
en3552
The party maintained control of all provinces except the Western Cape, which was won by the Democratic Alliance
Chipanichi chidapitirizabe kulamulira zigawo zonse kupatulapo Western Cape yomwe idapambana ndi Democratic Alliance
politics
Online/Wikipedia
en3553
Zuma, however, still appeared to have a majority of support. At the last minute he was challenged for the party presidency, but Zuma handily defeated him
Zuma, komabe, ankawoneka kuti ali ndi chithandizo chochuluka. Pomaliza adapikisana nawo pa utsogoleri wa chipani, koma Zuma adamugonjetsa
politics
Online/Wikipedia
en3554
In the 2014 elections the ANC’s status as the governing party was secured for another five years when the party won about 62 percent of the national vote
M’chisankho cha 2014 chipani cha ANC chinali ngati chipani cholamulira chinadziwika kwa zaka zina zisanu pamene chipanichi chinapambana pafupifupi 62 peresenti ya mavoti a dziko lonse
politics
Online/Wikipedia
en3555
At the provincial level it remained the dominant party in all provinces except the Western Cape
Kumaboma idakhalabe chipani chachikulu m'zigawo zonse kupatula Western Cape
politics
Online/Wikipedia
en3556
The success of the party came even though its membership base had seen erosion from dissatisfaction with the performance of the ANC-led government and by other parties gaining in popularity
Kuchita bwino kwa chipanichi kudadza ngakhale kuti mamembala ake adawoneka akukokoloka chifukwa chosakhutira ndi momwe boma lotsogozedwa ndi ANC komanso zipani zina zidatchuka
politics
Online/Wikipedia
en3557
The party’s loss of support was widely attributed to the electorate’s dissatisfaction with how the ANC-led governments at the municipal and national levels were handling the economy and delivery of services, as well as frustration with the persistent corruption and scandals associated with Zuma and the ANC
Kulephera kwachipanichi kudachitika chifukwa chakukhumudwa kwa ochita zisankho ndi momwe maboma otsogozedwa ndi ANC m'maboma ndi m'maboma ndi m'maboma akuyendetsa chuma ndi kupereka ntchito, komanso kukhumudwa ndi katangale ndi nkhani zabodza zomwe zimayenderana ndi Zuma ndi ANC.
politics
Online/Wikipedia
en3558
Another closely fought battle for the party’s presidency played out at the ANC’s national conference in December 2017, with the polarization of Zuma’s supporters and critics at the fore
Nkhondo ina yomwe idamenyedwa kwambiri yofuna kukhala mtsogoleri wachipani idachitika pamsonkhano waukulu wa chipani cha ANC mu December 2017, pomwe panali kusagwirizana kwa otsatira Zuma ndi otsutsa
politics
Online/Wikipedia
en3559
Both events increased the likelihood that the ANC would pressure Zuma to step down as president prior to the 2019 elections in order to stem the damage to the party from the allegations of scandal and corruption that had swirled around him for so long
Zochitika ziwirizi zidawonjezera mwayi woti chipani cha ANC chikakamize Zuma kuti atule pansi udindo wake ngati mtsogoleri wa dziko zisankho za 2019 zisanachitike kuti athetse kuwonongeka kwa chipanichi chifukwa cha nkhani zonyoza komanso zakatangale zomwe zakhala zikumuzungulira kwa nthawi yayitali
politics
Online/Wikipedia
en3560
In early 2018 ANC officials engaged in several meetings and negotiation sessions regarding Zuma’s remaining time as president
Kumayambiriro kwa chaka cha 2018 akuluakulu a ANC adachita misonkhano ingapo komanso zokambirana zokhuza nthawi yotsala ya Zuma kukhala mtsogoleri wa dziko
politics
Online/Wikipedia
en3561
The situation peaked on February 13, 2018, when the ANC announced that it had decided to recall Zuma from the presidency
Zinthu zidafika pachimake pa 13 February 2018, pomwe chipani cha ANC chidalengeza kuti chaganiza zochotsa Zuma pampando wamtsogoleri wa dziko
politics
Online/Wikipedia
en3562
The recall, however, did not legally compel Zuma to step down, so the party had to wait for him to offer his resignation
Koma kuchotsedwako sikunakakamize Zuma kuti atule pansi udindo wake, choncho chipanicho chinayenera kumudikirira kuti apereke udindo wake
politics
Online/Wikipedia
en3563
Zuma acquiesced, albeit somewhat defiantly, and offered his resignation the next day. He was succeeded as president of the country by Ramaphosa
A Zuma adavomera, ngakhale adachita mwano, ndipo adalonjeza kuti atule pansi udindo wake tsiku lotsatira. Adasankhidwa kukhala mtsogoleri wa dziko wa dziko ndi Ramaphosa
politics
Online/Wikipedia
en3564
On the national stage, it was the party’s worst showing to date, a sign of the continuing dissatisfaction with the ANC-led government
Pabwalo ladziko lonse, zidali zoyipitsitsa mchipanichi mpaka pano, zomwe zikuwonetsa kusakhutira ndi boma lotsogozedwa ndi ANC
politics
Online/Wikipedia
en3565
At the provincial level, the party was able to keep control of eight out of nine provinces it previously held, with the Western Cape once again going to the DA party
Pachigawo chachigawo chipanichi chidakwanitsa kulamulira zigawo zisanu ndi zitatu mwa zisanu ndi zinayi zomwe zidachita kale, ndipo Western Cape idapitanso ku chipani cha DA
politics
Online/Wikipedia
en3566
After participating in rebellions against governments in the Dominican Republic and Colombia, he planned the overthrow of Cuban president Fulgencio Batista, launching a failed attack on the Moncada Barracks in 1953
Atatenga nawo mbali poukira maboma ku Dominican Republic ndi Colombia, adakonzekera kugwetsa mtsogoleri wa dziko la Cuba, Fulgencio Batista, ndikuyambitsa zigawenga zomwe zidalephera ku Moncada Barracks mu 1953
politics
Online/Wikipedia
en3567
After a year's imprisonment, Castro travelled to Mexico where he formed a revolutionary group
Castro atakhala m'ndende kwa chaka chimodzi adapita ku Mexico komwe adayambitsa gulu losintha anthu
politics
Online/Wikipedia
en3568
After Batista's overthrow in 1959, Castro assumed military and political power as Cuba's prime minister
Batista atagonjetsedwa mu 1959, Castro adatenga mphamvu zankhondo ndi ndale ngati nduna yaikulu ya Cuba
politics
Online/Wikipedia
en3569
The United States came to oppose Castro's government and unsuccessfully attempted to remove him by assassination, economic embargo, and counter-revolution
Dziko la United States linabwera kudzatsutsa boma la Castro ndipo linalephera kumuchotsa mwa kumupha, kuletsa kuletsa chuma, komanso kutsutsa kusintha kwa boma
politics
Online/Wikipedia
en3570
Critics call him a dictator whose administration oversaw human rights abuses, the exodus of many Cubans, and the impoverishment of the country's economy
Otsutsa amamuuza wolamulira mnzake, yemwe akulamulira anthu ambiri, ndipo anali wochiritsika wa chuma cha dzikolo
politics
Online/Wikipedia
en3571
He had become financially successful by growing sugarcane. His mistress and later second wife; together they had seven children, among them Fidel
Iye anali ndi ndalama zambiri chifukwa cholima nzimbe. Mbuye wake ndipo kenako mkazi wachiwiri; pamodzi adali ndi ana asanu ndi awiri, mwa iwo Fidel
politics
Online/Wikipedia
en3572
At age six, Castro was sent to live with his teacher in Santiago before being baptized into the Roman Catholic Church at the age of eight
Ali ndi zaka zisanu ndi chimodzi, Castro anatumizidwa kukakhala ndi aphunzitsi ake ku Santiago asanabatizidwe mumpingo wa Katolika ali ndi zaka zisanu ndi zitatu
politics
Online/Wikipedia
en3573
Being baptized enabled Castro to attend the La Salle boarding school in Santiago, where he regularly misbehaved
Kubatizidwa kunathandiza Castro kupita kusukulu yogonera ku La Salle ku Santiago, kumene nthaŵi zonse anali kuchita zoipa
politics
Online/Wikipedia
en3574
Although Castro took an interest in history, geography, and debate at Belén, he did not excel academically, instead devoting much of his time to playing sports
Ngakhale Castro ankachita chidwi ndi mbiri yakale, malo, ndi kukangana ku Belén, sanachite bwino m’maphunziro, m’malo mwake ankathera nthawi yake yambiri akuchita masewera
politics
Online/Wikipedia
en3575
In 1945, Castro began studying law at the University of Havana. Admitting he was "politically illiterate", Castro became embroiled in student activism and the violent gangsterism culture within the university
Mu 1945, Castro anayamba kuphunzira zamalamulo ku Yunivesite ya Havana. Kuvomereza kuti anali wopanda ntchito ', Calro adalowa mu chinsinsi cha ophunzira ndi chipani chachiwawa cha zigawenga mkati mwa yunivesite
politics
Online/Wikipedia
en3576
Castro became critical of the corruption and violence of President Ramón Grau's government, delivering a public speech on the subject in November 1946 that received coverage on the front page of several newspapers
Castro adadzudzula katangale ndi ziwawa za boma la mtsogoleri wa dziko Ramón Grau, pokamba nkhani yapoyera pankhaniyi mu November 1946 yomwe idasindikizidwa patsamba loyamba la manyuzipepala angapo
politics
Online/Wikipedia
en3577
A charismatic figure, he advocated social justice, honest government, and political freedom, while his party exposed corruption and demanded reform
Iye anali munthu wachikoka, ankalimbikitsa chilungamo cha anthu, boma loona mtima, ndi ufulu wa ndale, pamene chipani chake chinavumbula katangale ndi kufuna kuti zinthu zisinthe
politics
Online/Wikipedia
en3578
Student violence escalated after Grau employed gang leaders as police officers, and Castro soon received a death threat urging him to leave the university
Ziwawa za ophunzira zidakula pambuyo poti Grau adalemba ntchito atsogoleri a zigawenga ngati apolisi, ndipo posakhalitsa Castro adaopsezedwa kuti aphedwa ndikumuuza kuti achoke kuyunivesite
politics
Online/Wikipedia
en3579
However, he refused to do so and began to carry a gun and surround himself with armed friends
Komabe, iye anakana kutero ndipo anayamba kunyamula mfuti ndi kudzizungulira ndi anzake okhala ndi zida
politics
Online/Wikipedia
en3580
In later years, anti-Castro dissidents accused him of committing gang-related assassinations at the time, but these accusations remain unproven
M'zaka zamtsogolo, otsutsana ndi Castro adamuimba mlandu wopha anthu okhudzana ndi zigawenga panthawiyo, koma milanduyi sinatsimikizidwe
politics
Online/Wikipedia
en3581
I joined the people; I grabbed a rifle in a police station that collapsed when it was rushed by a crowd. I witnessed the spectacle of a totally spontaneous revolution
Ndinalowa nawo anthuwo; Ndinatenga mfuti papolisi yomwe inagwa pamene gulu la anthu linathamangitsidwa. Ndidawona chiwonetsero chakusintha kodzidzimutsa
politics
Online/Wikipedia
en3582
That experience led me to identify myself even more with the cause of the people
Chochitika chimenecho chinandipangitsa kudzizindikiritsa ndekha ndi chifukwa cha anthu
politics
Online/Wikipedia
en3583
Returning to Havana, Castro took a leading role in student protests against the killing of a high school pupil by government bodyguards
Pobwerera ku Havana, Castro adatsogolera ziwonetsero za ophunzira zotsutsa kuphedwa kwa mwana wasukulu yasekondale ndi alonda aboma
politics
Online/Wikipedia
en3584
The protests, accompanied by a crackdown on those considered communists, led to violent clashes between activists and police in February 1948, in which Castro was badly beaten
Zionetserozi, zomwe zidatsagana ndi anthu omwe amawaona ngati achikomyunizimu, zidayambitsa mikangano pakati pa omenyera ufulu ndi apolisi mu February 1948, pomwe Castro adamenyedwa koyipa
politics
Online/Wikipedia
en3585
Returning to Cuba, Castro became a prominent figure in protests against government attempts to raise bus fares
Pobwerera ku Cuba, Castro adakhala wotchuka paziwonetsero zotsutsana ndi zomwe boma likufuna kukweza mabasi
politics
Online/Wikipedia
en3586
That year, he married Mirta Díaz Balart, a student from a wealthy family, through whom he was exposed to the lifestyle of the Cuban elite
Chaka chimenecho, adakwatira Mirta Díaz Balart, wophunzira wochokera ku banja lolemera, kudzera mwa iye adadziwika ndi moyo wa anthu osankhika aku Cuba
politics
Online/Wikipedia
en3587
The relationship was a love match, disapproved of by both families, but Díaz Balart's father gave them tens of thousands of dollars, along with Batista, to spend on a three-month New York City honeymoon
Ubalewu unali mgwirizano wachikondi, wosagwirizana ndi mabanja onse awiri, koma abambo a Díaz Balart adawapatsa madola masauzande ambiri, pamodzi ndi Batista, kuti azigwiritsa ntchito miyezi itatu ku New York City
politics
Online/Wikipedia
en3588
I was like a blindfolded man in a forest, who doesn't even know where north or south is. If you don't eventually come to truly understand the history of the class struggle, or at least have a clear idea that society is divided between the rich and the poor, and that some people subjugate and exploit other people, you're lost in a forest, not knowing anything
Ndinali ngati munthu wakhungu m’nkhalango, amene sadziwa n’komwe kumene kuli kumpoto kapena kum’mwera. Ngati simufika pakumvetsetsa mbiri ya nkhondo yamagulu, kapena kukhala ndi lingaliro lomveka bwino kuti gulu lagawikana pakati pa olemera ndi osauka, ndikuti anthu ena amagonjetsera ndi kudyera masuku pamutu anthu ena, ndiye kuti mwatayika. nkhalango, osadziwa kalikonse
politics
Online/Wikipedia
en3589
In response, Prío agreed to quell the gangs, but found them too powerful to control. Visiting Havana's poorest neighborhoods, he became active in the student anti-racist campaign
Poyankha, Prío adavomera kuthetsa zigawengazo, koma adawapeza amphamvu kwambiri kuti sangawalamulire. Kuyendera madera osauka kwambiri a Havana, adayamba kuchita nawo kampeni yolimbana ndi tsankho la ophunzira
politics
Online/Wikipedia
en3590
Castro continued to put himself at risk, staying active in the city's politics and joining the 30 September Movement
Castro adapitilizabe kuyika pachiwopsezo, kukhalabe wotanganidwa mu ndale zamzindawu ndikulowa nawo 30 September Movement
politics
Online/Wikipedia
en3591
The group's purpose was to oppose the influence of the violent gangs within the university; despite his promises, Prío had failed to control the situation, instead offering many of their senior members jobs in government ministries
Cholinga cha gululi chinali kutsutsa chisonkhezero cha magulu achiwawa mkati mwa yunivesite; ngakhale adalonjeza, Prío adalephera kuwongolera zinthu, m'malo mwake adapatsa akuluakulu awo ambiri ntchito m'maunduna a boma
politics
Online/Wikipedia
en3592
Castro volunteered to deliver a speech for the Movement on 13 November, exposing the government's secret deals with the gangs and identifying key members
Castro adadzipereka kuti akayankhule za gululi pa 13 November, kuwulula zomwe boma likuchita ndi zigawenga komanso kuzindikira mamembala ofunikira
politics
Online/Wikipedia
en3593
Attracting the attention of the national press, the speech angered the gangs and Castro fled into hiding, first in the countryside and then in the US
Pokopa chidwi cha atolankhani mdzikolo, zolankhulazo zidakwiyitsa zigawengazo ndipo Castro adathawa kukabisala, poyamba kumidzi kenako ku US
politics
Online/Wikipedia
en3594
Returning to Havana several weeks later, Castro laid low and focused on his university studies, graduating as a Doctor of Law in September 1950. Castro intended to overthrow the presidency of General Fulgencio Batista
Atabwerera ku Havana milungu ingapo pambuyo pake, Castro anadekha ndikuika maganizo ake pa maphunziro ake a ku yunivesite ndipo atamaliza maphunziro ake monga Doctor of Law mu September 1950. Castro ankafuna kugwetsa utsogoleri wa General Fulgencio Batista
politics
Online/Wikipedia
en3595
Castro co-founded a legal partnership that primarily catered to poor Cubans, although it proved a financial failure
Castro adayambitsa mgwirizano wazamalamulo womwe udathandizira anthu osauka aku Cuba, ngakhale zidawonetsa kulephera kwachuma
politics
Online/Wikipedia
en3596
Caring little for money or material goods, Castro failed to pay his bills; his furniture was repossessed and electricity cut off, distressing his wife
Posalabadira za ndalama kapena katundu, Castro analephera kulipira ngongole zake; katundu wake wamnyumba adalandidwa ndipo magetsi adadulidwa, zomwe zidakhumudwitsa mkazi wake
politics
Online/Wikipedia
en3597
He took part in a high school protest in Cienfuegos in November 1950, fighting with police to protest the Education Ministry's ban on student associations; he was arrested and charged for violent conduct, but the magistrate dismissed the charges
Anachita nawo zionetsero za sukulu ya sekondale ku Cienfuegos mu November 1950, akumenyana ndi apolisi kuti atsutsane ndi kuletsa kwa Unduna wa Maphunziro ku mabungwe a ophunzira; adamangidwa ndikumuzenga mlandu wochita zachiwawa, koma woweruza milandu adakana
politics
Online/Wikipedia
en3598
He was instead nominated as a candidate for the House of Representatives by party members in Havana's poorest districts and began campaigning
M'malo mwake adasankhidwa kukhala phungu wa Nyumba ya Oyimilira ndi mamembala a chipani m'madera osauka kwambiri a Havana ndipo anayamba kuchita kampeni
politics
Online/Wikipedia
en3599
During his campaign, Castro met with General Fulgencio Batista, the former president who had returned to politics with the Unitary Action Party
Pa nthawi ya yokopa anthu, Castro adakumana ndi mtsogoleri wankhondo Fulgencio Batista, mtsogoleri wakale yemwe adabwerera ku ndale ndi chipani cha Unitary Action.
politics
Online/Wikipedia
en3600
Batista offered him a place in his administration if he was successful; although both opposed Prío's administration, their meeting never got beyond polite generalities
Batista anamupatsa malo mu ulamuliro wake ngati atapambana; ngakhale onse awiri adatsutsana ndi kayendetsedwe ka boma ka Prío, misonkhano yawo mopyolera zokambirana zongocheza
politics
Online/Wikipedia
en3601
On 10 March 1952, Batista seized power in a military coup, with Prío fleeing to Mexico. Declaring himself president, Batista cancelled the planned presidential elections, describing his new system as "disciplined democracy"
Pa 10 March 1952, Batista adalanda mphamvu pagulu lankhondo, pomwe Prío adathawira ku Mexico. Podziwonetsa yekha kukhala mtsogoleri, Batista adaletsa zisankho zautsogoleri zomwe zidakonzedwa, ponena kuti dongosolo lake latsopanoli ndi 'ufulu wodzilamulira wosunga mwambo"
politics
Online/Wikipedia